ngati mzimu ukhala mwa munthu umalingalira za mau achikondi konda nzako monga uzikondela mwini koma ngati uzimu wachoka pa munthu ndi umunthuso umasowa ndipomwe maganizo oipa amabwela kufunsila mkazi wa nzako that means No love at all mwachidule zosayenela kutelo ine ndati NO .
Abena, Sellina & Sandra mukhalitse❤❤
Mmmmm ai zosakhala bwino izi ufiti umalowapo apa ai simnazikonde
Perfectly words
Great words moms
❤
😂😂zimachitika zimenezo ine zinandichitikirapo zimenezo zanga weniwen zimatheka
Kuno Zambia tikumvelelela
Ziliko zimenezi🎉🎉🎉
Your best friend can be your best enemy....anthufe kuganiza ndikosiyana....that's nature .
Pg iyiyi imandiwaza😂😂😂
Azimai mumatha
Mmm azimayi mudziwe kuti, mamuna ngati wafika saze yokufusilani, mumayambitsa ndinu, mamuna kwake mkuyankhula, koma kufunsira kuli ndi azimayinu, ma green light.
ngati mzimu ukhala mwa munthu umalingalira za mau achikondi konda nzako monga uzikondela mwini koma ngati uzimu wachoka pa munthu ndi umunthuso umasowa ndipomwe maganizo oipa amabwela kufunsila mkazi wa nzako that means No love at all mwachidule zosayenela kutelo ine ndati NO .
Shaaaaa azimai zikomo
Yankho should be NO, osachulutsa Gaga m'diwa......
Azimayi inu mwaitokota
Abena mumuna ngati akufusila.mwafomele ndisochokela kumwamba
Ayi usavomere
❤😂😂😂
Mpole moto adzimayi 🤣🤣🤣
Umukane
Kkkķkkkk
Kkkkk