Ndibwino mukafuna kumakhala ngati mtolankhani muzidzitsata zinthu. This lady si MP koma ndi director of women wa DPP ko southern region Mai Ndadowa wa ku Thyolo.
Ndipo ndindani iyeyu kuti akalembele anzake malire? Angaope kubwera kumeneko ndi ndani? Tizikapita ku America Nde tiope m'dziko mwathu kuopa 🙆🤣😂🤣😂🤣😂🙌.... Nde inunso titi simubwera ku central ndi northern region? Mwaphya mtimatu kwambiri ndi zitukuko, mufadi ndi ma BP simunati, mfundo kutukwana, kusinjilira ndi kunyoza mtsogoleri wa dziko, koma muli ndi tsoka amai inu
@@Hassanianusa-go9wvchitsilu cha munthu ukafuse chakwera chikangawa wakoyo zomwe adad anapanga,,,,,,dziko lagwirizana kale ayeee ndi Peter ekhayo akulowa boma Chaka chamawa❤❤
Powerful speech from a courageous woman, I like her courageousness ❤❤❤
Kodi ndimayi ndani ameneyu kkk koma ndiolimba mtima
Mcp kumalawi yalakwitsa zinthu zambiri DPP welcome back
Wosaopa wosafoka wosatopa keep on moving 💪💪💪🔥🔥🔥
😂😂😂😂😂😂,kukoonza!
Zoonadi tidzabwererenso mu mdima.
My sister tiye nayo yomweyo Dpp woyeeeeee waboma❤❤❤❤2025
Ndimadikira kuti ndimve ko mfundo yogwra mtima ya chitukuko. Koma ndakhumudwa nkhani apa wakula ndi mkwiyo ndi sanje.
Cakwera ali mmadzi wasakadza dziko waononga 2025 apeter mutharika ali konzenso dziko
Ndipo kwambiri
Tsono ufuna kuzavula tonse tizabwera kudzaona uchisiru wa dpp viva mcp
Kasambe kuko ndi mcp yakoyo
Mziti chikangawa kt aziwe mwachangu😂😂
HaHaHaHaHaHaHaHaHaHaHa Mpaka Muzayenda Buno Bwamuswe?? Ayi Am Here Patiently Waiting.....
Kkkkkkkkkk 😂😂😂😂😂
Ndibwino mukafuna kumakhala ngati mtolankhani muzidzitsata zinthu.
This lady si MP koma ndi director of women wa DPP ko southern region Mai Ndadowa wa ku Thyolo.
Koma mayiyu a Dpp munamupeza kuti amaposa amuna poyankhula .chikangawa samamuopanso ayi
Ndpo ine ndye amandsangalatsa bwanj ❤❤
Dzowonadi Lazaro akudyetsa anthu chitedze Shane on running government
😂😂😂😂 More fireeeeeee mama auzeni zoona ❤❤❤2025 dpp woyeeeee
Ife tigwilitsa tchito njira inailiyonse koma tikuchotsa lazaro masikin8
Wayenda kale ameneyo
Mama mumatha muma kwana❤
Maliseke adzaonetsewo ndi wake ndipo adzachite manyazi ndi iyeyo,amuna ake,ana ake komanso bambo ake ndi mai ake adzamva chisoni.Ambiri tidzangoona kuzerezeka.
Kumpingo ayambiretu kuchita khansel komanso chonde ma prophet thamangani kukatulutsa chiwanda ichi chovulavula.Komanso mumulandiritse YESU KHRISTU.
Nde akazavula chitazachitike nchani kaya?.
Mwina maliseche akewo amaphulika kuti azapha anthu kapena, koma nditukwana kwinako
Kkkkk zidakanika Ena kuyenda chovula ku Blantyre
Zo wona a Malawi as zaone mtendetele❤❤❤
Zingondikhuza kuti athu Ena Malo mokhoza zithu kuti mcp ichoke upitanso kuka joiner shame😢
Azimayi oterewa atakhalapo 10 zongabebesotu
Chipani cha Lomwe komanso mukuchedwa
Akabweraso muwalase ndi legeni
Ndale zopusa zimenezo, azimai ndi anthu aulemu osayenera kumalengeza kumsonkhano kuti muzavula muzayenda maliseche ufiti chani? Mukatelo mwanena mfundo?
MCP sipanga nawo za tippex, ngati kuli mbala zobela mavoti ndinu. Pakamwa panupo olo manyazi kukamba zolaulazo aaaaah ndakaika inu simzimai mwangovala dress . Kuphya mtima kumeneko muchimwa nako
More 🔥 DPP
2025 tiyambe kupha malobino welcome back my party 🥳
Azamuwonera anthu ulere akazavula zake izo
Anthu akufuna mutalika ifine anthu tilikujon tonse tikufuna DPP mulungu anamuika chakwela phapando affine azafune mulungu amuchoza DPP iwina tikufuna kugula zithu mochipa
👍👍👍👍👍👍✊✊✊✊✊✊
Mayi ndinu katundu kudosssiiiihhhh
DPP oyeeeee
More fire
Ndebwino tizakuwonele kumatako
Dpp boma 2025 chakwela wanditopetsa
Kumene kufuna DPP kufuna kudzalamuliranso, mpaka kudzavula? Koma ya
Amayi mulimbikitsa ziwawa malankhulidwe awawa siyani muzingonena zomwe mudzachite osati kuno tatseka mkwa pitala Malawi mngwatonse uyu .
Ndipo ndindani iyeyu kuti akalembele anzake malire? Angaope kubwera kumeneko ndi ndani? Tizikapita ku America Nde tiope m'dziko mwathu kuopa 🙆🤣😂🤣😂🤣😂🙌.... Nde inunso titi simubwera ku central ndi northern region? Mwaphya mtimatu kwambiri ndi zitukuko, mufadi ndi ma BP simunati, mfundo kutukwana, kusinjilira ndi kunyoza mtsogoleri wa dziko, koma muli ndi tsoka amai inu
Ife pheee kudikira kudzaona malisechee
Mayi olimba mtima osafooka osawopa osatopa tili pamboyo pano
Dpp inathadi
More fire 🔥
iiii ndipo anthu awa afika poyankhulisana pambali mwamva kkkkk
Campaigning for a 85 years person that's total useless thinking 😂😂
Total useless indeed
Chikangawa
Imirani inuyotu tikuoneni bakha weni weni kadyeni chitedzecho uko chitsilu chamunthu
Ndie tidzaonatu elukuluku😂
Yankhulani mayi
Awunzeni aziwiletu Dpp ikubwera
Asazayeseredi kuba popeza ndimbava zazikulutu ofunika kutongola maso
Dzavuleni mai ndi ufulu wanu
Chipani chikutha uku anthu akuthawa ,anthu akupita ku mcp uku
DPP singathe ndipo ilipo ovotera DPP ndife tili kumudzi musapusisike MCP DPP iri ndiwathu ngati nyerere ena sitionekera ndipo MCP kunama.
Akugulidwa awo
Hahaha zoti chikangawa akugula anthu ofoila sukudziwa
Koma azimayi ena inu eeee
Anthu amasapota zopusa and ku dpp kulibe munthu amene amalankhula zanzeru. Munthu ungamayankhule zogawanitsa mtundu?? Munthu yi ali mbuuuu kutuwa nkumalankhula zinthu zopanda nzeru? Nanga adakakhala wowonekako bwino zidakakhala bwanji ndipo zooti ali pabanja ndakaika and sangakhalenso ndimwamuna. Mumuuze ndale zonyozana zinatha kale anthu akufuna mfundo pano
Anthu oyankhula zofoila mulipo ambilitu
Mbolo yako osadulayo yoloza pansiyo osadzimvera chisoni bwanji imirani inuyotu tikuoneni bakha weni weni kadyeni chitedzecho uko
inu anyau usawumbala mboliyanu muziwaso
Chaka chamawa nkutali please
Auze
Mmmmmm sono mukudikira kuti mudzaberedwe aaaaa zofoila
Kk😢😅
Amayi maso kusongolo asabere ma vuto achakwela
Malo motenga action pano mukufuna muwapatse mpata obera
Mpite kumpoto mukapulikiske chitumbuka
Kuyakhula kwa bwanji uku azimai amayakhula mopoira .
Yes mau ameneo
Adpp ndi achisilu munali mboma mwachitapo chani zisilu inu
@@JoziMaulanachisilu ndi iweyo chikangawa wapanga chani kupha ndi kuba wopusa iwe eti
galu iwe@@JoziMaulana
@@Hassanianusa-go9wvchitsilu cha munthu ukafuse chakwera chikangawa wakoyo zomwe adad anapanga,,,,,,dziko lagwirizana kale ayeee ndi Peter ekhayo akulowa boma Chaka chamawa❤❤
Kkkkkk muvulatu chama chino
Za uhule basi palibeso fundo apa
Nkazi kopanda NZERU uyu
Kuyankhula kofoila uku, ifenso sitikuikira kumbuyo ulamulirowu koma kayankhulidwe aka nkosayenera