Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
It's very best of best Koma musamachedwetse kutulusa captain joxy
Komaso kafupika udyo
kutulusatu mukumachedwa plus ikufupika kwambili
Birthday party ya chule, instead of cake🎉 kkkkk. Ching'axy & Jokes ndinu Afiti ndithu
😂😂😂 koma yeah, zilibwino guys koma ikuchepa kwambiri than mene ankakhalira oyambilira aja
😅😅😅😅😅😅 Keke akutha kuno ndanyamata opandamano😅😅😅 osamachedwesa kutulusa anyuwanii
Komadi mr jokes tawonjezani ma minutes please ❤❤❤
Nice koma ikumafupika komaso idzituluka kawiri pa week
Jokes and ching'axy ana ovuta kulera🤣
Mukumachedwa kutulutsa komaso nthawi ikumachepa Mr Jokes
Maguys awa ndmadolo kwambilimbili 💥💥😂😂😂Km osamachedwa kutulusa
Can't wait to see that frog you were talking for 🤣 watching from DURBAN RSA , umakwana guys
Nthawi ikuchepa Mr Jokes
Out of people mr Ching'axy 😂😂😂😂😂😂 kma guys inuyo ndi one
Cake amadya chonchoooo kkkkkkk mwapha film yi anthuni,,, muziponya awir awiri
Jokes nd ching'axy simuzatheka 😂😂😂😂😂Keep the fire burning guys ❤
🤣🤣🤣😂 pa week muzitulutsa kawiri
Achin'gani ng'ani ndiye ana dalatu yawu get Man movie yiliyose
Watching from mwineriwa vg mulanje ❤
Greatest comedy but please you must try kutipatsa next episode mwachangu
Koma ching'aning'ani adha, ati koma ndiye shuga amamponyamo bwanji kkk
Kkkkkkk ufiti jokes muikemo chule😢😢😢
Malawi ndimwe ba Kali much love from Zambia
Kodi comedy iyi munasiya
Bt y it's so short mn
Still following... This is great
Koma sugar nde amamuponyamo bwanj😂😂😂😂😂
😂😂😂out pipo ..muchokepo apap...km ching'aning'ani
Kodi basi inatha ? Next please
Ma episode ako ukuchepesa kwambili ase uzitolele
😂😂😂😂 sindichapila makape ine iwe
ndaseka kale before watching🤣
Very nice koma ikuonjeza kufupika iiiiii
Good job.Koma nthawi ikumachepa.Can't you make ma episode wa 20 minutes?
Tikufuna part 2 please
Very nice,,Km kakufupika Inu
Akuona ngati tilibe ife mano akuona ngati ndife makape😂
Gayz mwaiponya patali koma onjezani kathawiko plz
Muli nyatwa guys koma ikufupika kwambiri kumafanana ndi nyimbo za nkasa paka
Eeee pa cake pokhapo ee mwakungapotu kkkkk❤
Very nice kma nthawi yachepa kwambiri
Kkkkkkkkkkk mumandisangalatsa kwambili 😂
mukuchedwetsa kwambiri
Ma guyz awa anaza😂😂😂
😂😂 ajokes kukana kumuchapila ex wako kkkk
Uku ndye kujaila sopano 😂😂😂😂😂😂
Kodi mwamaliza?? Kapena inafera kuchikangawa?
Mr jokes you one is so nice movies
😂😂😂 Boyz yadya cake.....
Am the first to watch
😂😂😂😂😂😂😂😂 Nanunso mwat muname apa
@@ManuelEndson-zr7hk serious am the first one 😀
Mr jokes and ching, axy 😅😅😂
Thawi yachepa kwambiri
That's so welcome to malawian people
Kd guys Ina yituluka liti tikudikiratu ife🧑🎤🧑🎤
Nyc one ma guy 🔥 following
Athu awa amatha
I wish you must do 20 minutes as well, ❤
It's too short eee
Outstanding 🔥🔥🔥
Ai zikomo Mr jokes keep it up
Koma jokes polamoto cake uja wapitabus Next plz guys 😊
Koma guys ikufupika kwambili muwonjezeleso ma minis please 🙏
Akeeee nde kuthera pobeba2 kkkkkk
🙆♀️🙆♀️🙆♀️hamayoo cake ya birthday ija kunooo😜😜😜🤣😂😅
Koma Mr joke's vs chinga,Ning,Ani mumakwana
Mukuidula kwambili km
10 mins ikumachepa guys
Next please
🤣🤣🤣🤣🤣 koma anthu ena aaaah hahahahaha
Mr Jokes mumakwanila and Ching'aning'ani pitilizani
Muli nyatwa guys
Kom suger akumachulusa😂😂😂😂😂
Kodi sizingatheke mudzitulutsa after ma days ochepa? mukumachedwatu kutulutsa ina ma Bigy, changu inayo tikudikira
At tiko fewa😂😂
😂😂🤣🤣🤣 maguyz wa ndi madolo
Koma nthawi onjezeran
Achikulire tikudikira episode 15
Koma mukufupikitsa kwambili gayz
Zili bwino pamenepo
Mutat muzipangako 20mn at least
Akuona ngt kutha Mano kwathuku ngat tilibe nzeru
Make it 30 minutes
Next please😂
Ka week ino kachepatu aa
Too short
Waiting episode 15
Good ❤❤
Tikuonela kuno ku chileka
Nthawi Koma ikuchepatu kwambili
Mbambande
kkkkkkk kma gys munadza
Koma akumachedwetsa kutulusa
Chule azangolumpha bs 😂😂😂😂
Mmmmmm mmmmm cake choncho guys kkkkkkk
🔥🔥
Koma matokwana akhwaka
Ikumachepnso gyz
Awoneseni azimayiwo.tikudikila ina pano
Komatu ikumafupika kwambili wonjezelani ma minutes
Koma kumpandauku🙌
Km Chi ng'axy
😂😂😂 mumakwana
Tikudikira chule birthday
Movie on guys
It's very best of best
Koma musamachedwetse kutulusa captain joxy
Komaso kafupika udyo
kutulusatu mukumachedwa plus ikufupika kwambili
Birthday party ya chule, instead of cake🎉 kkkkk. Ching'axy & Jokes ndinu Afiti ndithu
😂😂😂 koma yeah, zilibwino guys koma ikuchepa kwambiri than mene ankakhalira oyambilira aja
😅😅😅😅😅😅 Keke akutha kuno ndanyamata opandamano😅😅😅 osamachedwesa kutulusa anyuwanii
Komadi mr jokes tawonjezani ma minutes please ❤❤❤
Nice koma ikumafupika komaso idzituluka kawiri pa week
Jokes and ching'axy ana ovuta kulera🤣
Mukumachedwa kutulutsa komaso nthawi ikumachepa Mr Jokes
Maguys awa ndmadolo kwambilimbili 💥💥😂😂😂Km osamachedwa kutulusa
Can't wait to see that frog you were talking for 🤣 watching from DURBAN RSA , umakwana guys
Nthawi ikuchepa Mr Jokes
Out of people mr Ching'axy 😂😂😂😂😂😂 kma guys inuyo ndi one
Cake amadya chonchoooo kkkkkkk mwapha film yi anthuni,,, muziponya awir awiri
Jokes nd ching'axy simuzatheka 😂😂😂😂😂
Keep the fire burning guys ❤
🤣🤣🤣😂 pa week muzitulutsa kawiri
Achin'gani ng'ani ndiye ana dalatu yawu get Man movie yiliyose
Watching from mwineriwa vg mulanje ❤
Greatest comedy but please you must try kutipatsa next episode mwachangu
Koma ching'aning'ani adha, ati koma ndiye shuga amamponyamo bwanji kkk
Kkkkkkk ufiti jokes muikemo chule😢😢😢
Malawi ndimwe ba Kali much love from Zambia
Kodi comedy iyi munasiya
Bt y it's so short mn
Still following... This is great
Koma sugar nde amamuponyamo bwanj😂😂😂😂😂
😂😂😂out pipo ..muchokepo apap...km ching'aning'ani
Kodi basi inatha ? Next please
Ma episode ako ukuchepesa kwambili ase uzitolele
😂😂😂😂 sindichapila makape ine iwe
ndaseka kale before watching🤣
Very nice koma ikuonjeza kufupika iiiiii
Good job.Koma nthawi ikumachepa.Can't you make ma episode wa 20 minutes?
Tikufuna part 2 please
Very nice,,
Km kakufupika Inu
Akuona ngati tilibe ife mano akuona ngati ndife makape😂
Gayz mwaiponya patali koma onjezani kathawiko plz
Muli nyatwa guys koma ikufupika kwambiri kumafanana ndi nyimbo za nkasa paka
Eeee pa cake pokhapo ee mwakungapotu kkkkk❤
Very nice kma nthawi yachepa kwambiri
Kkkkkkkkkkk mumandisangalatsa kwambili 😂
mukuchedwetsa kwambiri
Ma guyz awa anaza😂😂😂
😂😂 ajokes kukana kumuchapila ex wako kkkk
Uku ndye kujaila sopano 😂😂😂😂😂😂
Kodi mwamaliza?? Kapena inafera kuchikangawa?
Mr jokes you one is so nice movies
😂😂😂 Boyz yadya cake.....
Am the first to watch
😂😂😂😂😂😂😂😂 Nanunso mwat muname apa
@@ManuelEndson-zr7hk serious am the first one 😀
Mr jokes and ching, axy 😅😅😂
Thawi yachepa kwambiri
That's so welcome to malawian people
Kd guys Ina yituluka liti tikudikiratu ife🧑🎤🧑🎤
Nyc one ma guy 🔥 following
Athu awa amatha
I wish you must do 20 minutes as well, ❤
It's too short eee
Outstanding 🔥🔥🔥
Ai zikomo Mr jokes keep it up
Koma jokes polamoto cake uja wapitabus
Next plz guys 😊