Nkhani Ya Commission Of Inquiry Ya Chilima - Comrade Ntanyiwa Pa Limpopo Fm

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 14 дек 2024

Комментарии • 9

  • @PatrickZinenanie
    @PatrickZinenanie 17 часов назад

    The only truth Chilima anachita kupheddwa

  • @Jamilahchinyama-y9b
    @Jamilahchinyama-y9b 47 минут назад

    Koma kungoti achakwera akufuna kuti dziko muno mukhare nkhondo

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 3 часа назад

    Akakhal Chakwera akuyenda okufa ifa uja ndpo imfa ya Chkwera adzafa imfa yowawa omudandaula achuluka dzikol

  • @DonaldJenner-vb1me
    @DonaldJenner-vb1me 5 часов назад

    Zakudima ngakhare atatenga achibare awonse anamwalila simupeza mayanko pati ndizikudima pakhala popanda umboni mbaka karekare zisiyeni kwamulungu ndizi vuta kwambiri musazapangeso kavukuvuku kwena mukuchedwa nazo asaneso kt zipangizo munalibe sonse zinalimo koma Vuto ndizakudima simungapeze umboni weni weni mbaka kale kale tizisiye mumanya mwamulungu basi

  • @PatrickZinenanie
    @PatrickZinenanie 17 часов назад

    Chikangawa anapha chilima koma sakuziwa kuti nayenso azafa

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe 5 часов назад

    A SIR A NTANYIWA CHIFUKWA CHIYANI A CHAKWERA NDI MCP YAO IYI YAO COMMISSION OF INQUIRY AIIKAYI A CHAKWERA. BWANJI AKUTI @ ANTHU ONSE AMAJBULA NGOZI YA chilima ndi 8 ena aja..Aimbidwe mulandu ndi kuti amangidwe.
    Kodi transparency imakanidwa ? A opposition nonse must vomere zimenezi zomanga omwe anajambula ngozi yonse ija.!@ izitu akupànga chifukwa akuppa @ izi ndamva ndikupna lero mmawa muno.pa utube

  • @PatrickZinenanie
    @PatrickZinenanie 17 часов назад

    Commission of inquiry chakwera chikangawa anatenga azibale ake okha nanga bwanji sanatengeko mmodzi wa ku banja kwa chilima???

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 3 часа назад

    Ntanyiwa popangra audio ndi patipo nane ndiikutumule yanga