Chingachitike ndichan Namadingo atakhala president Wa dziko?

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 25 окт 2024

Комментарии • 78

  • @sammalvitha
    @sammalvitha  Год назад +3

    Thanks for watching... Remember to like the video and share.... 🎉

  • @EmmanuelZiba-qz6ug
    @EmmanuelZiba-qz6ug Год назад +2

    Namadingo is are good person me from Lusaka Zambia am coming to vote for namadingo 👍👍👍

  • @chifundonkhoma-uv4bw
    @chifundonkhoma-uv4bw Год назад +3

    Guys palibe chimene chingalepheretse kuti Namadingo asakhale president wa dziko ....iyeso ndi munthu atha kukhala mtsogoleri, remember aliyese Ali ndi humble begining (anabadwa Ali maliseche ) don't underrate human... the future remains in hand of God....

  • @jayries35
    @jayries35 Год назад +1

    The voice and story line is promising for the great future

  • @paulbexter2641
    @paulbexter2641 Год назад +2

    Tinkati abusa ndamene akhoza kutitsogolera bwino pano aliyense akulira .nde or Namadingo atakhala president kucheza naye kwathela pomwepo ,pompo kusintha anzake ocheza naye

  • @susanthundu3771
    @susanthundu3771 Год назад

    We will vote for Namadingo

  • @MuhireDominic-rw4vf
    @MuhireDominic-rw4vf 6 месяцев назад

    Ameneyo ngat watopa nd kuimba akayambe kuphunzitsa ku primary

  • @jaysurpresa1999
    @jaysurpresa1999 Год назад

    Keep up the good work

  • @chipibanda1611
    @chipibanda1611 Год назад

    Adzaimila ku Zambia kapena Malawi I understand that he is a Zambian citizen

  • @StaphelMvula
    @StaphelMvula 8 месяцев назад

    "Dziko linapita patsogolo ndi ma jokes"... Inu kazikakumbani manda palibe chanzeru mukukamba

  • @DavidAllie-j1i
    @DavidAllie-j1i 7 месяцев назад

    ❤sure

  • @enerstmwitha392
    @enerstmwitha392 Год назад

    Alise athakukhala president chifukwa bili imatuuza sukulu sotsongoleli kunali president ambili Ku African osapita kusulu

  • @josiahgarley3824
    @josiahgarley3824 Год назад

    Much as i love Namadingo but he is not fit to be a president.Mwayamba zachibwana

  • @chrissygama8678
    @chrissygama8678 Год назад +1

    Nanunso mumasowa zokamba nthaw zina bwanji

  • @unarinematshomo2841
    @unarinematshomo2841 Год назад

    I think Namandingo atakhala president azathula dziko la Malawi .

  • @bornface4786
    @bornface4786 Год назад

    Why not Lucius Banda

  • @paultembo9550
    @paultembo9550 Год назад

    va ziii iwe chimanga no music kagoneni che

  • @ZahirZaheer-h3d
    @ZahirZaheer-h3d Год назад

    Kodi Namadingo simunthu woyimba, iyeyo ndi wa mash up not singer

  • @laurankhana9833
    @laurankhana9833 Год назад

    Achinyamata Bola mwina zitukuko zingapitile kutsogolo nanga achikulire awa amapanga zatsogolo lawo ndi Banja lawo zayeseni namadingo zizaoneka 2025

  • @jameschidafumbwa1039
    @jameschidafumbwa1039 Год назад +2

    Kudwala sikugona pa phasa pokhayi, ena amayenda akudwa ngati iweyo zooona ungamaganize mbwelerazo😅😅😅

  • @simeonkhamwaha8529
    @simeonkhamwaha8529 Год назад

    Sam apa ndiye mwapala tu sikhani youza amalawi iyi

  • @lingstonenagoli7729
    @lingstonenagoli7729 Год назад

    Pa woyimba onse mwaganiza za Namadingo why?

  • @user-Nix-jose
    @user-Nix-jose Год назад

    Doc

  • @Eliasiwhite-foreveryoung
    @Eliasiwhite-foreveryoung Год назад +1

    Ayesere ife tizamuvotera

  • @ShadreckLiffa
    @ShadreckLiffa 8 месяцев назад

    Kodi iwe ukudwala mutu waukulu eti, ukuona ngata uprestent ndiopweka

  • @RafickOsama-k2r
    @RafickOsama-k2r 22 дня назад

    Tili naye kaye fredo ntchana

  • @destinekambwiri
    @destinekambwiri Год назад

    Mwakhuta eti,,mungokamba Za Muzik bs, mxieew iweso eti

  • @amabhohlela.3492
    @amabhohlela.3492 Год назад

    Zaziiiiiiii!!!!tu zenizeni!!!kungowononga Data langa

    • @memorymakala6593
      @memorymakala6593 Год назад

      Aaaaa uyu wasuta uyu iyaaaaa😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @HalisonKennedy-wp6cg
    @HalisonKennedy-wp6cg Год назад +1

    Namadingo happey

  • @MadalitsoShuga-no8ix
    @MadalitsoShuga-no8ix 11 месяцев назад

    Ife tikudikila ufumu umene uthetse maufumu osewa posachedwapa zochitika dikilani ndipo anthu amene angazalamulidwe ndi ufumu umenewo sazakhumudwa nawo osati izi mukunenazi ayi mwalephela nose apa

  • @PaulMvuma
    @PaulMvuma 11 месяцев назад

    Uhule ku state house

  • @MarkManyowa
    @MarkManyowa Год назад

    Anzanuwa Ali ndi Chibwana eti??

  • @comfortchinongone
    @comfortchinongone Год назад

    Inu musamakambe bwerera zanuzo,,,aaaaah zandinyasa bwanj

  • @bornface4786
    @bornface4786 Год назад

    Ngati analephera kukhulupirika pa sin ija yofuna ku thandiza odwala koma kuhasula what about anthu oti sakudwala timankonda ngati oyimba osati mtsogoleli

  • @YamikaniChataika-mg7qc
    @YamikaniChataika-mg7qc Год назад

    Kd zimene mukunena apazi wakuwuzan ndani?

  • @mussamapira801
    @mussamapira801 Год назад +1

    Ndalama pena paliponse

  • @victorauwana7258
    @victorauwana7258 Год назад

    Abusa ajaso munawakokomeza motele

  • @maxwellchilima5440
    @maxwellchilima5440 Год назад

    Tizidzangoimba basi, sitingatachite chilichonse

  • @johnmalupia1754
    @johnmalupia1754 Год назад

    Dziko likhoza kuwonongeka namadingo atakhala President chifukwa ndi mbuli

    • @Kassamajibu
      @Kassamajibu Год назад

      Or Ataima mu 2025 akhodza kuwina🎉

  • @BulahaniMashah
    @BulahaniMashah 9 месяцев назад

    wabwalesa nkhani yi pamyana pambuye ako ukut mavusa kaya kutt ndani ngati ukufuna ndama pamsana pako

  • @shushahmuhammad-rx2hu
    @shushahmuhammad-rx2hu 8 месяцев назад

    Mwasowa choyankhula iwe

  • @jermahkell8538
    @jermahkell8538 Год назад

    Tiuzen kaye za peter ndi razalo

  • @MadandoChannel
    @MadandoChannel Год назад

    Kwabwera kale Gaddafi 2025 mwana

  • @Yabwata
    @Yabwata Год назад

    Iwe pala wakhuta nsima gonanga wapulika vazii ukuyooya vambula natchito so vivichi ivi ntheee , asaa

  • @JustineBanda-z9u
    @JustineBanda-z9u Год назад

    Zilibwino kwambili

  • @kennethkaunda3636
    @kennethkaunda3636 Год назад

    Mbudzi iweyo

  • @morriskadzuwa1017
    @morriskadzuwa1017 Год назад

    Wakhuta utaka eti ukusowa khani, wamatama ameneyo

  • @ralphkapanga6404
    @ralphkapanga6404 Год назад

    Nkhani zake😅😅😅😅

  • @gracioussinoya2850
    @gracioussinoya2850 Год назад

    Chibwana ife ai waimva iwe👎👎👎👎👎👎👎👎

  • @yusuffatch4146
    @yusuffatch4146 Год назад

    Wayamba kuonetsa mbali. This may be starting of your downfall. Ena sakonda Namadingo like team Gwamba n team Onesmus. These fans will blindly hate you including some of their fans.
    Za mkutu zakozo ukooo

  • @victorauwana7258
    @victorauwana7258 Год назад

    Bushiri can be ,,,

  • @gracianbinali2272
    @gracianbinali2272 Год назад

    😂😂😂 Mwapopa2 Doc iiiish 😅😅😅

  • @thomasmwitiya1447
    @thomasmwitiya1447 Год назад

    Aaaaah kkkkkkk,,,nde kulilowetsa zibwana dzikolitu mpakana Namadingo???

  • @YekhaBouy
    @YekhaBouy 7 месяцев назад

    Zooonad

  • @amabhohlela.3492
    @amabhohlela.3492 Год назад

    Aaah inunso mpaka Namadingo...ndie azizangotimbatu

  • @mbaliehaward947
    @mbaliehaward947 Год назад

    Tizavota

  • @johnmakanjira339
    @johnmakanjira339 Год назад

    Mumalotanso eti

  • @symonyohane6989
    @symonyohane6989 Год назад

    mmmmmmm

  • @memorymakala6593
    @memorymakala6593 Год назад

    Kodi iwe ndiwakuti aaaa hahaha 😂😂😂😂😂😂😂 ukutinso economis instead of economics kikkkkk ku Malawi tikapuma kumwamba shuwaaa

  • @shadreckmatenje6629
    @shadreckmatenje6629 Год назад

    Ndiwe galu kobasi

  • @MarriamOkwey-bz5bz
    @MarriamOkwey-bz5bz Год назад

    Insha-Allah Namadingo

  • @sayidimisessa
    @sayidimisessa Год назад

    Aaaa zachambabasi

  • @isaacmussa2942
    @isaacmussa2942 Год назад

    Aaaa maloto ako amenewo lweyo

  • @lewisbonongwe8518
    @lewisbonongwe8518 Год назад

    Zazii

  • @jobisjawadu4779
    @jobisjawadu4779 Год назад

    Ndeye kut ziko latha

  • @jameswajumpha6790
    @jameswajumpha6790 Год назад

    Kkkkkkkkk

  • @memorymakala6593
    @memorymakala6593 Год назад

    Aaaaaaaa 😂😂😂😂😂

  • @ZahirZaheer-h3d
    @ZahirZaheer-h3d Год назад

    Haaa kufuna kusokoneza dziko munthu ozikonda ngati Namadingo,iyeyo ali ngati Kamwana kenakake kamatchedwa,Kelly K, what nonsense of this name 😅