Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Mayi xokoxoko ndi amuna awo chisangalalo nthawi yoxepa, kenaka maphokoso okhawokha, kkkkk!!!
Koma banja la A shokoshoko. They deserve each other ❤️❤️🔥
Chipwana ndi munyani mumakwana ndikudikila nep man ndikazi omwe akaonkha asanafusele aja koma kumapanga msanje ❤
Kma mercy usithadi iwe bwanji ukusekaso😂😂😂😂
Chipwanya ndi munyanyiwa ayi mumandi wadza kkkk nice comedy
😂😂😂😂 akuti ngt ulibe list ija uzingoti ndikupita kunsika osati ndukagula ma groceries 😂😂😂 love you more team of mndyangu
Ashokoshoko ndi akazi awo eeeeeh koma mkaziyo ndi waya
Chiphwanya anakomza😂😂😂😂😂😂😂 eish nsanje mpkana kumuyalutsa mzako kunama ya mikozo
Mwana _-_-_-__-_---_wa--__-_-aaaa-__---__-mmnka_-_-nkanka-__-ngoo-_--ndi_-_ndi---__-nee_-_---_-Ju_-_---_--ju_-_-maa🤣🤣🤣🤣🤣🤣🙌🙌
Koma ziliko😂😂
Lecturing Mr shokoshoko, malangizo abwino
Apa ndiye zilibwino mayi shokoshoko❤❤❤❤❤❤
Mdyangu ,mfumukadzi angochepetsa kuphunzitsa kulandana amuna/akadzi pakhomo.Izi zikulimbikisa uhule .anyway masewero anu ndiaboo
I like mlelemba family ❤❤❤
I like shokoshoko family
A prophet mulelemba kkkkk 😂😂😂
Banja la a Shokoshoko losinthasintha ngat nyengo 😂 Chiphwanya n Munyanyiwa nd 1 😂 n finally we have Mr n Mrs Chuma sopano 😂 Mulelemba m'busa wachinyengo
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂❤❤❤❤❤ l love it this comedy
Mayi Shokoshoko une kwanyadilatu kobasi kuti nyaduuu from Alexander (RSA)
All the way from GERMISTON SAKOMA SHOKO-SHOKO 🎉😂😂😂😂
Ineyo banja la a Shokoshoko limandiwanza nsaname😂😂😂😂😂😂
Koma shokoshoko ukunena zoona ndithu unalidi ku chimbuzi iweyo kkkkkkkk 😂😂😂😂
Koma chipwanya kkkkkkkkkkkk ayi guys mmakwana ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Excellent comedy 👏👏👏👏 guys you're the best , Mercy you're number one 😂😂😂😂
Am watching in south africa fire❤❤❤❤❤
Kodi okagula mapasi aja sanabwerebe kkk😂😂😂😂
❤koma mkazi shokoshoko eshiii please nipaseni cross mtima sulimmalo akumanipweteka kwambiri
Mercy your number 1
Mai shokoshoko mbambande bola mwayamba kuseka tsopano 😂
😂😂😂😂 koma chipwanya misomali 😂 mnyanyiwa mupase mbama chipwanya 😂
Mlelemba wachosa 5pn kwamfana ofoila
Koma chibwibwi mpaka kuimba likhwelu🤣🤣🤣
Kkkkk Mai shokoshoko koma ziliko eeeh
Ndi mwano wapangawo zizindikiro zopita ku toilet sindikuziona mwina ndi mmawa ching'axy the machine
Mlelemba waxotsapo 5pn mpaka!! Mneneri waxinyengo!!!
Amen watching in America koma mululemba mmmmm anakodza😂😂😂😂
Koma abale mnyanyiwa zimutengani abale😂😂😂 ndi chiphwanya
Chokochoko amafuna atachinda queen 😂😂😂😂
Mmmm chichewa chabwanji ichi
Mercy ndi chuma ayi ndakusililani ine 😂😂😂😂😂
Prophet mulemba nd one
Kwavuta ndikunyema ashokoshoko😅😅😅
Achita kutchekana kuno Mr Shokoshoko ndi mkazake😂😂😂😂😂
❤
Nice show ever
Mulelemba usazafe uzagosowa ndimakunyadira
Komatu mulelemba amaonjeza😂😂😂
Tionere zimenezi,team Nepman
Mercy tu wavutikila chuma 😂😂😂😂
Koma akaza mlelemba mimba imeneyi adzachila 🤣
Komatu Mercy amamutola Chuma 😂😂😂😂😂
Ching'aning'ani uja ndi chi master chomaliza 😅😅😅
Achuma nawoso kufika pa home 😂😂😂😂
Kkkkk km juu walawilatu
mercy wapata hug koyamba kulimbikira kumapidula osamafowoka
Ati thako lankhuku nyophilo 😂😂😂😂 koma mulelemba
😂😂😂 half mn wamutulukila mulelemba
Number one mdyangu
Mnyanyiwa mwana wanzako ndi steak😂
Mulelemba kkkkkk ndi 1
Anyamata inu mumayitha koma ine mayi chokochoko thako yoooo
Shokoshoko is a best
Nice movies
Koma ulendo uno ❤❤❤❤😂😂😂😂
Mlelembe the prophet wonama
Kkkkk junior yemweyo
Munyeliwa wamuonetsatu mzake mpakana tulo kikikikiki
Kkkkkkkkkkkk queen ndalamu ake
Banja la sasoka ndilokhalo lonjoya mu play iyiyi
Chipwanya it's the best kkkk 😂😂😂
Km chipwanya nsanje kkkk😂😂😂
kajuu ndikahule kobasi
Kma shoko shoko umumvesa kukoma mercy ndi hundred thousand
Amulelemba awoneka dolo kunyumba ND ndalama yopasidwa
Ching'aning'ani umandivetsa kukoma kwabwasi
Nepman am waiting 😂
Basi mwanayo ndiwa shokoshoko ndithu 😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂😂😂😂 mlelemba
Ine koma ulemu kwa mlelemba prophet wabodza kkkkkk umakwana ase
Pena ashoko shoko mumamuputa dala Cecilia ndani angapilire zimenezi munthu mulamu wake😂😂
Kkkkk km kumeneko
Shokoshoko amaziputa dala 😊😊😊
Shokoshoko it's the best
Mercy walifuna banja😂😂😂😂
Kkkkkk pastor more 🔥 🔥🔥🔥🔥 kkkkkkkkk
❤❤❤❤❤❤
Download ikukana zikut bwanji❤
Mayi shokoshoko mbambande
Kkkk amayi shokoshoko eti pano adzitolela🤣🤣
❤❤❤❤
Anthu azayamba kudelela🤣
Ilibwino kwambili guys more fire mabomba
kuminila kumwnwko queen
Mlelemba munthu osokoneza
Mumakwana inuy
😂😂😂😂munyanyiwa
Kuonera from Capetown
Chiphwanya 😂😂😂
Koma achiphwanya Ai ndthu koma ndaseka
Time?
Shokoshoko looks like Kondwani Chirwa
Kkkkkk chipwanya mmm
Mercy kuipatsa moto Ulemu ndiwofunika

All the way from GERMISTON SA
KOMA SHOKO-SHOKO 🎉😂😂😂😂

Mercy kuipatsa moto
Ulemu ndiwofunika