Ndi President uti Yemwe Amalawi Anapindula Naye? (Ntchito Zawo Ziachitile Umboni)

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 13 дек 2024

Комментарии • 72

  • @AgnessMaumbo-b2p
    @AgnessMaumbo-b2p 8 часов назад +2

    Bingu anali Machine opangira machine anzake ❤ Mzimu wawo uzipumulabe mmtendere ngati kuli kotero

  • @EmmanuelGordon-q9s
    @EmmanuelGordon-q9s 8 часов назад +2

    Kwa ine Bingu 80%..Kamuzu 40%..Bakıli 50%..Peter 50%..Joyce.30%..inawa 20%

  • @NdemboBrothersAdam
    @NdemboBrothersAdam 4 часа назад +1

    kamuzu ankaika maina ake pa zitukuko za ena

  • @ManesKamtambo
    @ManesKamtambo 12 часов назад +4

    Peter n bingu

    • @Blessings31
      @Blessings31 5 часов назад

      APM ndikape nkona tinamchotsa mu 2020

  • @josephalfred5138
    @josephalfred5138 11 часов назад +2

    Mtsogoleli wa nzelu ndi Bingu wamuthaluka ndi Peter muthalika chakwela his a wester

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 6 часов назад

    Popanda ufulu palibeso mphindu respect to bakili muluzi ❤❤❤

  • @HaroonMasterchindamba
    @HaroonMasterchindamba Час назад

    For me bingu and Peter Koma bakili pa ufulu respect

  • @mkajikosya-uq5hs
    @mkajikosya-uq5hs 3 часа назад

    Mpakana lero HE Dr Joyce Banda akugwirabe ntchito zachifundo

  • @dianachabs
    @dianachabs 3 часа назад

    JB ndi machine 🔥 makina the only president that can change Malawi 🇲🇼

  • @GrantArnold-j9h
    @GrantArnold-j9h 3 часа назад

    Kwa Inenso Kamuzu80% Bakilimuzi 90% Bingu 95% Joyce Banda 75% Peter Muthalika 90.5% Chakwera 35%

  • @Staphelsavimbindhlovu
    @Staphelsavimbindhlovu Час назад

    Bingu❤❤❤

  • @msatisi.reangfordphiri
    @msatisi.reangfordphiri Час назад

    Aaaaa iwe Sam watani kodi, Kamuzu stadium siinamangidwe ndi Kamuzu. Koma inasinthidwa dzina ndi Kamuzu in 1964. I was maintained by him in 1968.

  • @chanceykalimah1965
    @chanceykalimah1965 Час назад

    I can’t think of any other than Dr Joyce Banda. When bingu died and before he died this country was collapsing before our very on eyes but Joyce Banda changed all that , talk of fuel, electricity and availability of forex JB was behind all that.

  • @Blessings31
    @Blessings31 5 часов назад +1

    Bingu Stadium inayamba kumangidwa mu 2013 ndipo ndi ya JB

    • @mwale86
      @mwale86 Час назад

      Ndipo true story

  • @vitujames53
    @vitujames53 4 часа назад

    Anayesesa mzimayi asafe akubeleka ameneyu ndiye msamaliya wachifundo HE Dr Joyce Banda

  • @vitujames53
    @vitujames53 4 часа назад

    President yekhayo yemwe samagona anthu akamagona ndi njala..Mama JB

  • @mwale86
    @mwale86 Час назад

    Kwa ine nde HE Dr Joyce Banda president woti analowa dziko lilipamavuto koma in 100 days anabwezeletsa kalikose mchimake masten ndimachine

  • @mkajikosya-uq5hs
    @mkajikosya-uq5hs 3 часа назад

    JB anasintha zinthu kwa masiku 100 okha komanso Kabaza yense tikumuona leroyu ndi Dr Joyce Banda anayambitsa

  • @JamesMaidaBanda
    @JamesMaidaBanda 18 часов назад +3

    Bingu

  • @e.r.mchanel1460
    @e.r.mchanel1460 5 часов назад

    Bingu adali amuna osati awowoawo

  • @vitujames53
    @vitujames53 4 часа назад

    Mama JB mtima wothandiza anthu amamidzi

  • @ThoccoChimbali-h6g
    @ThoccoChimbali-h6g 5 часов назад

    Chakwela nde mbuzi yeni yeni

  • @ThannabMtendere
    @ThannabMtendere 18 часов назад

    Yemwe anabwelesa ufulu kuti asogoleli osewa athe kuyendesabwino zikoli zopanda wufuluwo sitikanawaziwa wosewa❤

  • @salafinamhone-rd1ku
    @salafinamhone-rd1ku 9 часов назад

    Kamuzu and chakwera did nothing rather than greedy, they only change names zitukuko za amzao

  • @Blessings31
    @Blessings31 5 часов назад

    Mayi Banda analowa m'boma kuli mavuto phwii ku Malawi koma zonsezo anathana nazo in 100 days

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 5 часов назад

    Mphindu la Bingu linali kuba boma la UDF kupitisa Ku DPP

  • @FrancisStima-sc7zs
    @FrancisStima-sc7zs 18 часов назад +1

    Kamudzu Banda ndifiti kamudzu amangositha zithu maina kumaika mudzinalake

  • @akhtarmunaf7121
    @akhtarmunaf7121 6 часов назад

    Koma bingu anari akatundu

  • @YahyaUmari-t5t
    @YahyaUmari-t5t 17 часов назад +1

    Bakili muluzi ndiyemwe anatitsegula maso guys tisaname amalawi tinali anthu opusa kwambiri padziko lonse lapansi ngakhale iweyo amene ukulankhulawe ufulu umenewo anabweletsa ndi Muluzi, ufulu wama Radio station TV, cell phone tadzidziwa chifukwa chamuluzi kumachenjela patown 😂

    • @BubaMkolola
      @BubaMkolola 17 часов назад

      Izi ndiye zoona zake koma a malawi nsanje yomwe imavutapo guyz

    • @AlihIbrahim-s7v
      @AlihIbrahim-s7v 9 часов назад

      ​@@BubaMkololaonyoza Bakili muluzi ndimbuli,,,,75% educated in Malawi from 45% munthawi ya Kamuzu,,,,magetsi tinawadziwa m'malawi kumadela athu kamba ka Muluzi,,,ma school palipose zipatala,,,free primary Education,,ma CDSS palipose,,analimbana ndi m'ngango m'thakati yemwe amalawi ochuluka analuza miyoyo yawo ena kuzuzidwa,,,Muluzi number 1

  • @vitujames53
    @vitujames53 4 часа назад

    JB mtsogoleri wachikondi

  • @mastonmacford-l7k
    @mastonmacford-l7k 8 часов назад

    kamuzu is my hill malile pa apetet koma chakwela aaa ay anaononga chuma chomwe osewa anachipanga kuphana katangale kukondela anthu amtundu wawo kusavela zika zawo kumana chitukuko mboma maboma

  • @AlihIbrahim-s7v
    @AlihIbrahim-s7v 8 часов назад

    Palibe zochitaso kufusa apa,,,kumanena chilungamo,,,vuto ana ama 2000 sitikudziwa kalikose kuti anthu amakhala m'moyo wotani nthawi ya Kamuzu,,,,Kamuzu mwina akankhala kuti anali m'malawi dzikolino palipose pakanakhala polozeka,,,koma kamuzu analisiya dziko lino lilitchile kumamidzi kulibe magetsi,,anthu amaletsedwa kumanga manyumba owoneka bwino,,,anthu amayika mu umbuli kuti azibabwino chuma chamalawi mkumakabisa kunja,,,
    Anasintha mayina zinthu zomwe adazipeza mkumaziyika mudzina lake useless President,,adamanga Blantere ma Building koma personal not opindulila amalawi,,,Chayamba House ndima Building ake,,,komaso simazapezeka President kumalawi emwe anaba komaso olemela kuposa kamuzu,,,,3 Trillions ku Baclys Bank komaso ma Back osiyana siyana ndalama zokabisa,,anthu amanyongedwa kamba ka chikutilo cha Animal Farm,,,
    Odzudzula katangale m'boma amakhala kuti wasayinilatu zamoyo wake,,,
    Zidakomela ena olimba mtima kumugwetsa kuti amalawi amudziwe Jackie Chani😂😂😂wina mkumanyoza muluzi muzifusa kwa azigogo anu azikuwuzani
    Enanu makolo anu or a sayidziwa sadapiteko ku school pomwe inu ana anu akumphuzila primary yawulele mukunyoza Muluzi umbuli,,,Of course dziko la Malawi mavuto akadalipo,,,koma palibe akadasintha dziko la malawi kuposa KAMUZU chifukwa analiyekha nthawi yake,,,koma dyela,,,kuba nkhaza ndizomwe zidakula basi,,,

  • @mkajikosya-uq5hs
    @mkajikosya-uq5hs 3 часа назад

    JB anamangira nyumba anthu osauka

  • @noahkalima5294
    @noahkalima5294 14 часов назад +1

    Kamuzu banda sanapangepo kalikose,,chitukuko mumachiona chija nd chasamunda,,

  • @SteveKanongwa
    @SteveKanongwa 9 часов назад

    Guys musanditukwane chonde ine ndasankha chakwera mokakamizidwa

  • @FladielMwase
    @FladielMwase 18 часов назад +1

    Bingu wamuthalika

  • @esthermalixani2244
    @esthermalixani2244 2 часа назад

    Bakili muluzi

  • @CatherineFly
    @CatherineFly 9 часов назад

    Bakili muludzi

  • @CharlesLuciano-i1k
    @CharlesLuciano-i1k 9 часов назад

    Iweso History sumaiziwa kamuzu stadium ndi yasamunda ukapitiliza zakozo uzalandila unfollow

  • @NdugeGamah
    @NdugeGamah 2 часа назад

    Bingu anal wa look shap zimu wake use mumtendele osatha

  • @MathewsMynus-v9u
    @MathewsMynus-v9u 18 часов назад

    Anatipindulira osewa kupatula chakwera palibepo

  • @GhettoWalliAddi
    @GhettoWalliAddi 8 часов назад

    Mai Joyce Banda hule lokuba ndani angaiwale cashgate maiwa ndiachisilu awa mosogozana NDI awa achakwela,chakwela ndee ndi bundichi galu wachabe chabe

    • @Blessings31
      @Blessings31 5 часов назад

      Iwe ndwe galu kwambiri.JB ndiyemwe anapangitsa amalawi kuzindira kuti anthu amaba ndalama m'boma ndipo Cashgate inayamba ndi DPP and Bingu..Sitinaiwale Bingu wamtharika amatuluka m'boma ndi 61 billion ku account mpaka account kupangidwa Freeze..sikuba kumeneko..Ndeno tandiuzeni pomwe khothi linagamulapo kut JB amupatse chilango chifukwa Cha Cashgate?

    • @MalickMkweche
      @MalickMkweche 4 часа назад

      Komatu binguyo zinthu zimayenda bwino fetereza mbwembwe chokudya mbwembwe kaya anaba tinalibe nazo ntchito

    • @vitujames53
      @vitujames53 4 часа назад

      Kuyankh kopusatu uju zoti kukubedwa ndalama munaziwa chifukwa cha ndani??? Yemweyo JB ndiyemwe anadziwitsa mtundu wa a Malawi kuti ndalama.zikubedwq

  • @MateusJacob-h6t
    @MateusJacob-h6t 8 часов назад

    Pá osewe pita ndigalu😂😂😂😂

    • @Blessings31
      @Blessings31 5 часов назад

      Ndipo ndigalu kwambiri

  • @BashielSalade
    @BashielSalade 18 часов назад

    Ay ndi mphanso ya mulungu

  • @REXCHARLESKAJAWO
    @REXCHARLESKAJAWO 16 часов назад

    Bingu ndiye munthu

  • @MdokaJames
    @MdokaJames 11 часов назад

    Bakili Muluzi ndamene anachita bwino kwambiri

  • @PraiseWisdomson
    @PraiseWisdomson 18 часов назад

    Zaka zikutchulidwazo nzabodza

  • @IqrahOmar-x6w
    @IqrahOmar-x6w 10 часов назад

    Bakili muluzi ufulu

  • @TobbiePahuwa
    @TobbiePahuwa 14 часов назад

    Chikangawa mfiti ya bodza

  • @GodfreyKampezeni
    @GodfreyKampezeni 10 часов назад

    Chakwera kkkk😢

    • @SteveKanongwa
      @SteveKanongwa 9 часов назад

      Nde ukuseka chani 🙌😂😂😂

  • @EstherchavulankhomaNkhoma
    @EstherchavulankhomaNkhoma 12 часов назад

    Bigu wsmuthalika

  • @MaggieKampingo-v1b
    @MaggieKampingo-v1b 3 часа назад

    KB

  • @JamesMaidaBanda
    @JamesMaidaBanda 18 часов назад

    Ngwazi

  • @IsaacBwanali-m8c
    @IsaacBwanali-m8c 18 часов назад

    Kamuzu Banda'

  • @LeoChimaliro
    @LeoChimaliro 10 часов назад

    Bingu

  • @Sherrie-b5s
    @Sherrie-b5s 9 часов назад

    Kamuzu Banda

  • @BeatrinceChanza
    @BeatrinceChanza 2 часа назад

    Bingu