Boma lapanga hayala asilikali a Rwanda ndi Zimbabwe kuti adzagwire Bakili Muluzi TV

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 5 окт 2024

Комментарии • 482

  • @JohnConar-kq4hi
    @JohnConar-kq4hi 4 месяца назад +57

    Bakili muluzi TV RUclips channel Never arrested I'm telling you this is home land we are democracy now🇲🇼🇲🇼🇲🇼

    • @harrisbanda5891
      @harrisbanda5891 4 месяца назад

      Dat's true bro, we're in a democratic society and noone lemme repeat noone can come and intimidate us in our own country!, Bakili Muluzi tv is a genuine freedom fighter and He's a Hero and watever is saying or talking is the truth!, mukuleka kusakana ndikumangana nokhanokha am'boma inu amene mukutionongela misonkho yathu, pano mwagundika kupanga hire kapena kuti hayala mbava ndizigawenga zimzanu zaku Zimbabwe ndi Ruanda kuti zithane ndi anthu olankhula chilungamo, for wat!, shame on you zikhale ng'oma and mozesi kumukuyu, shame on you!, .
      Bakili muluzi tv will Never ever be arrested and if u'll try to do dat, we'll fight each other!,

  • @LetsSeePlaces43
    @LetsSeePlaces43 4 месяца назад +11

    Kodi kukukumbutsani bodza lomwe munkatisambitsa nalo 2020 lija kukhaleso mulandu?? Mukuba ndipo aliyense akuona komaso Akudziwa kukuwululani ukhale mulandu??? Viva Bakili muluzi Tv ❤❤❤❤

    • @LuundoJohnkabage
      @LuundoJohnkabage 4 месяца назад

      Ndipo inu ati tidzisangalala ngt zukomela tose kma Mulungu alipo ndipo ndimwini chitetezo ameen

  • @DumisaniMhango-e4i
    @DumisaniMhango-e4i 4 месяца назад +15

    We love bakili muluzi tv than chakwera

    • @MsondaBanda
      @MsondaBanda 3 месяца назад

      Amaphoyisa bophani yonke uyathuka Mulungameli , bayadelela laba banthu

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 4 месяца назад +4

    Keep it up bakili muluzi TV ziyaluke mbamva zimenezi

  • @serakillo8668
    @serakillo8668 4 месяца назад +5

    Nkukuyu phwala lako ndithu osakungwira iwe unapha alani witika bwanji bolo yako kuphatikiza zinkhale ng'oma ndi chakwera nose bolo zosadulindwazo zozaza madeya muuzane ❤❤ bakili muludzi channel tsimupata munyera manyi onukha

  • @Lizzie-h1k
    @Lizzie-h1k 4 месяца назад +6

    Palibe, we love bakili muluzi tv....osati tv ya muluzi..😂😂😂😂😂

  • @Vincentmandota
    @Vincentmandota 4 месяца назад +2

    We love Bakili muludzi tv best TV ever

  • @CharlesTambala-zn2bd
    @CharlesTambala-zn2bd 4 месяца назад +4

    Kodi..uwu wa mutu ngati nkhonkhwe mmati ndani... ? Kunkuyu ..akunama kwambiri....
    My brother, you are opening the minds of vulnerable Malawians. Keep it up...afa ndi mtima

    • @Allan-bk1
      @Allan-bk1 4 месяца назад

      😂😂😂😂😂😂😂 koma ndaseka

    • @harrisbanda5891
      @harrisbanda5891 4 месяца назад

      😂😂😂😂😂, wamutu ngati chikwele cha nkhunda kkkkkkk

    • @mussasamuel774
      @mussasamuel774 4 месяца назад

      😂😂😂😂😂😂

  • @AhmedPhillip
    @AhmedPhillip 4 месяца назад +7

    Machende achakwela ndi agalu azake osavinidwa am here Durban lamontville ngati akufuna andipeze viva bakili muluzi 📺 we are behind you

  • @rashidlamos3403
    @rashidlamos3403 4 месяца назад +1

    God protect bakili muluzi channels tv

  • @MathewsMynus-ow6no
    @MathewsMynus-ow6no 4 месяца назад +1

    Aaaa koma ana inu mwasowa zochita et wa bakili muluzi tv Mulungu amutezera

  • @MaIikhiziDawood-lm7mg
    @MaIikhiziDawood-lm7mg 4 месяца назад +1

    God BLESS You
    Appreciate TE You
    AND RESPECT You
    DEFINI TELY For You

  • @Dee-h7c
    @Dee-h7c 4 месяца назад +2

    Long Live bakili muluzi tv 🎉🎉

  • @AmandaConstance-fx8cr
    @AmandaConstance-fx8cr 4 месяца назад

    The angles of God will be always around you protecting you where ever you are sir Mr bakili TV 🙏❤❤❤❤

  • @OZIELBLESSINGS
    @OZIELBLESSINGS 4 месяца назад +1

    Ndakayika ngat angazikwanise akuziyambazi, people loves you boss and I'm one of them ❤

  • @ishaqyassin5001
    @ishaqyassin5001 3 месяца назад +1

    Koma Mwapanga ko note kuti WA Bakili Muluzi TV kuti ziiiiii?

  • @EddieBakali
    @EddieBakali 4 месяца назад +1

    We stand with bakili muluz

  • @marshacee8315
    @marshacee8315 4 месяца назад +1

    Koma guys nduna ziwiri kukanika kugwira ntchito za Boma nkhani koma Bakili muluzi tv zoona?😂😂😂

  • @HarryKabambe
    @HarryKabambe 4 месяца назад +1

    Muuzeni galu was kaunjikayo kuti its not TV ya muluzi Bakili, it's TV on its own

  • @NoohNowa
    @NoohNowa 4 месяца назад +3

    Malawi police kukanika kugwila munthu wamba ndiye angagwile zikale ng'oima homeland security wakubayo 🤣🤣🤣

  • @injesimadera1313
    @injesimadera1313 4 месяца назад

    Stay safe my brother!!! We love you and we wish you a long life

  • @CassimMbalaka
    @CassimMbalaka 4 месяца назад +1

    Kuliufulu Mani tsitsani suger soap ndi Xina musiyeni muthu

  • @mathewsphiri5779
    @mathewsphiri5779 4 месяца назад +1

    No worries we are together atigwira tonse

  • @HashimChimdidi
    @HashimChimdidi 4 месяца назад +1

    Mcp kupumila ku nkhwapa chifukwa cha bakili muluzi tv munya agalu inu ndi corruption yanuyo bakili muluzi inabwera kuzakhala pano ndipo sizasitha

  • @LemanJackson
    @LemanJackson 4 месяца назад +2

    Mitu siukugwila kulimbana ndianthu Malo moto akonze ziko

  • @MustafaLikaomba
    @MustafaLikaomba 4 месяца назад +1

    Boma lopusa kwambiri satana amadana ndichilungamo ziwanda izi

  • @cassimyusuf6683
    @cassimyusuf6683 4 месяца назад +1

    Zimapanga hate akubanu, pomwe ife osawukafe timanjoya ndi bakili muluzi TV kuposa chilichose

  • @PatiencejonasiAustin
    @PatiencejonasiAustin 4 месяца назад +1

    Agalu anenewa asagwila mbava zikuba ndalama boma

  • @HarryNtanga
    @HarryNtanga 4 месяца назад

    Bakili muluzi tv osafooka ndip osaopa Pali chilungamo sipakhala mantha kip it up love you more

  • @Drmuhammadchiwona
    @Drmuhammadchiwona 4 месяца назад +1

    Kkkkk koma azikhale mwangokula mutu koma ulibe nzelu bakili muluzi tv simungamukwanise ameneuja ndipatali ife tithane ndinu sopapano agwape inu

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm 4 месяца назад +4

    Akutaya nthawi Yao zangamupeze ameneyo Chakwera must go

  • @jameschibisa1433
    @jameschibisa1433 4 месяца назад

    Mphwanga iweyo ndi akatundu police ya ku malawi yakukanika 😂😂😂😂😂 kenako akunena zosemphana brother keep it the fire burning one year left

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx 4 месяца назад +1

    Yesani kumumanga muwone ngati mukuganiza kuti timakuopani.
    Mukuona ngati ndinu amuyaya inuyo eti.
    Nafensotu mifuti tilinayo

  • @FrankBanda-c3e
    @FrankBanda-c3e 4 месяца назад +1

    Best tv ever in Malawi ❤❤❤

  • @IbrahimDailes
    @IbrahimDailes 4 месяца назад

    Tchito kulimbana ndi anthu azanu si kukweza kwacha we love this guy bakuli TV mo 🔥

  • @augustMag
    @augustMag 4 месяца назад

    Mmmmmhu mpaka asilikali akuja akuchedwa brother Bakili Muluzi TV 🔥 iwowatu ai Mulungu ai ndbwino kuti azingopanga zoti adyeretu chifukwa nthawi yawathera 2025 ulamuliro wao ukutha monga momwe MULUNGU anawatulusa Aisrae ku Egypt ifenso ku Bagga moyo tikutulukako ndithu Mulungu wamphamvuzonse apitiliza tchito imene anayamba mwa Inu Ndipo azikutetezani 🙏

  • @MisheckKamwendo-w9n
    @MisheckKamwendo-w9n 4 месяца назад +1

    Paja kalindo amawuza kuti ndilipano mundimange amamuopa asamakuopsyezeni ameneo thawi Yao yatha akupita ameneo

  • @Nathkala997
    @Nathkala997 4 месяца назад +2

    Bomba sakhalisa chifukwa likaphulika silibisika

  • @Moses51
    @Moses51 4 месяца назад

    Keep up bakili muludzi best TV in Malawi 🇲🇼💯

  • @patrickscott9086
    @patrickscott9086 4 месяца назад +1

    Uyu2 amanena chilungamo mugwile mbava zili m,boma nanga mpaka kulimbana ndi mwana ngat ameneyo. Pangani zina

  • @GiftMwale-i4k
    @GiftMwale-i4k 4 месяца назад

    You will never get Bakili muluzi TV he's always with God and I am praying for him to be safe bakili muluzi TV is there to tell us truth

  • @DicksonBlack
    @DicksonBlack 4 месяца назад +1

    Akamupeza chakwela azankhala wamuyaya bolezamawo muonaso Kodi bakili muluzi ndiye ikugwesa kwacha iiiya zausilu basi

  • @HassanCharle
    @HassanCharle 4 месяца назад

    Ndine mosi kwa andu amene amasapota Bakili muluzi TV sikomo amalawi asanga

  • @zephasibanda4462
    @zephasibanda4462 4 месяца назад +1

    Kodi aboma mulibe zina zochita kuma offece anuwa mwatikwanatu pano bakili muluzi simavuto athu ife tikufuna ma passport agaru inu kodi mukufuna anthu atani

    • @harrisbanda5891
      @harrisbanda5891 4 месяца назад

      😂😂😂😂😂, amenewa siagalu ayi koma imbwa za dogs

  • @milliambandah1939
    @milliambandah1939 4 месяца назад +1

    Mmalo mosaka zakudya anthu akufa ndinjala ndiye kumaononga ndalama kusaka wa tv mbuzi zanthu

  • @saidichirwa5456
    @saidichirwa5456 4 месяца назад +1

    Sitikuopa ,mukudana ndi chilungamo inu.mukufuna kumaba opanda okudzudzulani.Brother usanyumwe nawo makapewa.

  • @Ocean20020
    @Ocean20020 4 месяца назад +2

    That will not happen

  • @tisamulangala5570
    @tisamulangala5570 4 месяца назад

    Bakili tv God bless you ❤❤

  • @EdwardMwale-p2j
    @EdwardMwale-p2j 4 месяца назад +1

    Mukapanga masewela tiyambisa gulu lazigawenga tithana namwe sitingakuopeni ayi

  • @ibrahimmeemzy9754
    @ibrahimmeemzy9754 4 месяца назад +1

    Number one tv❤❤❤🎉🎉

  • @FonexLackson
    @FonexLackson 4 месяца назад

    Zisilu izizi Bakili Muluzi TV. Musakhotese nkhan pamenepo akuti TV ya abakili mapazi ao anthu okuba inu

  • @MusaWilliam-t8n
    @MusaWilliam-t8n 4 месяца назад +1

    Komanso nkulu ameniyi akuti nduna yanji sichidakwa chimenechi

  • @JannatuyaseenmwangaMwanga
    @JannatuyaseenmwangaMwanga 4 месяца назад

    Zitsiru za anthu izi
    Mwavomereza kuti akunena zowona
    Mulungu amutetezere B muluzi ❤❤❤

  • @ShadreckKaleso
    @ShadreckKaleso 4 месяца назад

    Mulungu atithandize ameneyi asamupeze ndithu, mwaiyeyi tikudziwako zinsisi zambiri🙏

  • @JimmyIsaac-xd4ef
    @JimmyIsaac-xd4ef 4 месяца назад +1

    Mitu yanu simagwira. Malo mokoza mavuto amene akukumananawo a Malawi

  • @sanlakedickson6780
    @sanlakedickson6780 4 месяца назад +1

    anthu akuba awa ndipo mayazi zitsilu izi zichoke boma zikuba kwambiri

  • @RhodrickKambale
    @RhodrickKambale 4 месяца назад +1

    Muchoka chaka chamawa inuyo ndipo simumukwanitsa wa bakili muluzi

  • @MuhammadBAKILI-kl2mj
    @MuhammadBAKILI-kl2mj 4 месяца назад

    😂😂😂😂😂😂😂 chimimba ngati finye
    Ifeyo we Love ❤️ Bakiri muluzi TV

  • @Nelsonmacken
    @Nelsonmacken 4 месяца назад +1

    Koma kusowa zochita boma ili aaaaa koma kuputsa kwenikweni uku

  • @paulpaseli6310
    @paulpaseli6310 4 месяца назад +1

    Boma lazaza ndi zisilu mwava

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 4 месяца назад +1

    Asa azibambonakulu akulu ngati inu mpaka kusaka bakili muluzi TV ASA kuwopa chilungamo koma azathu mwalemelatu ma tissue ndindalama

    • @owenmoses9434
      @owenmoses9434 4 месяца назад

      Komatu God is watching what u are doing guyz nd mcp yanuyo

  • @frankiechasokoneza5802
    @frankiechasokoneza5802 4 месяца назад +1

    Koma zoona bomali ndalama azionongela zachibwanaziii

  • @innocentissah2636
    @innocentissah2636 4 месяца назад +1

    Imeneyi ndiye nkhondo, mukuona ngati chipani chanuchi ndi chamuyaya eti

  • @HarrisonKalonga-k7p
    @HarrisonKalonga-k7p 4 месяца назад +1

    Bakili muluzi TV ❤❤

  • @alfredbanda1693
    @alfredbanda1693 4 месяца назад

    Remember security is rule number one maintain your situation awareness coz ili ndi boma but all in all keep it up

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733 4 месяца назад +1

    Zikhale ng'ona musamadana ndi chizuzulo zikalakwika zalakwika

  • @PreciousChlima
    @PreciousChlima 4 месяца назад

    I love bakili muluzi tv,, Mcp nthawi yanu koma chaka cha mawa tionana

  • @FatimaKazembe-ot1os
    @FatimaKazembe-ot1os 4 месяца назад +1

    Best tv

  • @SPAGHETTI313
    @SPAGHETTI313 4 месяца назад

    Ana achepa
    Bakili muluzi tv is our bold Best whole Malawi

  • @AndersonBishop-i2t
    @AndersonBishop-i2t 4 месяца назад +1

    Mbuzi ya munthu president ameneyo kuchita kuwopa bakili muluzi Mesa kubako achina mapwalanu

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo 4 месяца назад +1

    Mungoonanga ndalama zaboma a zikhale ng'oma Pangani za minster of finance ija ndinu agalu kwabasi

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 4 месяца назад +1

    Ayelekeze kukumanga Ku Malawi kuvuta ndithu

  • @jamesgama5489
    @jamesgama5489 4 месяца назад

    Viva bakili muluzi tv 📺 ♥️ viva, bakili muluzi tv woyeeee ku nkuli kwereko kuchitekete.

  • @saidichirwa5456
    @saidichirwa5456 4 месяца назад +1

    Iyi ndi tv #1 kumalawi

  • @HajieMusitafa
    @HajieMusitafa 4 месяца назад +1

    Zisilu iizi zosowa zochita mmalo mokodza ziko ndiye munakula bwanji

  • @EvansPhiri-ug4oz
    @EvansPhiri-ug4oz 4 месяца назад +1

    Chakwela ndi cabinet yake zisilu

  • @AhmedHchipelesa-zm8oe
    @AhmedHchipelesa-zm8oe 4 месяца назад

    Imagine the whole government now it's against bakili muluz tv chilungamo baba munya

  • @JogaJoseph
    @JogaJoseph 4 месяца назад +1

    osaopa ndi agaluu amenewo chilungamo chikuwawawa

  • @JACKSONHULUWA-j2n
    @JACKSONHULUWA-j2n 4 месяца назад +1

    We are in democracy

  • @Innocent-vr6pu
    @Innocent-vr6pu 4 месяца назад

    Kd za mikangano ya Malawi ndi Mozambique chinachitika ndichani ?

  • @unarinematshomo2841
    @unarinematshomo2841 4 месяца назад

    A achipani cholamula odana ndi chulungamo, ndee mwati Bakili tv ikulakwitsa pati?

  • @NgomaRaheem
    @NgomaRaheem 4 месяца назад +3

    Pepe kale kod uuzitenga ngat ndiiwe wamuyaya et ediot Nkukuyu mbuz

  • @rangersonngirazi6741
    @rangersonngirazi6741 4 месяца назад

    Keep fire burning

  • @Kaliati91
    @Kaliati91 3 месяца назад

    Bro is on the run

  • @WinerdShadreck
    @WinerdShadreck 4 месяца назад

    Boma la ambuli but do you know social media 😂😂

  • @patrickthomson
    @patrickthomson 4 месяца назад

    The power truth, God protect your Angel, he is unlocking most of received civilians

  • @AbdulNyambi-n4s
    @AbdulNyambi-n4s 4 месяца назад

    Kunyasa ngati manyi ulibe manyazi ukamayankhula zimezo malo moti muzipanga solted out za kwacha devaluetion mboli zanu muyelekeze mu gwile wa bakili muluzi tv muziwona nosenu tithana nanu

  • @KumbukaniChimbalanga
    @KumbukaniChimbalanga 4 месяца назад +1

    Sizoopsesa anthu mdziko muno ali mu democracy

  • @KumbukaniChimbalanga
    @KumbukaniChimbalanga 4 месяца назад +1

    Ungamugwire ndani iwe

  • @emmanuelchavula7144
    @emmanuelchavula7144 4 месяца назад +1

    Zaziiiii nduna zina zomwe zilizopandq zeru zimenezi

  • @ChimwemweSafelana
    @ChimwemweSafelana 4 месяца назад +1

    Kukula mutu koma zeru zero basi tamaendani mmidzimu koma muende opanda ma guard ok

  • @ThokoBanda-s9p
    @ThokoBanda-s9p 4 месяца назад

    Akulu ife tidzalowelera serious tidzapanga mademo coz palibe zimene mukhoza kumagwidwila mudziko la democracy

  • @JoeMahata
    @JoeMahata 4 месяца назад +1

    Mbuzi za wanthu mmalo mothana ndi mavuto awanthu ndalama muzionongela kumanga munthu

  • @sufiammadi
    @sufiammadi 4 месяца назад +1

    Anthu sakugona tulo eti 🙌🙌

  • @mussasamuel774
    @mussasamuel774 4 месяца назад

    Ife ndye bakili muluz tv yo😂😂😂😂 paja amat chilungamo nd mwano😅

  • @VillanMakwacha
    @VillanMakwacha 4 месяца назад +1

    Koma nayo nduna busy kufuna munthu wapq yutube abare instead of focusing on PASSPORT PROBLEM

  • @EmmanuelLemson
    @EmmanuelLemson 4 месяца назад +1

    Kutengera nd video iyi ikiperekera umboni oti anthuwa si anthu

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 4 месяца назад +3

    Pa mtumbo pake Chakwera ndi anzake

  • @hassammaulana4529
    @hassammaulana4529 4 месяца назад

    Kusiya kusaka akumba ndlama mboma koma tv yathu eeti
    Musiye kumba tisiya kunena za inu

  • @georgemponda
    @georgemponda 4 месяца назад

    Boma lolephera ngati ili have never see it before.... instead of getting busy fixing major problems that many Malawians are facing today they are busy hunting BAKILI MULUZI TV, shame on you useless leaders