Lucius Banda ndiwoopondereza i saw it during before the death of Matafale, eve Lulu waponderezedwa kwa nthawi yaitali panopa ndiye kul Nepman kuponenderezedwa heavy.
Kod iweyo martse umamuzonda bwanji wasowa nkhan iweyo ukudana ndi munthu omwalira ukharechete pankhan ya martse tisazakumveso ifeyo ndi okwiya pankhan ya martin nkhata hiyaaa
Kodi umalimbana ndi matse Bwanji? Munthu anamwalira kale kale musiyeni akautse mu mtendele mwamva? Ndisanzamvetso
Ndichifukwa kuli ma buku a History... Anthu akuyenera kuphunzira mbiri za anthu....
@@sammalvitha Zoonad👏
@@shemarionwildwilson1930l
Uchitsiru basi
And that fucken Martse was useless. Sankathanso kuyimba. Imagine Mtumbuka aziyimba Rap zingamveke bwanji?
I love you ❤❤Martin
Lucius Banda ndiwoopondereza i saw it during before the death of Matafale, eve Lulu waponderezedwa kwa nthawi yaitali panopa ndiye kul Nepman kuponenderezedwa heavy.
Iweyo documentary imakugaya ase... umangokamba za anthu omwalira zotinso ulibe information. Mwana opepera
Izi ndi zoona cha mwini ndi cha mwini thanks for your information
Mutu wankhani ndizimene walomgosola apa sizikugwirizana.Ngati kulibe zokamba kwangokhala phee bwanji?
Kod iweyo martse umamuzonda bwanji wasowa nkhan iweyo ukudana ndi munthu omwalira ukharechete pankhan ya martse tisazakumveso ifeyo ndi okwiya pankhan ya martin nkhata hiyaaa
Iwe umakamba nkhani zoti sukuzidziwa
Tell him we still covering them coz we Loved Matafale not his brother 😂😂
Mulungu ndi wankulu
Koma utolankhan umakubvutabe ..explanation imakubvuta
aaaaaa zachamba eti kumakhala mgati mukufuna munene zolongosokatu
Umabwera nkhan zabwino koma ,summarization kukugaya...
Zaziiiii wasowa nkhani eti Let Martse rest well mxieeew
Mutu wa nkhani ndizomwe walongitsora sizigwilirazana
Nde ma blacks ikuwakhudza Pati nkhaniyi???,
Ine sindakukonde iweyo polankhura nkhani ya martse
Respect ❤❤❤❤❤ bro
kungofuna ma views basi! Kupusa aise
Kumalawi mkosauka
Gud
uli boh koma explanation yako ukuzungulira pamodzimodzi
❤❤❤
Komatu Muzifotokomza Zomveka Osamapalapasa
😂
you just wasting our data for nothing😔, palibepo chanzelu chayankhulidwapo
Zaziii