Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Crispy’s consistency is unmatched 🔥. I use to be a fan but after this am a whole air conditioner 🔥🇲🇼 🐐
Thass a bar tho
@@Sikovelli😊q1q1
utipweteka ndi bars,,, u need a feature
😂😂😂
Being a Spe fan is so fun
Live man
kupanda kuthamanga dziko nde limalanga, wekha kuzidabwa kuti mwina kwako kwatha, going jogging kumangofeela uzithamanga, 🎶🎶🔥🔥
Real gee komaso ya Zina Zina Zina Zina ikufunika fast fast
Tiyeni tikathamange ma guy
Dolo kwambiri!!!
The visuals are on point...zaudolo koma zapa easy
Ahhhh amwene landilani maluwa kachikenaso
Ine ndimapanga zomwe ndimafuna iwe umalandila zomwe amakupasa 🦅 2:29
Kudya runs
Kumathamanga
A crispy muzithamangaka
Olo Khili amaziwa spe amathamanga
Big stepper
koma spe iweyoo eeeeee 🔥🔥🔥🔥🔥iwe ndi FISI umadya ma goat
umanya kale🔥🔥🔥🔥
spe munyimbo zake muli nzeru🤩🤩🤩
Eish El Presidentè
I’m from Kenya 🇰🇪 can’t really understand the lyrics but nyimboyi ili mwala 🔥
😂😂😂 kma ndee waku kenya
😂😂😂😂😂
😂😂😂 koma nde akukenyadi
Akaka kokha nde Kali hard kwambili
Even spe atskhala ndi ma fan ochepa azablower be mpaka international 🔥🔥
Utha kusuta kuti ugenny confi🔥
Utha kusuta kt U Gainy ConfiiKm bola osathamanga 😅 Spe unanza iweyo tayambaso kale kuthamanga apa
Fada
I love you spe🎉🎉
BBrrrrr🚀🍄
spe 🔥 🔥 ine ndimatenga zomwe ndimafuna iwe umalandira zomwe amakupasa
Amene sali fan nde akumva kuwawa😂.. Kaya ife tikumva kukoma🔥
Spy ndi sha sha🔥🔥🔥
Abale sound system Ass🎉
Liwilo🔥💯🏃♂️🏃♂️gear
That's hes the Goat theee Goooaaatt
A daily dose of spe for my sanity🙏🏾
Madolo a Mario bros mmatulutsa nyimbo eeh 🔥🔥🔥🙌😅
Spe to the World
Bars😂😂 spe to the wrld
🔥😮💨🔥 ThAmangq
Spe Spe speeeee🔥🔥🔥
siya chilichose iwe crspy wadropps
Siwe hule sizongogona ku Culture 😂🔥 #SPE🔥🙌
Uzithamanga🔥🔥
Dolo kwambiri 🔥🔥🔥🔥
Nice piece Spe... Nyimbo zadzeru nyimbo zabwino
Pambuyo pa achina Spe😎
Mad respect🔥🔥🔥 concept and wisdom in it top tier
U Killed it
Spe uja ndi dolo🔥
sungakhale okwiya ndikumvera Spe😂
Goat 🐐
Madalo opseza ana amabwana sakumathanga 😂😂😂😂 spe adha
DELIVARY BOY MLWIAN
sungathamange madzi atafika nkosi
Umadziwa umadziwa 😂👍Tithamange basi 🚀🔥
Wow spe ain't playin 👌🔥🔥🔥
timakufilan amwene mumaika sound
Sankha kufila spe or kumwa tameki
Spe eeh👐
Int Spe
Spe on point u neva disappoint
Yessssir! 🐐
Spe to the world 🌍
Ma guy nde asankha kuti azifila spe🙌🔥🔥
Man’s is fresh wit’ it! Fire concept, flow & delivery! Creative for days! 🔥🔥🔥
Uzithamanga spe to ze world 🌎
After me raa someone has to come back again💯💯💯Ankanena @Spe🤫
Muli ka diss 😂🤣
Spe wabwera 🔥🔥🔥
Kumathanga🤞♥️
Madzi ali Nkhonsi athamanga bwa😂😂
Spe unapitilira❤
Run🔥🔥🔥
Spe 🔥🔥
NEXT BIG THING IN AFRICA BRO
Uthaku🚬🚬kma bola osa🏃♀️🏃♀️🏃♀️🏃♀️
Fadah🔥🔥🇲🇼
Spe for El Presidente
Âbálé ❤❤
🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Chimtchan changa Iwe
Kudya ma runs 🏃♂️
Kumathamanga 🔥🙌
Abale 💚
SPE for life🔥💯
Kom spe 🔥🔥🔥
Uzithamanga
Spe 🔥🇲🇼🐐
koma spe!! kutidzidzimutsa nayo 🔥🔥
Spy ur the best
Unaza fadha
Achina spe ase 🔥🔥🔥💯💯
Spe Will lats forever cause he's the greatest of all time I love u bro ❤
Speee ndi dolo ma guy
I can see the album coming 🔥🔥... Eeeh Spe unatha mantha
Achina spe
Spe iwey unabwera
Ndiwe dolo asee...iwe ndi Phineas are GOATS
To the world🔥
spe💯
dolo uzithamanga thaw yatha
Eeeh spe ukuthamanga😌😂
❤❤❤uzithamanga
Koma yah😂 running bas
Crispy’s consistency is unmatched 🔥. I use to be a fan but after this am a whole air conditioner 🔥🇲🇼 🐐
Thass a bar tho
@@Sikovelli😊q1q1
utipweteka ndi bars,,, u need a feature
😂😂😂
Being a Spe fan is so fun
Live man
kupanda kuthamanga dziko nde limalanga, wekha kuzidabwa kuti mwina kwako kwatha, going jogging kumangofeela uzithamanga, 🎶🎶🔥🔥
Real gee komaso ya Zina Zina Zina Zina ikufunika fast fast
Tiyeni tikathamange ma guy
Dolo kwambiri!!!
The visuals are on point...zaudolo koma zapa easy
Ahhhh amwene landilani maluwa kachikenaso
Ine ndimapanga zomwe ndimafuna iwe umalandila zomwe amakupasa 🦅 2:29
Kudya runs
Kumathamanga
A crispy muzithamangaka
Olo Khili amaziwa spe amathamanga
Big stepper
koma spe iweyoo eeeeee 🔥🔥🔥🔥🔥
iwe ndi FISI umadya ma goat
umanya kale🔥🔥🔥🔥
spe munyimbo zake muli nzeru🤩🤩🤩
Eish El Presidentè
I’m from Kenya 🇰🇪 can’t really understand the lyrics but nyimboyi ili mwala 🔥
😂😂😂 kma ndee waku kenya
😂😂😂
😂😂😂😂😂
😂😂😂 koma nde akukenyadi
Akaka kokha nde Kali hard kwambili
Even spe atskhala ndi ma fan ochepa azablower be mpaka international 🔥🔥
Utha kusuta kuti ugenny confi🔥
Utha kusuta kt U Gainy Confii
Km bola osathamanga 😅 Spe unanza iweyo tayambaso kale kuthamanga apa
Fada
I love you spe🎉🎉
BBrrrrr🚀🍄
spe 🔥 🔥
ine ndimatenga zomwe ndimafuna
iwe umalandira zomwe amakupasa
Amene sali fan nde akumva kuwawa😂.. Kaya ife tikumva kukoma🔥
Spy ndi sha sha🔥🔥🔥
Abale sound system Ass🎉
Liwilo🔥💯🏃♂️🏃♂️gear
That's hes the Goat theee Goooaaatt
A daily dose of spe for my sanity🙏🏾
Madolo a Mario bros mmatulutsa nyimbo eeh 🔥🔥🔥🙌😅
Spe to the World
Bars😂😂 spe to the wrld
🔥😮💨🔥 ThAmangq
Spe Spe speeeee🔥🔥🔥
siya chilichose iwe crspy wadropps
Siwe hule sizongogona ku Culture 😂🔥 #SPE🔥🙌
Uzithamanga🔥🔥
Dolo kwambiri 🔥🔥🔥🔥
Nice piece Spe... Nyimbo zadzeru nyimbo zabwino
Pambuyo pa achina Spe😎
Mad respect🔥🔥🔥 concept and wisdom in it top tier
U Killed it
Spe uja ndi dolo🔥
sungakhale okwiya ndikumvera Spe😂
Goat 🐐
Madalo opseza ana amabwana sakumathanga 😂😂😂😂 spe adha
DELIVARY BOY MLWIAN
sungathamange madzi atafika nkosi
Umadziwa umadziwa 😂👍
Tithamange basi 🚀🔥