MWANA AMENE MATSOKA AMANGOMUTSATIRA, ANTHU OMUSUNGA AMANGOMWALIRA MWA DZIDZIDZI

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 7 фев 2025

Комментарии • 40

  • @UlemuChisale-q6x
    @UlemuChisale-q6x 10 дней назад +1

    Honer to the creater ❤

  • @MariaKampando
    @MariaKampando 13 дней назад +4

    Akundimvekere ngati brother wake wa Maxwell Kaluba.

  • @CharityKatunga-v4r
    @CharityKatunga-v4r 12 дней назад +3

    Moyo uliwonse Mulungu amakhala nawo cholinga ndipo amaulemekeza that's why or anthu akude koma Mulungu is always on your side Ambuye azikula nthawi zonse

  • @ChikondiTewesa
    @ChikondiTewesa 12 дней назад +3

    Eeee Koma kumwamba kuli mulungu ndipo munthu aliyense amakhala naye ndicholinga😢mnyamata wadusa munyengopweteka uyu God is great

  • @JosephyMoyenda
    @JosephyMoyenda 11 дней назад

    Tsogoro ra muthu or mutamutchinga bwanji kom murungu amachita choti adan mitu igwe pas amen and amen

  • @JumahChitete-l8g
    @JumahChitete-l8g 13 дней назад +3

    God is good 👍

  • @ReginaAwali
    @ReginaAwali 12 дней назад

    Eeee koma ya kuchigayoyo mmm kunalidi kutali, pano kaya anaika mkati muja 🙌🙌🙌🙌

  • @AffectionateLemming-ie7mr
    @AffectionateLemming-ie7mr 13 дней назад +1

    That's my wish also....may God help me

  • @DalisoulThom
    @DalisoulThom 13 дней назад +1

    God bless you

  • @PrinceChapola
    @PrinceChapola 12 дней назад

    Timusiye mulungu akhale mulungu ndipo amakonda aliyense God is good

  • @KennethSingano
    @KennethSingano 13 дней назад +3

    Eshii koma moyo ndi ulendo wautali kwambiri komanso omvuta mulungu atithandize ndithu

  • @chirwaellace1093
    @chirwaellace1093 12 дней назад

    Potazio God is good

  • @FloridaKaunda
    @FloridaKaunda 13 дней назад

    God is good

  • @ChifundoNinje
    @ChifundoNinje 8 дней назад

    Mulungu akudalise ukugwila tchito yotamandika

  • @LucyKulemeka
    @LucyKulemeka 13 дней назад

    God should continue enlargening your territory 🙏

  • @CatherineNantchengwa-d4w
    @CatherineNantchengwa-d4w 13 дней назад

    Mmmm pepa km Mulungu Ndiwabwino Nthawi Zomse

  • @ImranWyson-e9o
    @ImranWyson-e9o 14 дней назад

    Nkhani yochititsa chidwi❤

  • @faithkunjilika
    @faithkunjilika 13 дней назад

    MULUNGU akafuna kusintha munthu amapanga zimenezi ndaonela David anakhlapo mfumu ya ISRAEL koma anamuchosa kodyesa ziweto kutchile

  • @SamuelKhumbiwa
    @SamuelKhumbiwa 13 дней назад

    Mulungu ndiye mboni yako.kuseli kwa mavuto kuli mayankho,kumuziwa mulungu timamuziwa moteromo.

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn 14 дней назад

    Sad story

  • @gertrudeJim-o6l
    @gertrudeJim-o6l 11 дней назад

    Kuli Yaweh kumwamba

  • @LuciousJacksonMbewe-w6x
    @LuciousJacksonMbewe-w6x 13 дней назад

    Anali wovuta ameneyo ndamukumbukira 2009

  • @ZilimumtimaMusah
    @ZilimumtimaMusah 14 дней назад

    My son watch this pls fleture

  • @IsabellaMphande-j6x
    @IsabellaMphande-j6x 13 дней назад

    Kumwamba kuli Mulungu

  • @ThomsonMusowa-w9g
    @ThomsonMusowa-w9g 12 дней назад

    Tapakidwapo mpunga pakamwa koma osadya olo supuni

  • @LovenessKapindula-t6e
    @LovenessKapindula-t6e 14 дней назад

    Simasoka koma ndi tumiki wa mulungu ameneyu

  • @BridgetChelewani
    @BridgetChelewani 13 дней назад +1

    Ineso ndadusa mofana ndi ameneyo

  • @MilicaNkhata
    @MilicaNkhata 13 дней назад

    Mmmm km yaaa

  • @MercyMatsimbe-f8j
    @MercyMatsimbe-f8j 14 дней назад

    Mulungu ndiodabwitsa

  • @Preciouspelera
    @Preciouspelera 12 дней назад

    𝑮𝒐𝒅 𝒃𝒍𝒆𝒔𝒔 𝒚𝒐𝒖

  • @raphaelmatias7194
    @raphaelmatias7194 13 дней назад

    Eishhh sorry

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm 14 дней назад +1

    Eeee zooopsa kwambiri Koma MULUNGU Ndi wa chifundo

  • @DannyKalumbaWaBanda-q7o
    @DannyKalumbaWaBanda-q7o 13 дней назад

    God bless you 🙏🙏🙏

  • @BerthaBenesi
    @BerthaBenesi 12 дней назад

    God is good 🙏🙏🎉

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm 12 дней назад

    God is good