COMRADE NTANYIWA PA LIMPOPO FM - KOMA ACHAKWERA UMUNTHU NDI UZIMU MULINAWO?

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 10 дек 2024

Комментарии • 229

  • @VictoriaBakuli
    @VictoriaBakuli Месяц назад +13

    Ntanyiwa walusa lero big up comrade I love you ❤

  • @daviskamonde4882
    @daviskamonde4882 Месяц назад +3

    I believe in you Ntanyiwa and BMtv.
    You are doing great work!!

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole Месяц назад +10

    Ngati amakwanitsa kupha anthu sangakhale ndi chisoni uyuyu ndi satana ndipo imfa ikumuphonya pati aaaa

    • @AsiyatuMazembere
      @AsiyatuMazembere Месяц назад

      Ii anthu otelewo safelamotu amasiyadala kt azichimwilabe

  • @JamayakoJamayako-rv2he
    @JamayakoJamayako-rv2he Месяц назад +2

    Our one of prophet
    Keep the fire burning

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule Месяц назад +3

    Mutanyiwa God bless you ❤

  • @AbudullahDaudi
    @AbudullahDaudi Месяц назад +1

    Mumatiyimilira Mr Comrade inuyo mulungu apaseni moyo wautali us Malawian,s always we are prayer hard for you Comrade

  • @BennettNjedza
    @BennettNjedza Месяц назад +6

    Akanakhala ndi umunthu chakwera akanachita resign anthu ochuluka mmalawi sakumufuna, ndipo mcp anthu anaichosa mmalingaliro kale kale ndipo kupanda amakhoti ndi chilima sizikanatheka kulamula mcp nde mmalo moti achite zinthu zokuti anthu awakonde akungozunza anthu sprit ya 1960 akuibweresa lero nthawi ya democracy shem, Achakwera chitani manyazi Musachite kupangidwa za Gadafi chonde Ndinu Man of God chosani mtima wa mwalawo

  • @FlorryVugy-g4f
    @FlorryVugy-g4f Месяц назад +4

    Powerful mr Mtanyiwa , I like you lets fight for freedom boma ili mmm its fool of shit

  • @TimeAbilu
    @TimeAbilu Месяц назад +1

    Masha Allah Masha Allah comrade mtanyiwa u can't die because u don't have any problem to anyone

  • @Fanzo-h2l
    @Fanzo-h2l Месяц назад +3

    Mmmm Ambuye imilirani mu dziko la Malawi ndikupulumutsa Malawi walira momvetsa chisoni Ntanyiwa kulilira amalawi 😭😭😭😭

  • @ElsaMalunga
    @ElsaMalunga Месяц назад +1

    Abusa awawa taona abusa koma mulungu mulungu mulungu mulungu kd inuyo mulungu mulindiphavu zochepa tiziti achakwera alindi phavu kupambana inuyo mukulora munthu modzi azuze ntundu wanu mukumusiilaji Rab Rab Rab sharikati mulungu tileretseni Kwa farao amen

  • @LoveKhobiri
    @LoveKhobiri Месяц назад +1

    God be with u my brother, enough is enough

  • @gideonMataya
    @gideonMataya Месяц назад +1

    Am much proud of you brother, tell them.

  • @VincentKalata
    @VincentKalata Месяц назад +1

    Eshiiiii no word with this leadership

  • @NdemboBrothersAdam
    @NdemboBrothersAdam Месяц назад +3

    Akuyenera kubweza ndalama kwa anthu amenewa chifukwa kuzipha nkwachiziwikire ngati salandira ndalama zomwe anaononga plus transport abweze a immigration

  • @McshonWilliam
    @McshonWilliam Месяц назад +1

    our king dont worry god is with you nothing will happen in the name of otilengayo

  • @EmmanuelSteve-q7b
    @EmmanuelSteve-q7b Месяц назад +1

    Congratulations comrade mthanyiwa

  • @oscarkadzombe7266
    @oscarkadzombe7266 Месяц назад +2

    Ameneyu Si president komaa namathanyula

  • @bissankal774
    @bissankal774 Месяц назад +2

    😢 iyiy nd one of the major issues in our country and eis we have finished.

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 Месяц назад +2

    Osaopa osatopa osafooka Mr Comrade ntanyiwa Allah alipo

  • @BenJamson
    @BenJamson Месяц назад +1

    Comrade we trust on you and we love you

  • @getrudeminikwa9636
    @getrudeminikwa9636 Месяц назад +5

    So painful painful serious

  • @EstherBair
    @EstherBair Месяц назад +1

    I love you mumatiimilira inuyo 🔥🔥

  • @Sophie-b5o6c
    @Sophie-b5o6c Месяц назад +1

    Chakwela unzimu unachoka kalekale,taganizani kunenedwa koseku osanvachisoni!!olo galu kumupanga choka amasuthapo komauyuaaaah Sina oneanachezela kuona ndaonela chakwela ambuye tiyendeleni.atichimwitsa malakhuliewe amen

  • @HassanBabujr
    @HassanBabujr Месяц назад +1

    More 🔥 mr

  • @AshrafShadid
    @AshrafShadid Месяц назад +3

    Vuto sichina ife kusava/komaso kusayamika tinkanyoza munthu waumunthu kumasula balaba.... Sitinati ndipo nde tinya zenizeni, apa tikuvutikira limodzi ndiomwe amakhuta nkumakasaka mavutowa😢😂😂

  • @JonaSato-j8e
    @JonaSato-j8e Месяц назад +1

    That's true ❤❤❤❤

  • @VenançioZocueza
    @VenançioZocueza Месяц назад +1

    Freedom fighter,umakwana.

  • @Spaw-BTheGogoBoy
    @Spaw-BTheGogoBoy Месяц назад +1

    Limpopo fm 🔥🔥

  • @HappyBhanda
    @HappyBhanda Месяц назад +1

    Mwakiyatu lero comrade muuzeni zooona ndakunyadilani

  • @ChimwemweSabuni
    @ChimwemweSabuni Месяц назад +3

    Mbambande comrade zatkwana ziko likhala ngat tachita kubweleka kut tikatjana nalo tibweza kwa mwini eshhhhh😢😢

  • @HabiboZimba
    @HabiboZimba Месяц назад +2

    ❤❤❤❤❤ ndagalu kwambiri iiiiii

  • @FredKanyerere
    @FredKanyerere Месяц назад +1

    So sad serious painful,comrade.

  • @MikeSymon-si8dw
    @MikeSymon-si8dw Месяц назад +1

    Mulungu atichitire chifundo kma eeee😢😢😢😢

  • @takomtuwa
    @takomtuwa Месяц назад +1

    A Word Is Enough For The Wise. Yakwiya Ndi Mizimu

  • @steavejafali
    @steavejafali Месяц назад

    Comrade more fire zoona sakutiona ngati ifeso anthu ngati iyeyo chofunika ndikukwiya basi kukayenda pamsewo

  • @PaulBandason
    @PaulBandason Месяц назад

    Mr mtanyiwa let's fight for freedom,

  • @AdamDawood-h7l
    @AdamDawood-h7l Месяц назад +1

    Comuledi mwatopainu ndikuyakhula. Tiitanileni ameyano. Ndikukamu. Pwasamulakunyumbakwakeko. Chakwela eeeeè watikwana. 😢😢😢😢😢😢😢😢😢

  • @JohnMota-o2u
    @JohnMota-o2u Месяц назад +1

    The only way is to dethrone this Ideh Amin Chakwera

  • @OsmanDonMussah
    @OsmanDonMussah Месяц назад +1

    Comrade musazafe Malawians loves you more

  • @CharityPhiri-q1c
    @CharityPhiri-q1c Месяц назад +1

    Dziko likuyendesedwa ndi ma mafia yoooooh zinthu zavuta ine kumva chison😊

  • @SamalaniMaloya
    @SamalaniMaloya Месяц назад +2

    Chakwera waonongat zikoli ndipo ameneyu ndisatanic kwambiri umunthu alibe😂😂😂😂😂😂

  • @JohnGreen-v8f
    @JohnGreen-v8f Месяц назад +2

    Biggy mtanyiwa walusilatu ndipo chakwela akadakhala pafupi inali mbama

  • @RoseChimbwefu
    @RoseChimbwefu Месяц назад

    Exactly we are seek and tired Mr ntanyiwa eshiii

  • @FatimanickisJaffer
    @FatimanickisJaffer Месяц назад +1

    Ndip angakhal manyaz alibe zoti adzachoka pa mpando ai sakudziwa ai km mulungu adanena kut masiku yakusadziwa yehova adalekelera apapa mulungu wanthu ndiwankul akudziwa zosez thaw kubwera azatiyankha

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 Месяц назад +4

    Eish koma zinthu zake mmmmh

  • @StewartGoma
    @StewartGoma Месяц назад +1

    Let's devided malawi to make three country northern Region central Region n southern Region

  • @MaxonNyirongo
    @MaxonNyirongo Месяц назад +1

    Mulungu atinthandize mmm😢

  • @GileNyamula
    @GileNyamula Месяц назад +1

    Ntanyiwa umakwanila❤

  • @ThomasiSalijeni
    @ThomasiSalijeni Месяц назад +1

    Amene akumati boma ndilomweli akuziwa kt chikangawa ndichisilu president opanda vision

  • @ThivadoartistDyson
    @ThivadoartistDyson Месяц назад +1

    Mtendele chakwela suupeza ndipo bed lako likhala ngat mphasa, chimodzmodz kunkuyu komaso chimwendo banda

  • @lyiemanganjira9708
    @lyiemanganjira9708 Месяц назад +1

    Ayi umunthu ndie mulibemo,, koma nthawi ikubwera Mulungu si James

  • @SamuelChiwere
    @SamuelChiwere Месяц назад +1

    😢😢😢 mine is invalid koma l can't do mistake to come right now ku Malawi kuti ndikudzapanga renew or another one while l truely know that instead of making my blight future ndidzangodzibweletselapo mavuto upon my life because of a Fake passport, my best wishes it May goes to Peter wa Muthalika for me to had a Original Passport even though right now is invalid komabe am still seeing my goals because ndikadari komkuno not in Malawi 🙏

  • @TayibuUmalikauta
    @TayibuUmalikauta Месяц назад +1

    Komadi bwenz akumatinvera chisoni anthu osauka ife apa nde sanaganizepo😭😭😭

  • @AbudullahDaudi
    @AbudullahDaudi Месяц назад +1

    Chakwera ndi m,fiti ndipo akuyenera kufa even before zisankho

  • @WesleyKunjilika-t2y
    @WesleyKunjilika-t2y Месяц назад +1

    Achakwera please dzikoli silanu chonde anthu akuvutika munthu wavutika kusaka ndalama kukapatsidwa passport ndi Boma yopanda ntchito.chabwino abwezereni ndalama zawo

  • @MosesTangwe
    @MosesTangwe Месяц назад +1

    Lavula Moto m'bale wanga. enough is enough we are tired.ma business athu aphwasuka Palibeso chikuyenda.moyo ukuwawa
    Misozi yomwe tikugwesa panoyi mulungu ayankha pompano sikaleso ai😢😢😢😢

  • @AdamDawood-h7l
    @AdamDawood-h7l Месяц назад +1

    Ingomuphulisani. Inundi. Boni kalindo. Kutimudikile. Zoti atulepasi udindo sangatule. M,fitiameneyo. Komamu ngomulodzabasi. 😢😢😢😢 18:26 18:28 18:29

  • @PhillipChisanu-k3r
    @PhillipChisanu-k3r Месяц назад +1

    God! For give us, we were absent minded, this is too much,onse omwe amkat DPP ichoke pano ndimanyazi okhaokha,APM achoke akuba,APM ndi nkhalamba,pano ikufunikanso,ai zkom

    • @ronaldordinga6537
      @ronaldordinga6537 Месяц назад

      Chakwera wangowonjeza,,,,, koma APM nayeso amalakwisa onsewa ndi akuba kuba kwakeso kopanga kuganizira anthu ovota ifeee

  • @HappinessGelapindan
    @HappinessGelapindan Месяц назад +1

    Chakwela mau anga paiweyo musiku laleloli ndikuti iweyo ngati mulungu amadalisa tchimo lamunthu akudalise iweyo komaso ngatiso mulungu yemweyo amalanga munthu ochimwa iweyo iweyo mulungu awone nawe chochita zikomo sithembelelo koma tidzava😢

  • @GiftNgwira-e8l
    @GiftNgwira-e8l Месяц назад +1

    Eish boma ili lafika pauchitsiru kwambiri mpaka kumatipatsa passport yafake.Chakwera ndi galu kwabasi

  • @blessingsmwenela1308
    @blessingsmwenela1308 Месяц назад +1

    Na lero wakwiya zoona ndipo wayankhula zofunika...it's really too much

  • @cynthiataulo5211
    @cynthiataulo5211 Месяц назад +1

    Anthu oipa awa, anthu ambiri akuzunzika silently, ena anachosedwa ntchito chifukwa chozuzula nkhaza za mcp.

  • @petermagombo2733
    @petermagombo2733 Месяц назад +1

    This is too much, ma guy you know how stressed when you traveling from Malawi to South Africa yooo .

  • @WilliamNhlane-fd9hi
    @WilliamNhlane-fd9hi Месяц назад +1

    Chakwera akawinaso tigawana zigawo . Chakwera akalamule chigawo chapakati , kumpoto ndi kumwera sitikumufuna

  • @ImraanSamson
    @ImraanSamson Месяц назад

    Let's gather here 😅😅

  • @DoreenLikomeNkhoma
    @DoreenLikomeNkhoma Месяц назад

    😂😂😂ndye mwati mphanvu zoposa mulungu eti??? Ay zikomoo

  • @GeoffreyMaulana-rh5rx
    @GeoffreyMaulana-rh5rx Месяц назад +1

    Achakwela mavuto amunthu olo manyazialibe ndizianthu zake zazikulumituzija

  • @joebonface4443
    @joebonface4443 Месяц назад +1

    Am very sorry for those people sent back for using fake passport unknowingly. Malawi is @ Roundabout.

  • @nthandozamantungwakhumalo1507
    @nthandozamantungwakhumalo1507 Месяц назад +1

    koma kumalawi mmmm tivutikadi ndi agalu awa

  • @masingatichilumba8263
    @masingatichilumba8263 Месяц назад +1

    akamati boma ndi lomweli sindikugwilizana nazo awa achoke basi atikwana ndi nkhanza zawo

  • @MuhamadMpate
    @MuhamadMpate Месяц назад +1

    Or ma licence akufufutika nkhope

  • @JoaquimElidioChiwisse
    @JoaquimElidioChiwisse Месяц назад +2

    Ndipo zaonjeza anthu mpaka kubwezedwa zomvetsa chisoni

  • @TayibuUmalikauta
    @TayibuUmalikauta Месяц назад +1

    Akufuna angotimaliza bas kutisakasako munthu uyu

  • @Rwabill.s.c.zErick-k5e
    @Rwabill.s.c.zErick-k5e Месяц назад +1

    Zimenezo alibe nazo ntchito ngati anampha anthu mundeg anthu ten komanso angopha anthu osalakwa

  • @FrankWales-p7t
    @FrankWales-p7t Месяц назад +3

    Mulungu azikudalisani thawizonse

  • @StaffordKamanga
    @StaffordKamanga Месяц назад

    Ntanyiwa go forward,to inform Malawians all secret,things.

  • @NuneAxmed
    @NuneAxmed Месяц назад

    Mr ntanyiwa ndi chilungamo zomwe mukunenazo

  • @RuthTimothyChirwa
    @RuthTimothyChirwa Месяц назад +1

    Apolice A Malawi palibe chimene akuchita

  • @hassanmussa1356
    @hassanmussa1356 Месяц назад

    More fire Mr

  • @SifatiMoses
    @SifatiMoses Месяц назад +1

    Chakwera asamawatenge anthu ngati opusa, ndipo malawi wake siwaleloyu amene azimutengera kutodzo ngati maliro anjoka anthu anatopa ndi chilungamo. Anthu akatopa samawelenganso kuti ndi president wa dziko amapanga ziganizo panthawi imeneyo asamale kwambiri ngati amanamidzidwa azachisiya. Anthu amalorelatu kuswa mutu through sniper bola apulumutse miyoyo ya anthu ambiri chakwera usamale.

  • @SpiweKatunga
    @SpiweKatunga Месяц назад +1

    Koma izizi nde zanyanya enafe tikufuna Kuti tipange ma passport nde tipanga bwa

  • @SABITIKAISI
    @SABITIKAISI Месяц назад

    😢😢😢 ANYANI amthu a mcp

  • @tingamasi106
    @tingamasi106 Месяц назад +1

    Pliz we love you but pliz do urself a favor by speaking in chichewa

  • @malingakazembe8354
    @malingakazembe8354 Месяц назад

    Just magic passport ya fegi guys ulendou wawutali

  • @EltiyaChirwa-fp7cz
    @EltiyaChirwa-fp7cz Месяц назад

    Lero mthanyiwa walusa osati masewera yoo

  • @BlessingsSuwedi-u9x
    @BlessingsSuwedi-u9x Месяц назад +1

    Inuyo mumaima pachilungamo osaopa ai

  • @NicksonMphipa
    @NicksonMphipa Месяц назад +1

    Nkhan yopweteka kwambiri chifukwa anthu akulipila ndalama ku bus zochuluka kwambiri pafupifupi k500000

  • @NaomieBanda-t6g
    @NaomieBanda-t6g Месяц назад +1

    Ineyo kuzakhala vuto yanga ngati will scan imigrants izakhala pavuto olo azandimanga

  • @YusufAlidi
    @YusufAlidi Месяц назад

    Eish zosayenda

  • @InockNtumwi
    @InockNtumwi Месяц назад

    Ine umandisangalasa kusekako😂😂😂😂

  • @HestingsEdward
    @HestingsEdward Месяц назад

    Passport bwana mungokhala ngati coupon yogulira fertilizer kuvetsa chisoni anyamata dziko layeni mumaudziwa ufolena kapena poti azanthu mudasankha kobadwira

  • @MphatsoGeorge
    @MphatsoGeorge Месяц назад

    Eti anthu athawira kuti ndiye awineso ameneyu ee ayi ambuy musalore 😢😢😢

  • @CharlesSungani-j8c
    @CharlesSungani-j8c Месяц назад +1

    Usadzafe ntanyii uzangosowa tizakufuna funa tizakupeza

  • @ChapwetekaChauluka
    @ChapwetekaChauluka Месяц назад +1

    Zoonadi Comrade anthu abwezedwa pa Beit Bridge boarder ...

    • @LindaKubala
      @LindaKubala Месяц назад

      Sad development 😢😢😢😢

  • @PempheroDindo
    @PempheroDindo Месяц назад

    Mbolatu😢

  • @ChisomoKasekera-ue3zq
    @ChisomoKasekera-ue3zq Месяц назад +1

    Akuopa kumangidwa apakula kwambiri mchifukwa akufuna asachokemo m'boma

  • @kantionsankhulani
    @kantionsankhulani Месяц назад +2

    Uzangosowa samwa madzi agalu amenewa abwapini

  • @rashirdbanda8204
    @rashirdbanda8204 Месяц назад

    So sad 😭😭😭

  • @EltiyaChirwa-fp7cz
    @EltiyaChirwa-fp7cz Месяц назад +1

    Zoonadi bwana wanga amandifuna week yapitayo what kind of president is his