*Wife Material Lyrics by Phyzix & Pon G* *(INTRO: Phyzix)* Kukakhala kunjaku kwacha bho... yeah/ yeah Kukakhala kunjaku kwacha bho/ zachita kudzadzamo bobobo/ Wifey material/ terial/ terial/ Wifey ma ti ti ti ti *(VERSE 1: Phyzix)* Ndinapeza chibhebhi anthu adziwe/ sindimachibisa sichapadziwe/ yemwe zikumuwawa adhiwe/ koma ichichi ndi changa chi Lindiwe/ sichingazakupatse mphindi iwe chimakhala chili ndi ine uzimva iwe/ vuto lake iweyo kuzimva iwe umangogwira akazi openga ma byzwe/ Za ife ndi zokoma zothila curry/ sitimvetsana kuwawa tsabola wa kale/ Uyuyu ndi wanga si temporary/ ndikanena kuti ndimugaya si mphale/ kutentha ngati Nali samalani abale/ akusungila sugar wonyambititsa mbale/ Mkazi uyu ngoiwalitsa abale/ amakomedwetsa ngati anthu a Ndale/ Very Good Very Good *(HOOK: Pon G & Phyzix)* Mami ndinu chi Mkazi chooneka bho Mumachita kukhala ngati a M'video Mami muli pure ngati ka viligo/ mukazafuna banja ife tilipo Ndinu wifey material terial terial Wifey ma ti ti ti ti Wifey material terial terial Wifey ti ti ti ti *(VERSE 2: Phyzix)* Ichi ndi chi ndiwo koma si mpiru/ sindinachite kuchiba koma ndi chi dhilu/ ichi ndi chibhebhi chodzadza feel/ dzina lake ndinaliyika kale pa will/ chimandikumbutsa Maggie Mwaupighu/ mahope anga a ku Primary ku Mphungu/ tili mafana oyankhula chizungu/ she had a chocolate skin ndimamufila khungu Chibhebhi changachi chandipatsa khungu/ ndikayenda m'townimu sindiona buthu/ Ndadwala Chikondi 10 pa 10/ chachita kundifika pe mpeni/ Ndavomera Mami ndi malizeni/ sindipempha kuti Ambuye ndichilitseni Izi si za gulu si za m'memo/ Ineyo ndili momo m'menemo/ Very Good Very Good *(HOOK: Pon G & Phyzix)* Mami ndinu chi Mkazi chooneka bho Mumachita kukhala ngati a M'video Mami muli pure ngati ka viligo/ mukazafuna banja ife tilipo Ndinu wifey material terial terial Wifey ma ti ti ti ti Wifey material terial terial Wifey ti ti ti ti *(BRIDGE: Pon G & Phyzix)* Gal you di wife material/ I just wanna make you my wife ooh Gal you di one in a million/ this feeling for you I can't deny ooh Iwe ndiwe Mkazi wooneka bho/ wooneka bho/ wooneka bho Iwe ndiwe chi Mkazi chooneka/ chooneka bho/ chooneka bho Iwe ndi Mkazi wofitha bho/ wofitha bho/ wofitha bho Iwe ndi chi Mkazi chofitha bho/ chofitha bho/ chofitha bho *(HOOK: Pon G & Phyzix)* Mami ndinu chi Mkazi chooneka bho Mumachita kukhala ngati a M'video Mami muli pure ngati ka viligo/ mukazafuna banja ife tilipo Ndinu wifey material terial terial Wifey ma ti ti ti ti Wifey material terial terial Wifey ti ti ti ti
Powerful songs guys. Physics and Pon G you are great musicians in Malawi for sure. I can challenge you guys,if you can produce 100 tracks just Physics ft Pon G all of them should be top notch songs for sure!!
*Wife Material Lyrics by Phyzix & Pon G*
*(INTRO: Phyzix)*
Kukakhala kunjaku kwacha bho... yeah/ yeah
Kukakhala kunjaku kwacha bho/ zachita kudzadzamo bobobo/ Wifey material/ terial/ terial/ Wifey ma ti ti ti ti
*(VERSE 1: Phyzix)*
Ndinapeza chibhebhi anthu adziwe/ sindimachibisa sichapadziwe/ yemwe zikumuwawa adhiwe/ koma ichichi ndi changa chi Lindiwe/ sichingazakupatse mphindi iwe chimakhala chili ndi ine uzimva iwe/ vuto lake iweyo kuzimva iwe umangogwira akazi openga ma byzwe/ Za ife ndi zokoma zothila curry/ sitimvetsana kuwawa tsabola wa kale/ Uyuyu ndi wanga si temporary/ ndikanena kuti ndimugaya si mphale/ kutentha ngati Nali samalani abale/ akusungila sugar wonyambititsa mbale/ Mkazi uyu ngoiwalitsa abale/ amakomedwetsa ngati anthu a Ndale/ Very Good Very Good
*(HOOK: Pon G & Phyzix)*
Mami ndinu chi Mkazi chooneka bho
Mumachita kukhala ngati a M'video
Mami muli pure ngati ka viligo/ mukazafuna banja ife tilipo
Ndinu wifey material terial terial
Wifey ma ti ti ti ti
Wifey material terial terial
Wifey ti ti ti ti
*(VERSE 2: Phyzix)*
Ichi ndi chi ndiwo koma si mpiru/ sindinachite kuchiba koma ndi chi dhilu/ ichi ndi chibhebhi chodzadza feel/ dzina lake ndinaliyika kale pa will/ chimandikumbutsa Maggie Mwaupighu/ mahope anga a ku Primary ku Mphungu/ tili mafana oyankhula chizungu/ she had a chocolate skin ndimamufila khungu
Chibhebhi changachi chandipatsa khungu/ ndikayenda m'townimu sindiona buthu/ Ndadwala Chikondi 10 pa 10/ chachita kundifika pe mpeni/ Ndavomera Mami ndi malizeni/ sindipempha kuti Ambuye ndichilitseni
Izi si za gulu si za m'memo/ Ineyo ndili momo m'menemo/ Very Good Very Good
*(HOOK: Pon G & Phyzix)*
Mami ndinu chi Mkazi chooneka bho
Mumachita kukhala ngati a M'video
Mami muli pure ngati ka viligo/ mukazafuna banja ife tilipo
Ndinu wifey material terial terial
Wifey ma ti ti ti ti
Wifey material terial terial
Wifey ti ti ti ti
*(BRIDGE: Pon G & Phyzix)*
Gal you di wife material/ I just wanna make you my wife ooh
Gal you di one in a million/ this feeling for you I can't deny ooh
Iwe ndiwe Mkazi wooneka bho/ wooneka bho/ wooneka bho
Iwe ndiwe chi Mkazi chooneka/ chooneka bho/ chooneka bho
Iwe ndi Mkazi wofitha bho/ wofitha bho/ wofitha bho
Iwe ndi chi Mkazi chofitha bho/ chofitha bho/ chofitha bho
*(HOOK: Pon G & Phyzix)*
Mami ndinu chi Mkazi chooneka bho
Mumachita kukhala ngati a M'video
Mami muli pure ngati ka viligo/ mukazafuna banja ife tilipo
Ndinu wifey material terial terial
Wifey ma ti ti ti ti
Wifey material terial terial
Wifey ti ti ti ti
terial mbambande
Very good very good
On repeat, very good very good 👍
Muli super
Umatha inuyo
My daughter is Lindiwe so every time she's sad I say to her ICHICHI NDICHANGA CHI LINDIWE!! Her smile is always priceless. ❤is
Say hie to her😢
@@EmmanuelMtendere I will,thanks.
@@magdalinemafunase2440 she has a phone
@@magdalinemafunase2440she has a phone
@@magdalinemafunase2440she has a phone
Achimwene this is nice. From your neighbour Zambia🇿🇲
On repeat all day.. 🇿🇲🇿🇲
One of the dopest tracks so far, receive your flowers Gamba
Nyimbo ili fine heavy!!!!!!!!!!!!!
Phyzix umwa chani wandikozera tsiku langa💥💥💥💥💥💪💪💪💪
I can play this song more than five times per day
The fuse of old xool element into an afro beat gt me goose bumps, 25B Kanthepa yaimika manja Lol
We appreciate you 😊
This song never gets old ❤❤
You are and you will always be my best Rapper in Malawi,,keep fire burning
Mukazafuna banja Ife tilipo ❤❤❤❤❤😂❤❤
Love this song VERY GOOD VERY GOOD 👍🏽
❤️❤️❤️🔥🔥🔥🙏🏽🙏🏽🙏🏽
Homie nyimboyi ili bhooo 👍✌
Koma wife material ndi🔥🔥even the hook 🔥
Koma Pon G..everything you touch turns Gold.
Phyzo ndi bwana Mesa.
This is big tune MAN.
🇿🇲 loves it keep it up 🇲🇼 👆 the world
Too much moto🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Phyzix is one of the lyricist, vocabulary physicist.
My motivation speaker physics
💥💥💥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 gamba sukhumudwisa very good very good
Mmmmm madhala phyzo this is great tune👌👌🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥✊✊💪💪💪💪💪💪
Wakhiya fresh kabisa
My favorite 😍
More fire umatha inuyo guys
Hoookeed 🔥🔥🔥🔥🔥😍😍😍
Lovely Video,Lovely song too. From Zambia keep it up Neighbor
Mmm in this song nali has been added 🔥🔥🔥🔥
man phyzix za ana oziwa iziz
Wife material yili boh heavy
Phyzix 🔥🔥🔥
Love this 🇿🇲🇿🇲🇿🇲
More 🔥 🔥 🔥 big man
Mwayitha man this is what we want in our generation keep it up
Inuyo mumatha man phyzo 🔥🔥🔥🔥
What a beauty
Umatha iyse
Let's chill here❤wife matititi🌻
Si Mphale big up captain bae
Love from Ghana
Track yanyatwa heavy
Ili bo, on repeat!
Big up phyzo……keep repping the ghetto and inspiring many!
On repeat 🎧🔥🔥🎶
Taking our beloved malawi on another levels physics iweyo umatha we are waiting for international colab
Legendary
Beautiful
Gamba saphwekesa
Big up 🔥🔥🔥director skript also nailed it
Gamba❤
So catchy! Love it!
Very good very good,🤑🔥🔥umantha iwe
Gamba wa sweet
Ili Best
Great song!
Wife material nyimbo ya bho 💚🔥
♥️
Kachimalawi ,,,,,live from cape town
The moment i heard about you guys this January 2024 aaa sidafune tsiku lipite nsalowe your u tube ❤
Role model 🔥🔥🔥🔥🔥
WE HERE!
Nyimbo ina iliyonse ya phyzix imakhala fire 🔥
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥wife ti ti ti!
This song is another level
Very good very good🎉🎉🎉
This is a masterpiece bro, keep up the good
Big up phyzo🙌🏾✨✨
Chi heat🔥
phyzix word play game on 100
You're the best, PHYZIX,, IOE
Wife material I love this song 🎵 😍 big up Phyzix mbambande!
♥️👠👑
Very good Very good , Big up Pon G nice hook
Ilibhoo hvy
Beautiful piece
Wife Material 🔥💯💯
The song is 🔥🔥🔥
Phizix u always sing like Ur not from malawi❤❤much love
Thank you 😊
U have nailed it Phyzix
(Wife material in my mind)
Physics fire
🔥🔥🔥🔥🔥 this is what we call good music ☺️☺️☺️
🇮🇲
Respect 💯..ili welo heavy 🙌🤝
Nyimbo mwapha iyi
Yoo🔥
🔥🔥🔥💯
Quality video - Phyzo
this is a masterpiece man Phyzo🥰🥰
Good music 🔥
🔥🔥🔥
Big up from France.
Dope
Wifey ma ti ti ti ti❤️🔥🔥🔥
Powerful songs guys. Physics and Pon G you are great musicians in Malawi for sure. I can challenge you guys,if you can produce 100 tracks just Physics ft Pon G all of them should be top notch songs for sure!!
Very true...
Very good very good
Thumb up 🤙 Gamba
Ngini yabho
Wakwapula ♨️♨️♨️♨️♨️♨️
Hahahha vele gudu vele gudu... love it
🔥🔥🔥🔥
Captain Bae very good very good.
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Respect
From zambia enjoyin
Phyzo you are a legend 🔥
Respect 🕴️ boss