NKHANI ZA ZERO_A NAMIWA ASEPHANA NDI COMMISSION OF INQUIRY YOMWE ACHAKWERA ADAKHAZIKITSA

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 29 окт 2024

Комментарии • 27

  • @MichiasWaluza
    @MichiasWaluza 2 часа назад +5

    Namiwa wapuluka pangonongon pakati pa mikango Oh God bless

  • @Bowa-c7g
    @Bowa-c7g 2 часа назад +3

    Namiwa umatiimilila wakane pagulu apange manyazi

  • @ElizabethMulinde
    @ElizabethMulinde 2 часа назад +2

    Ambuye akhulukukile nonse mumat anamiwa adya bazi nderelo bazi lija lilikut tisamafulumile kuweruza ena zachinyengo simbali yawo

  • @PeacefulBackpacker-mn2gi
    @PeacefulBackpacker-mn2gi 2 часа назад +2

    Namiwa ndi big man ozisata

  • @andrewchakanza6738
    @andrewchakanza6738 Час назад

    🎉 my God bless you all the time and mumatiyimilila big up

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 3 часа назад +2

    Namiwa ai ukuimiradi Amalawi ovutika God bless u

  • @lewisdicksonmlozi130
    @lewisdicksonmlozi130 Час назад +1

    Tsono fuso mkumafusa akupangiranji commission pamene anthu akufuna zobisa kutitenga amalawi fe kupusa

  • @BeckhamDavid-v6c
    @BeckhamDavid-v6c 2 часа назад +1

    Namiwa mulungu apitilize kukupatsa zelu zakuya choncho

  • @JamesRoben-dy7bx
    @JamesRoben-dy7bx Час назад +1

    Sir namiwa mwapanga bwino akanakuphan awa oipa

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 3 часа назад +1

    Kunkuyu chimutu chopanda nzeru iwe ungamuuze Namiwa zochita munthu opusa ngt Kunkuyu sndinamuonepo Namiwa ndimunthu odzindikira safuna zopusa ngt iweyo Kunkuyu

  • @Yungjoe786
    @Yungjoe786 2 часа назад +1

    ❤❤❤❤thanks Namiwa 🫡

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 3 часа назад

    Mwachita bwino Mr namiwa mcp ndichipani chakupha Brov Brov Brov comrade Namiwa

  • @HassanJimmy-r1n
    @HassanJimmy-r1n 2 часа назад

    Ndiyeno mademo achitika kapena ayi?

  • @Davis-qo4qp
    @Davis-qo4qp 3 часа назад

    Mafuta akapezeka ogulitsa pa black market sangapezeke . Vuto ni kusowa kwa mafuta.

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt Час назад

    Udf ddp utm aford boma❤

  • @KossimasiMaluwa
    @KossimasiMaluwa 2 часа назад

    Chakwera walephela bas achoke namiwa umakwana

  • @IsraelMajamanda
    @IsraelMajamanda 2 часа назад +2

    Anthu ngati inu akusowa muli azi busa achinyengo menemo ambuye akudalitse ndipo akutetezeni ndalama ya mwazi ndi yoipa kwambili

  • @ALEXAlli-ck8lj
    @ALEXAlli-ck8lj 46 минут назад

    Tinanenatu ife kut iyi si comission of enquiry yeniyeni ndi za fake lero siizi.

  • @johnniemvula3479
    @johnniemvula3479 3 часа назад

    Namiwa machine 4:18

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 3 часа назад

    Kwachematu

  • @AlihIbrahim-s7v
    @AlihIbrahim-s7v 2 часа назад +1

    Koma mcp😂😂😂😂eeee inu,,,black market inayamba kalekale ndiye ivute lelo😂😂😂abale a central region tiyitanileni kwanuko mafuta mesa alingambwingambwi😂😂😂

  • @EvansNaphazi
    @EvansNaphazi 2 часа назад +1

    Mpunga wa india tu uwu nde muzit mcp

  • @CourageBanda-d1g
    @CourageBanda-d1g 3 часа назад

    Namiwa thank you pa chilungamo kusapakidwa nayo zachinyengo

  • @AlihIbrahim-s7v
    @AlihIbrahim-s7v 2 часа назад

    Koma malawi ndidziko loseketsa ndithu,,,,kukangocha basi tivanji😂😂😂😂

  • @AlihIbrahim-s7v
    @AlihIbrahim-s7v 2 часа назад

    Mwatetezetu Amayiwa😂😂😂😂mcp musayiyiwaletu

  • @AlihIbrahim-s7v
    @AlihIbrahim-s7v 2 часа назад

    Inu bwelani ku Hot currency,,,malawi basi wavunda uyu,,,,wa mcp sangapange comment apa 😂😂😂😂chilungamo akuchiwona okha,,,koma atani basi Boma ndilomweli la Malawi😂😂😂😂😂

  • @BeckhamDavid-v6c
    @BeckhamDavid-v6c 2 часа назад

    Namiwa mulungu apitilize kukupatsa zelu zakuya choncho