Ineso sindimamumvesa koma apa ndamumvesa , koma panopa ziko linasintha si tonse tingaonele live, koma mwina aziyagawa alive paokha apa social media pawokhaso, Eyetu mr jokes sakulakwisa ai kudandaulaku chonchi. Maybe group ya maso award -wa zimaoneka kuti ndi business ku internet -ku amapeza phindu choncho Ku ma live -ku palibe chimene amapeza , ine ndikuona ngati choncho.
Uyu ndiwanzeru ngati Dr Michael Usi❤❤❤
Kuzindikira ndie kumeneko bravo jokes
That's true
Akudandawula zoonadi ku Malawi kupondereza pazilizose
Komatu nkhaniyoso ndiyowona timuvesese
Malawi sazatheka ndithu🥴🥴
Ineso sindimamumvesa koma apa ndamumvesa , koma panopa ziko linasintha si tonse tingaonele live, koma mwina aziyagawa alive paokha apa social media pawokhaso, Eyetu mr jokes sakulakwisa ai kudandaulaku chonchi. Maybe group ya maso award -wa zimaoneka kuti ndi business ku internet -ku amapeza phindu choncho
Ku ma live -ku palibe chimene amapeza , ine ndikuona ngati choncho.
Mr jokosi ingoyedzeka basi kkkkkkkkkk
Jokisi yi sakunama athu tikuvota koma owina awawinisa kale
Koma nde zoona
Actually ndizoveka zomwe akukamba only few people can understand this let it go buddy