Phyzix - FOLLOW THE LEADER ft MC Kold (Official Video) 2011

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 12 сен 2024
  • FOLLOW PHYZIX ON SOCIAL MEDIA
    (All social media profiles are verified).
    Facebook: / phyzixmw
    X (Twitter): / phyzixmw
    Instagram: / phyzixmw
    Tik Tok: / phyzixmw
    Spotify: open.spotify.c...
    Apple Music: / phyzix
    Audiomack: www.audiomack.c...
    Don’t forget to SUBSCRIBE to be part of our community.

Комментарии • 24

  • @patrickmoyo6497
    @patrickmoyo6497 5 месяцев назад +1

    Right now amfumu this song is on repeat. Over 20times. My easter going on well. Marist days. Powerful

  • @Phyzix
    @Phyzix  Год назад +1

    *Follow the Leader Lyrics by Phyzix & MC Kold*
    *INTRO: MC Kold*
    Yeah/ oh oooh
    Oh oooh/ yeah/ oh ooooh
    *VERSE 1: Phyzix*
    Money Money Money/ I love money
    More especially zikhale many many many
    Ndimadana ndi maluzi/ zeni zeni
    Ndayikwiyila ndalama ndatenga mipeni
    Ndimadana ndi ma loss koma ma gain
    Ikakhala patali ndimatenga legeni
    Makwacha ma pound/ nthawi zina ma yeni
    On a new level fighting a new devil/ koma ndikupita cha mutu ngati eveil kaneivel
    Not a rebel/ just independent/ ndimapanga za ine ma man mundithaime/ Man Phyzo ndimadyelera aire
    *HOOK: Phyzix & MC Kold*
    Follow the Leader/ Follow the Cheddar
    Komwe kuli ndalama ndikomwe ndikupita
    Follow the Leader/ Follow the Cheddar
    Komwe kuli ndalama ndikomwe ndikupita
    Follow the Leader/ Follow the Cheddar
    I don’t see why ma man mukundida
    Despite the hating am still getting better
    Komwe kuli ndalama ndikomwe ndikupita
    *VERSE 2: Phyzix*
    I don’t really care/ olo ndili pansi
    Olo minibus bola ndikapeze dollar
    Komwe zabisalako ndikomwe ndikupita
    Zobweletsa ndalama ndi zomwe ndikuchita
    Ndikukula ndikuyenera kusanja/ nthawi yake ndi ino ndisanamange banja/ ine ndi wolimbikila dollar zindiyanja/ iwe siu riser ngati mwala mu nyanja/ daily pa nseu ndikumenya filimu/ wofuna kuthaimila mundipeza cinema/ kodi ndigule chani benz or a beamer/ ndiganiza bho ndikadyele kaye nsima
    *HOOK: Phyzix & MC Kold*
    Follow the Leader/ Follow the Cheddar
    Komwe kuli ndalama ndikomwe ndikupita
    Follow the Leader/ Follow the Cheddar
    Komwe kuli ndalama ndikomwe ndikupita
    Follow the Leader/ Follow the Cheddar
    I don’t see why ma man mukundida
    Despite the hating am still getting better
    Komwe kuli ndalama ndikomwe ndikupita
    *VERSE 3: Phyzix*
    Tsiku lililonse ndi lokazisaka dollar/ ndikazigwira ndimazikiyila mu khola/ kuzinenepetsa ndizazidya zikakula/ wa ku Bank kulemba cheque cha bulanki/ kopanga deposit ndimapita ndi bag/ sikuti ndi maluzi ndikamamwa chi bagi/ ndimafuna kukhuta pamene ndikuledzera/ zomwe ndimapanga ine simungazimvetse/ chinthu cha chimidzi ndimachibweretsa sexy/ I make money/ give away money/ sindimaphangila ndimadya ndi ma man/ let’s break bread tizigawana the money
    *HOOK: Phyzix & MC Kold*
    Follow the Leader/ Follow the Cheddar
    Komwe kuli ndalama ndikomwe ndikupita
    Follow the Leader/ Follow the Cheddar
    Komwe kuli ndalama ndikomwe ndikupita
    Follow the Leader/ Follow the Cheddar
    I don’t see why ma man mukundida
    Despite the hating am still getting better
    Komwe kuli ndalama ndikomwe ndikupita
    *OUTRO: MC Kold*
    Yeah/ oh oooh
    Oh oooh/ yeah/ oh ooooh
    Yeah/ oh oooh
    Oh oooh/ yeah/ oh ooooh

  • @velloxykaunga6446
    @velloxykaunga6446 2 года назад +5

    You have to re shoot this video,the song is too great for such visuals

  • @mphogiftmjuma4112
    @mphogiftmjuma4112 12 дней назад

    2024 September we still here

  • @lawrencetheu3343
    @lawrencetheu3343 11 месяцев назад

    I've been in love with this song ever since
    Reshoot it again please & i wish ndizaonekemo😅😅

  • @chifuniroadams
    @chifuniroadams 15 дней назад

    Hit iyiyi nayiloweza nd zizayimbira mafana anga❤

  • @preciouskaunda7162
    @preciouskaunda7162 Год назад +2

    Re Shoot the Video my Man..This is one of the greatest Rap songs of all time in Malawi. 🔥🔥

    • @Phyzix
      @Phyzix  Год назад +1

      Thanks man

    • @timbanda4614
      @timbanda4614 3 месяца назад

      @@Phyzix PLEASE SHOOT THE VIDEO AGAIN , THIS IS GHETTO ANTHEM

  • @williamrozario8922
    @williamrozario8922 Год назад +1

    Man phyzo , my favorite song

  • @danieldzimau5304
    @danieldzimau5304 11 месяцев назад +1

    Mountain Goat. Re shoot the video please the track still dope

    • @Phyzix
      @Phyzix  11 месяцев назад +1

      I like the idea

    • @danieldzimau5304
      @danieldzimau5304 9 месяцев назад

      Next tym will come to you physically . This track still one of my best

  • @francisdouglas4720
    @francisdouglas4720 Год назад +1

    Classic

  • @bamabeatz17
    @bamabeatz17 2 года назад +1

    my favorite songggggg ever

  • @paulzgamb6710
    @paulzgamb6710 Год назад

    Good song fizo

  • @Eastgatetutoring
    @Eastgatetutoring Год назад +1

    I remember when phyzix was once a ghetto king

  • @henrychiona8963
    @henrychiona8963 4 года назад

    Still wristening to this hit

  • @JoelSlus16
    @JoelSlus16 18 дней назад

    2026 anyone

  • @stanleynazombe5851
    @stanleynazombe5851 2 года назад

    Man phyzo iyiyinso munagwetsa

  • @manuelnamasani3606
    @manuelnamasani3606 2 года назад

    Iyiyi ase🐐

  • @jacrea1205
    @jacrea1205 3 года назад +1

    Pano munagura BMW wow

  • @abdhlahassani2032
    @abdhlahassani2032 4 года назад

    Never give up pano tili pa jhoz kuzasaka ndalama Mani🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🤸🤸🤸🤸💯phyzis ndiwamugettor