Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Mayianu ndawatayira kamtengo Mukuoneka kumasuka mosonyeza kuti mukudzidziwatu .😂😂
Km winiko .....uja another name Mr Nyooo abwereso puliz😂😂😂😂
Mmmmm zokaikisa😂
Ndikudutsa munsewumu ndat ndikhwete kuno😂😂😂😂
Plz DR Manganya bring Winiko ...I love you all guys
Ukufuna azikangana 😂
Winiko sali mwakalee..mtayeeni
Juzi yokongola ndaivala dele😅😅😅😅😅😅😅
Komatu magaye, komaliteni ku nathenje😂, mwatitolatu apa😂
Koma kuthamanga kumeneku 😂😂😂🤣we need masikono and winiko back plz
Ngati wamukonda mufusire basi wako akakhara kwawo kkk😅
Manga😂😂😂😂kuthawaa kumeneko muti nchan😂😂
Maganya akuti koma mayi anu inu ❤❤Tikuferanji still Trending
Kkkkkkk akuti anabwera pano kuzagwira ntchito zonse naye ndi munthu kkkkkkk kma akazi
I like the Chewa flavour... ko Mariteni...nikhwetere uku
😂😂😂
Kkkkkkkk manganya woyeeee. Ayiyaiyaaaa guys mmabebetsa
🤣🤣🤣🤣 this is my house kkkkkk koma Manganya
😂😂😂Koma Maganya muli liwiro Koma abweletseni ma Sikono
Akuti manga no 🤣🤣🤣🤣 azimu oyera atero
Ayi Kani sipiki iwe ndindani ine ndi jetu 🤣🤣🤣
Speed ya Manganya ndiyamoto😂
Manganya sadzathekayi kkkkkk
Manganya kuthawa kokha alibe zake 😂😂😂😂
Tikufelanji is not the same again bring ma sikono and winiko back azukulu anga
Ndipo inu aaah
Manganya ndi aviator payekha 😅😅😅😅
Ayi Kani sipiki ingilishi 😂😅
Ntchito iliyonse akhoza kugwira 🤣😂😂
Kodi mwanyamula iPhone a Thumbi? Nde gesture ya manjayo cholinga tione lamya 😂😂😂😂
Koma Manga 😂😂😂😂😂....great one....
Very lesson, keep up tikufelanji
Kkkkkkk koma vice president momwe akuthamangila 😂😂😂😂uyu sangamuphe olo ndegeyo azichita kuyiposa kuthamanga
Mofaya Mr VP, kkkkkkk masewero musasiye 😅😂
Keep it up tikuferanji team❤
😂😂😂😂Komanso nanyoni Eeeee ayi akuti sakuopa Mai chisi😂😂😂😂
Bring back winiko guyz❤❤❤❤
amene mumajambula this video be mindful of the background noise that you make while taking this videos we can hear the footsteps
Komatu Nanyoni umatha ❤
first to comment ndikufuna zanga😂❤❤❤
Ine pano ase
Koma Manganya amathamanga osati masewera😂😂🙌🙌
Manganya Ali nkuliswatu liwiro😂😂
Kkkkk koma manganya wadya gear😂😂😂😂😂
Ai kani sipiki....afuna ntchitoooo😂😂😂😂
kkkkk avayisi musamusiye nyo winiko
Kamanganya kasokoneza banja uku😅😅😅
Ati ukati usamalike ndikudzidzilaku ufa ndikudzidzila chilichose peza uvale 😂😂👘
ATI junzi Yokongola kkkkk km manganya anabwera 😂😂😂😂😂
Ukati usamalike ndikuzizilaku ufa peza chilichonse uvale
Every test is a new test
Koma kwachema 😂😂😂 manganya
Mr manganya Ngat zingateke we miss nyooo❤
Matumbi mulimbe nazo 😂😂😂😂
Kukazizila ndimene zimakhalila 🎶❤
Koma manganya eshhhhh 😂😂😂
Naye ndi munthu😂😂😂😂😂
Mr Nyo make Sikono pls
Komatu aku Nathenje mwatiwonjeza😂😂😂
Kkkk koma manganya eeee
Kkkk or kutenga cup osaopa kuyexgesa edzi
Uyuyu akamapanga masewelo amaoneka wa zelu koma ku bomaku zelo pa ten
Kkkkkkk
Ubwino wake salipo ekha m,bomamo alimo ambili or uchite zabwino wina ngat akuyipitsa basitu palibe chilipo nonse muyipa fenkis kumpando 😅
Kuthamanga ngati mphepo ya mkuntho Mannga🤣🤣🤣🤣🤣
Watching from mwineriwa vg mulanje ❤
Kom manga ndiphyuutaa kung'ambikako kkkk
Hahahahahhahahahahah koma liwilotu a VP
Koma a vp akati athamange kkkkkkk, mungofunik mubwer winik cz akusowa woyambisa ndewu
Nkhweta😂😂😂😂
Winiko Ali Kuti the DC pangolin
Mwana oopsa kwambiri
Ndipo kukhara ngati akulowesapo ndale
Nanyoni ndiokonda zinthu 😅😅😅😅
Bwelesani winiko
Kkkkkk manganya ndiye wanthawa
Mumakwana a mr manganya 😂😂
Ayi Kona anthu mumaakita😅😅😅
Ati olo azikatunga ndi cup kkkkk
Koma,, ,,mangany👌
Nice one, koma mukumachedwa kutulutsa inatu Mabwana, taponyani ina changu. Very interested now kuti mwapanga add ma comedian ena, thats nice. Koma Mayi a Sikono bwanji? Tawasowa kooopsa
ruclips.net/video/iy8Tu8AZixc/видео.htmlsi=gtb8GuGWRoe3LhHJ
Iyoo
Ati mukanavulala Lero mai😂😂
Manga wabwera ngat coming ❤❤❤
Manganya tikufunaso madam anu ma sikono❤
😂😂😂😂😂 km Nanyon
🤣🤣🤣 l can sipiki english for me mumatisangalatsa
Kkkk winiko 😂alikut
Kkkk koma manga ndi speed link tu kkkk amaliyala liwiro kooopsa
😂😂😂😂 speed ili nd Manga
Aphule liwiro kkkkkk
Kunlango kwaugele.... 😂😂😂😂😂
Kusowa kwakupitaaaa🤣🤣🤣🤣
Bosslady chiyao kkkk
Kukwapuka kumeneko anduna😅😅
Manganya kuthamanga ngati nyumba ikupsa
Koma manganya adakoza😂😂
Kkkkkk liwiro apule
Koma ndye kuthwatu😂
Koma manganya muli liwiro kkkkkkk
Koma doc pa speed pokha kulibeso
Manganya giving good vision to young ones
Hon kuthamanga choncho 😂😂😂
Kkkkkkkk amanga mumakwana mmmmmm
speed yamphepo
Manganya amakwana ndiwachikulire Ndipo muluso lake amatsangalarsa ndikuphumzitsa mmene tingapewere nthenda ya HIV
Manganya amanjonjola😂😂😂😂😂
Kom ma comment Ali apa kuwawelenga ku English translation utha kufa ndkuseka
Usampatse ndimpatsaaaaaa
Mwabwera magyz
Koma manganya 😂😂😂😂😂
Manganya mupole motto
Akuti kum'lango awugere
Mayianu ndawatayira kamtengo
Mukuoneka kumasuka mosonyeza kuti mukudzidziwatu .
😂😂

Bring back winiko guyz
❤❤❤❤
amene mumajambula this video be mindful of the background noise that you make while taking this videos we can hear the footsteps
Komatu Nanyoni umatha ❤
first to comment ndikufuna zanga😂❤❤❤
Ine pano ase
Koma Manganya amathamanga osati masewera😂😂🙌🙌
Manganya Ali nkuliswatu liwiro😂😂
Kkkkk koma manganya wadya gear😂😂😂😂😂
Ai kani sipiki....afuna ntchitoooo😂😂😂😂
kkkkk avayisi musamusiye nyo winiko
Kamanganya kasokoneza banja uku😅😅😅
Ati ukati usamalike ndikudzidzilaku ufa ndikudzidzila chilichose peza uvale 😂😂👘
ATI junzi Yokongola kkkkk km manganya anabwera 😂😂😂😂😂
Ukati usamalike ndikuzizilaku ufa peza chilichonse uvale
Every test is a new test
Koma kwachema 😂😂😂 manganya
Mr manganya
Ngat zingateke we miss nyooo❤