Mwa Atupele Muli Utsogoleri - Concerned Citizen

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 8 сен 2024
  • On Nyasa VoiceBox, one concerned citizen says that Atupele Muluzi, has the ability to be a good leader as President of the Republic of Malawi due to his academic qualifications and professional experience.
    Pa Nyasa VoiceBox, mzika ina yokhudzidwa yati Atupele Muluzi, ali ndi kuthekera kokhala mtsogoleri wabwino ngati Purezidenti wa Republic of Malawi chifukwa cha maphunziro ake komanso luso lake.
    #malawi

Комментарии • 41

  • @ClementsKamanga
    @ClementsKamanga Месяц назад +2

    Kod atupele sizingathele abambo anuo ukuthandizen kampen? Inetu ndikuona chomcho madalawo atithandize bwanji

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 Месяц назад

    Atupele is the only hope Malawians have now. This is the reason: He stops practising politics after general elections. This means he will start developing the country after elections. Please, let's try this.

  • @MzondiKaunga
    @MzondiKaunga Месяц назад +1

    Good msg

  • @Lingstone-r3z
    @Lingstone-r3z Месяц назад +1

    Excellent news

  • @EdwardMathuwa
    @EdwardMathuwa Месяц назад +1

    Well saying im with you 100%

  • @user-oc9vl9xz8e
    @user-oc9vl9xz8e Месяц назад

    Atupele muli usogoleli wabwino koma short temper koma ndi oganiza bhoo

  • @cacksygustarf6260
    @cacksygustarf6260 Месяц назад

    Voice 🔥

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h Месяц назад

    ❤❤ that's good idea 💡🎉

  • @edenbelievemseteka5197
    @edenbelievemseteka5197 Месяц назад

    Koma Atupele sizingagwire Guys dziko si la achina Muluzi ndi Achina Muthalikas

  • @user-fl7br3dw4h
    @user-fl7br3dw4h Месяц назад

    Akulu mukuyakhula zoona. Tikufuna anthu anzelu ngati inu. Pitilizani kupeleka upangili ngati uwu mpaka zithu zizasitha

  • @EssaSimon-qw8cl
    @EssaSimon-qw8cl Месяц назад

    Chikangwawa bisy kugwesa ndege ya vice president

  • @WilliamBanda-o5r
    @WilliamBanda-o5r Месяц назад

    Akulu mwanena zoona kwambiri.vuto ndi umbuli kwambiri ku Malawi.

  • @ThomasMaxwell-ks7yi
    @ThomasMaxwell-ks7yi Месяц назад

    Guys tiyeseni atupele pls amalawi

  • @Anafinyambi
    @Anafinyambi Месяц назад

    💯

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of Месяц назад

    Kumeneku ndiye kupusa ngati mmalawi muno zipani zikumatha chifukwa chake ndi choti zimakhala za mabanja basi munthu wazelu uli bze kusapota dpp kapena udf ?

  • @YusufuKaifa-fr4wt
    @YusufuKaifa-fr4wt Месяц назад

    I have 💯 of this speech

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt Месяц назад

    100❤

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Месяц назад

    Good Message Mr

  • @starneckkulemero7548
    @starneckkulemero7548 Месяц назад

    ,,💯zoona

  • @omarajibu860
    @omarajibu860 Месяц назад

    Ndipo zoona

  • @abdulsalammkwepu3321
    @abdulsalammkwepu3321 Месяц назад

    Well said

  • @WhiteRichard-cw2fo
    @WhiteRichard-cw2fo Месяц назад

    Mwayakhula bwino kwambiri amalawi ndi athu onvuta

  • @SildaKatundu
    @SildaKatundu Месяц назад

    MWA bubu mungakhale utsogoleri wanji , maphunziro sinkhani ,za ziiiiiiii

  • @MustapherLino
    @MustapherLino Месяц назад

    Amenewo ndiye mawu braz

  • @ThokohPrescotKalonga
    @ThokohPrescotKalonga Месяц назад

    Kodi apapa iweyo ukukamba zobera Mavoti or chani ? APM 2025 🇲🇼🗳

  • @mzeewandembonyirongo2972
    @mzeewandembonyirongo2972 Месяц назад

    Koma he should have gone ku mbaluku to campaign for his councllor. Koma kuopa kukapereka ndalama pa ground kuumila akuluwa.

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of Месяц назад

    Ine sindingasapote chipani chabanja ai

  • @Littlefair7
    @Littlefair7 Месяц назад

    Koma abale kodi tidzingomva zandale daily? Taonjezatu manyasa, tikukhala ngati timadya ndale tsopano.

  • @user-ky8eq5ek1p
    @user-ky8eq5ek1p Месяц назад

    Zoonadi Brother zikumveka ndithudi.

  • @johnkambala692
    @johnkambala692 Месяц назад

    Not Muluzi family, kusolola awa

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Месяц назад

    Zoona ndithu munthu oti anaphunzira za economics amayendetsa bwino dziko

  • @kennedybanda
    @kennedybanda Месяц назад

    Atcheya ndi wama jokes

  • @HypeGallery-ur9xd
    @HypeGallery-ur9xd Месяц назад

    Ok timuvotela

  • @HusseinAdamLidezo
    @HusseinAdamLidezo Месяц назад

    Nkhan pa ground wakumva wamva

  • @ahmedmsume1489
    @ahmedmsume1489 Месяц назад

    Atupele he can't make it as a leader,he fails at his own constituency as MP in machinga.

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Месяц назад

    Chikangawa kkkkkk

  • @kennedybanda
    @kennedybanda Месяц назад

    Azisiyana ma twins zochitika.

  • @GeorgeMwale-ce8eb
    @GeorgeMwale-ce8eb Месяц назад

    Sober minded man...

  • @HamzaLiya
    @HamzaLiya Месяц назад

    M pretty sure kut Atupele ndiekhao amene angaliphule dziko La Malawi pamoto

  • @edenbelievemseteka5197
    @edenbelievemseteka5197 Месяц назад

    Koma Atupele sizingagwire Guys dziko si la achina Muluzi ndi Achina Muthalikas