Ngati a Mec sakumva madandaulo awanthu amene akuwagwirira ntchito nde kuti sakufuna zamtendere let them do what they are doing chifukwa akudziwa chomwe akupanga.
Kodi ana a under age akulembetsawa is it not criminal? Is this not a move to rig ma vote by either opposition or ruling party? Is this not lawlessness?
ineyo ana acc anga kumzuzu anapita anaretsa ana ambiri seven anyamata cha kumzgora anabweza anyamata azaka email 20 ena 19 ineyo umboni ndiri nawo akuti pita uko zadutsa zimenezo chigawa cha nkhata bay anthu ambiri anawabwetsa nkhani yake tisabise anthu ambiri aribe ma id
Osalola zokamba za MEC,zonsezija zamaboza let's be strong pomenyankhondo yolesa mashine aja.ndipo pali results ya mcp kuti yawina ndi pamashine ,so be careful at that issue.
Akatundu bambo congratulations times 11
Keep it up Times. I appreciate your good work
I always talk about that machine
Congratulations times pitilizani kutipasira. Ma program abwino ndi TV yokhayo yomwe sibisa nkhani
Congratulations times 11years mukutumikira amalawi pitilizani
Happy anniversary times radio
Congratulations times tv and radio
Sima ya mamawa yalakwisaso nkhani Lero
Komaso ID simapanga expire mwini wake alimoyo
Tim's private radio not zbs under the mcp
apapatu palibe chobisa kalembela ayambileso
Ngati a Mec sakumva madandaulo awanthu amene akuwagwirira ntchito nde kuti sakufuna zamtendere let them do what they are doing chifukwa akudziwa chomwe akupanga.
yes
Muchita chani ngati MEC sisintha zomwe anthu akuwauza?komatu pamene palinkhani ndi pamashine ya asimartike.muone anthu aja sakulola kuti mashine asagwile ntchito ndekuti masamu yobela yonse anakazika kale,so kofunika kuti a malawi avale zilimbe potsutsana ndi chiganizo chogwilisa ncito mashine .zikatelo ndekuti a mec agwanayo yobela.
Kodi ana a under age akulembetsawa is it not criminal?
Is this not a move to rig ma vote by either opposition or ruling party?
Is this not lawlessness?
zowona sakuvera madando anthu ndiziwona achimwe chifukwa kunkhata bay anthu ndiambiri anawaretsa kuma id kurembetsa
ineyo ana acc anga kumzuzu anapita anaretsa ana ambiri seven anyamata cha kumzgora anabweza anyamata azaka email 20 ena 19 ineyo umboni ndiri nawo akuti pita uko zadutsa zimenezo chigawa cha nkhata bay anthu ambiri anawabwetsa nkhani yake tisabise anthu ambiri aribe ma id
Nphangala zikulu zikulu
Osalola zokamba za MEC,zonsezija zamaboza let's be strong pomenyankhondo yolesa mashine aja.ndipo pali results ya mcp kuti yawina ndi pamashine ,so be careful at that issue.