THE BACKGROUND

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 24 окт 2024

Комментарии • 82

  • @GodrineGerman
    @GodrineGerman 3 дня назад +13

    Komabe pena sakunama 😂😂😂 basi koma poti wa nzeru ndi amene ali ndi ndalama

  • @peacenamadzunda509
    @peacenamadzunda509 2 дня назад +5

    As long as akupanga inspire anthu and sakutukwana munthu let her enjoy what she has on her table now ......enafetu tilibe chabe ndalamazo ....komaso let her do what her heart wants ..... Amalawi maluzo ndikugwa kwakwacha plus njala ndidzuwa zikusokoneza koma

  • @RhodaGondwe-rw8uz
    @RhodaGondwe-rw8uz 2 дня назад +3

    I have heard alot of people saying what 10th May has said......finally someone has said it

  • @RahamanVenka
    @RahamanVenka 3 дня назад +8

    Ndli mbali ya 10may

  • @kettiempate7131
    @kettiempate7131 3 дня назад +7

    The guy is right,

  • @ZaithwaKunkwezu
    @ZaithwaKunkwezu 20 часов назад +1

    Ine nduwona ngati atipange sponsor ya bundle madam wo😅

  • @steadmangwazu5659
    @steadmangwazu5659 4 часа назад

    Km iyi yokha ndiyokoma 😂😂😂

  • @TapiwaMsutu-bu3ik
    @TapiwaMsutu-bu3ik День назад +1

    Aliyese pamalo pake chete iyaaa sanalakwe madam moinganjira kaya akapanga post ku bafa it's her on life zaziii

  • @chawanangwamkandawire5850
    @chawanangwamkandawire5850 День назад +1

    She didn't grow up in that lifestyle like her step children, nde kumamumvetsetsa munthu akamanyadira. Yemwe zikumunyasa just unfollow, it's that simple.

  • @Botomaniluster
    @Botomaniluster 3 дня назад +2

    Uphawi sizithu guys ndakhulupilira kt uphawi nditchimo cholimbanirana ndi zimayi ndichani kapena alakwirana kumbali zomwe sakunena kma akhale ndmanyaz nyamata amenei

  • @thokomatiti1671
    @thokomatiti1671 3 дня назад +2

    There is an element of sense in his nonsense

  • @NyashaNyalugwe-su9sb
    @NyashaNyalugwe-su9sb 2 дня назад +2

    10 May sasamba ameneyu nde uti??😅😅😂😂💔💔

  • @CarolChundah
    @CarolChundah 3 дня назад +1

    He is a bully ine aindikuonapo chomwe akunena i am only smellingvjelousy ngati ali ndi ma issues akumbali akanangowafotokoza otherwise angondionekela ngat munthu oti mutu wake sugwila coz sindkumutolela ndipo sindingamutolee

  • @KeishaFeston
    @KeishaFeston 2 дня назад

    Olo musiye comment yabwino sizoti akugayila ndalamazo ingonenani zomwe muganizilazo basi osati kufuna kusangalasa wandalama zambiriyo🦦✌🏽

  • @EthelKapachika
    @EthelKapachika 3 дня назад +6

    Aliyese amapanga zikumusangalasa musiyen Madam mpinganjira n palibe chimene umapindula kumalimbana ndi munthu oti amapanga zake pangan zoti zikuthandzen chabe n madam wo anakumana nd a mpinganjira ali ndi ndalama kale ndalama pa ndalama zinzake nde muvutika

  • @mikebikhesoko280
    @mikebikhesoko280 2 дня назад +1

    😂😂 zoti izeki ndi attention seeker simudziwa

  • @TaniahSawa-qc9yd
    @TaniahSawa-qc9yd 3 дня назад +1

    Osauka alibe mau ..alibe kaya anaimba nyimbo iyi ndani kaya fukwa penaso chilungamo chimawandikana ndi mwano😂🤣

  • @chilowaphiri3723
    @chilowaphiri3723 3 дня назад +1

    Chamba sizinthu...If our wishes were horses beggars might ride. In this context, the premise sounds Sarcastic,off board, uncalled for, mudslinging,immature,irrelevant,stunt,caricature and equivocal. Respect elders, you Wil be blessed. The family didn't complain. Let it be. Shalom

  • @LasmieKamwendo
    @LasmieKamwendo День назад

    He's right honestly

  • @desiredicki
    @desiredicki 3 дня назад +2

    Koma samanama mai mpinganjira Ali kaumbulidi

    • @LesenciaMulenga
      @LesenciaMulenga 3 дня назад

      Komapoti money talks

    • @desiredicki
      @desiredicki 3 дня назад

      @@LesenciaMulenga eya koma ndalamaso zikakumana ndi mbuli zimakhala chonchi

    • @LesenciaMulenga
      @LesenciaMulenga 3 дня назад

      @@desiredicki wachimidzi ndi wachimidzi Ola atakhala ndi ndalama zotani

  • @MadalitsoKafwafwa-q1u
    @MadalitsoKafwafwa-q1u 2 дня назад +1

    Sikunyada ayi koma nafeso tikadzalemela ena adzaona ngati matama

  • @marymndala-gi4jc
    @marymndala-gi4jc 2 дня назад

    Umphawi penapake tiziuona komwe ukukupitisa munthuuu, 😂😂😂😂😂😂😂😂😂 nsanje yaonjeza man waa zamanyazi😂😂😂😂

  • @EmmaSoko-w5s
    @EmmaSoko-w5s 2 дня назад

    As long as it doesn't bother the husband, why then does it bother munthu Dela,.ma pic wo the hubby amaonaso n sivuto coz ikanakhala vuto kwaiwowo sibwezi tikuziona....in short hubby alibe nazo vuto.

  • @MonalisaKalasa
    @MonalisaKalasa 20 часов назад +1

    Tamia ur the best

  • @zayfemw
    @zayfemw 2 дня назад

    Aliyense apanga zomwe zikumusangalasa ka ndy aaaaa ine sikuwona vuto Kaya amanyada ndalama ndi zake abale eeeeeee people 😂😂😂😂😂😂😂

  • @chrispinchimganda
    @chrispinchimganda 2 дня назад +1

    He just need some attention that'll 😅😅😅

  • @peacenamadzunda509
    @peacenamadzunda509 2 дня назад +1

    10may naye ngwamaluzi chabe

  • @SpokegStrongwell
    @SpokegStrongwell 3 дня назад

    Or chitakha chilungamo koma doloyu may Ake sadzakwatilidwa Nd Mr mpinganjira ngt uli uphawi sudzatha akapanda kuoimbikila

  • @SpokegStrongwell
    @SpokegStrongwell 3 дня назад +1

    10 may ufuti aaah nde sakwatilabetu mayi Ake ayi

  • @Laurinmuniya
    @Laurinmuniya 2 дня назад

    Akungoyenera kunyada she is beautiful and cash alinayo tiyeni timusiye mwati susochera

  • @MemoryMondela
    @MemoryMondela 2 дня назад

    Ndiwachimidzi nde +kauphawi eeh accident accident 😂😂😂

  • @marymndala-gi4jc
    @marymndala-gi4jc 2 дня назад

    Akufuna attention uyuuuu zaziiiiii

  • @NizziahBanda-mc7kf
    @NizziahBanda-mc7kf 3 дня назад

    Vuto lake kumalawi tili mchimidzi zimenezo kunena azungu ai tikhala chete the problem is iyeyo alibe

  • @MacDonaldMwanje
    @MacDonaldMwanje 3 дня назад

    Palibe za right apapa angonena kuti akufuna 2k timugayire Malo mwawo

  • @shupikayintuwaluwa-5899
    @shupikayintuwaluwa-5899 2 дня назад

    We also learn through others mistakes

  • @JoyJastin
    @JoyJastin 3 дня назад +2

    Kachilungamo kalimo😂😂

  • @errabmaso1337
    @errabmaso1337 День назад

    Adawo maluzi angomugagada😂😂

  • @OmegahKatanda
    @OmegahKatanda 2 дня назад +1

    Ndili mbali ngat Tamia ja

  • @EvieShoe
    @EvieShoe 3 дня назад +1

    Anakapepha ndiye zinavuta

  • @FelixmSankhani-x9d
    @FelixmSankhani-x9d День назад

    10may ali against Mrs mpinganjira

  • @CharityMkandawire-t8u
    @CharityMkandawire-t8u 2 дня назад +1

    Koma kuli ntchito

  • @SpokegStrongwell
    @SpokegStrongwell 3 дня назад

    Kod khope yake Nd iyii 10 may aaaah kutamba awa ,sakwatilabe may ake

  • @URBANMUSICPROMO-l7y
    @URBANMUSICPROMO-l7y 3 дня назад

    Background mwayichepesa

  • @JulietBanda-x9o
    @JulietBanda-x9o 3 дня назад

    Ameneyoyo Ali ndimavut akeso akufuna matukutuku hiyaa

  • @Bigceemacover
    @Bigceemacover 3 дня назад

    Welcome background ine ndi tamia jaa 😅😅

  • @AlickNtenje
    @AlickNtenje 2 дня назад

    uphawi ndi matenda taphuzilani kupanga zanu pilizi

  • @LUCKYSTARR-j4n
    @LUCKYSTARR-j4n 2 дня назад

    10 may mutu wake sugwira amadwala malungo akulu

  • @GrephaMzunga
    @GrephaMzunga 3 дня назад

    😂😂 Ife tiri pano kuona ma comment

  • @hereiam7206
    @hereiam7206 3 дня назад

    A praise team mwafikatu kale😊

  • @puritymsowoya3963
    @puritymsowoya3963 День назад

    Hater uyu chabe

  • @MosesMahowe-vn2tl
    @MosesMahowe-vn2tl 2 дня назад

    Your are beautiful ❤️ Mamie thyona

  • @kingsleydaud9094
    @kingsleydaud9094 3 дня назад

    Enawo angofunapo kuti anthu tiaziwe basi

  • @JalonMgawi
    @JalonMgawi 3 дня назад

    Azipanga zake 50 may yo za ziiiiiii

  • @MILOmw
    @MILOmw 3 дня назад

    His looking for attention koma His also right

  • @ElonBlack1999
    @ElonBlack1999 23 часа назад

    He has fact

  • @MirriamChaswa
    @MirriamChaswa 3 дня назад

    To be honest awawadi amaonjeza aaha
    Kaya it's part of marketing Kaya ndi u street street omwewodi
    Nanga what is that 😅😅😅10th May wangofika potopa ndi Dzuwali koma there's sense in his nonsense 😅
    Am out

  • @MphatsoPembeleka
    @MphatsoPembeleka 3 дня назад +1

    Team #10May😂😂😂🎉🎉🎉

  • @AbrahamBNNkhata
    @AbrahamBNNkhata 3 дня назад

    Sanje.. koma enawo😂😂😂

  • @BenLogistics
    @BenLogistics 3 дня назад

    Umphawi sizinthu 😂😅😂😂

  • @pililaningondo7163
    @pililaningondo7163 23 часа назад

    This guy has issues

  • @ElonBlack1999
    @ElonBlack1999 23 часа назад

    Tom boy iwe

  • @LucyMwaya
    @LucyMwaya 2 дня назад

    His just a bully

  • @SibongireKapalamula
    @SibongireKapalamula 3 дня назад

    Ti adani towilisa mkute mxie

  • @LloydKalanga-f1b
    @LloydKalanga-f1b 3 дня назад

    Mapazi ake…. 10may yo mxiew

  • @AnitaChakwana
    @AnitaChakwana 3 дня назад

    Zisandikhudze🙌🙌

  • @RoseShadreck
    @RoseShadreck 3 дня назад

  • @memorySpeak-m4f
    @memorySpeak-m4f 3 дня назад

    adani oshota awo😂

  • @mtisungejamu793
    @mtisungejamu793 2 дня назад

    Eeishhh 🤣

  • @Ralph092
    @Ralph092 3 дня назад

    That guy is looking for attention

  • @SamanthaNyirenda-p1q
    @SamanthaNyirenda-p1q 3 дня назад

    tiadani tosasamba

  • @DorcasSenzaniNhlane
    @DorcasSenzaniNhlane 2 дня назад

    Nilibe loya😢

  • @MedinahMahomed
    @MedinahMahomed 3 дня назад

    😂😂😂😂😂😂 koma kumeneko

  • @CovenantFBanda-f7h
    @CovenantFBanda-f7h 3 дня назад

    Adani owilisa mkute

  • @BerthaShemu
    @BerthaShemu 2 дня назад

    Tiadani toshota😂😂😂

  • @NizziahBanda-mc7kf
    @NizziahBanda-mc7kf 3 дня назад

    🤣🤣🤣🤣kma yaah

  • @SamNkhomo
    @SamNkhomo 3 дня назад

    🏃🏃🏃🏃

  • @PESHENSI
    @PESHENSI 2 дня назад

    😂