Amen Amen songs of salvation in our generation to God be Glory. Nyimboyi ikusunthila moyo wanga kwakuya ndikutha kuwona chisomo chachikulu pamoyo wanga mwa ambuye wathu Yesu mpulumutsi anyamata ntchito mwayigwila yotamandika mulungu azikudalitsani
Malawi music penaso simumatha ndisaname nyimbo izi ndinayamba kuufuna kuchokela 2019 kumayambililo mpakana lero ndilipo mwe mukuipanga upload siziona chimavuta ndichani nthawi yomwe nyimbo ili mu chat nthawi yomwe ndikuipanga upload kuti anthu aipange download azivile ndi kuonela awo ndimaganizo anga chabe chomwe chimavuta inuyo mukuchiziwa basi koma chomwe ndingalipemphe ndi nyimbo ya undilonderaji saulo aise plz tapangani imeneyo andidalitsa kwambiri or ngati zitatheka tumani Album yonse
mukuyimba bwino koma stop behaving like The Great Angels choir because they dance nanga achikunja...they dress into stunning dresses to show off the fresh...Please don't follow them...chifukwa alandiliratu kale photo yawo...mpaseni Ulemu Mulungu...
Beautiful message. Continue preaching brethren. I feel blessed. Albert Mtungambera, Mzuni.
Amen Amen songs of salvation in our generation to God be Glory. Nyimboyi ikusunthila moyo wanga kwakuya ndikutha kuwona chisomo chachikulu pamoyo wanga mwa ambuye wathu Yesu mpulumutsi anyamata ntchito mwayigwila yotamandika mulungu azikudalitsani
Zooonad
Amen powerful song❤
Good gospel music imandisisimusa
This song is good and I like it most, keep it up guys, may God bless
❤❤ mumatiimilila ambuye achite momwe akufunila ndimoyo wanu
nice one mbayani amanditenga moyo 5:27
apa mwabwera guys keep on moving, muli boh apa 99.999% basi 100% ya MULUNGU yekha
Pakanapanda Mbuye palibe wina akanatifela Amen
Congrats I feel like I'm at Malawi continue to bless us in the name of God
Ambuye akubalisseni noseno
I'm going to pay avisit to Malawi hoping to meet God's ministers 💃💃🤸🤸🤸🤸💃💃🙌🙌🙌🙏🏻🙏🏻🙏🏻
Amen amen
Mumakwana guys keep on
One of the best hits. Full of theology
Gosto muito dessa
Pakanapanda mbuye kutifera mndani akanatifera adazuzika chifukwa chamachimo athu tiyeni abale tizikumbukila zowawa zomwe anakumana nazo tikamachimwa timakhala tikutsutsula mabala ake ambuye atichile chidundo
Thank you very much may GOD BLESS YOU
That's great message 🙏🙏🙏
Padakapanda mbuye ndinali yani ine amen🙏🙏
Amen 👏👏
Nice
Eish Malawi is God fearing country i love it Ooo father bless my mother land and his people. See us through in Jesus name.God bless you all
zoonadi panakapanda Mbuye Yeah Kristu panalibe wina. A bale amathawadi
Pitilizani kunditumikira.
Amen ❤
Yooh Guys I still remember the days I was in Malawi God bless you 🙇♀️🙇♀️🙇♀️🙇♀️
We hope to see you again thank you for listening .
Mumatha ndakunyadirani
Amen
Eeeish Guyz Mulungu apitilize kukutsekuliran makomo azisomo mumadyetsa moyo wathu wauzimu mwapaderadera 💃💃🎵🎶📣🎼🎤
Nice music mmmmm
Tokuguritsa maredmi 4x mahonor mahuawei patengo wabooo
mbayani
esta bem da para assistir
Nice music... Undilondelanji saul plz...
Natumiza komatu
❤
🙏🙏🙏🙏
Thanks
amen
Amen
Nyimbo yabwino.
Saulos msofi
muchepetse...kugwedeza chuno..mzochokera kwa satana
abwana anga anasowa awo pano atsogolera mwamphamvutu
Limbikiran zikuthk
Uthenga wabwino
Moyo
Ndimadalisika ndi nyimbo zimenezi
Malawi music penaso simumatha ndisaname nyimbo izi ndinayamba kuufuna kuchokela 2019 kumayambililo mpakana lero ndilipo mwe mukuipanga upload siziona chimavuta ndichani nthawi yomwe nyimbo ili mu chat nthawi yomwe ndikuipanga upload kuti anthu aipange download azivile ndi kuonela awo ndimaganizo anga chabe chomwe chimavuta inuyo mukuchiziwa basi koma chomwe ndingalipemphe ndi nyimbo ya undilonderaji saulo aise plz tapangani imeneyo andidalitsa kwambiri or ngati zitatheka tumani Album yonse
Will try to do so in near future we really appreciate your concern thank you
Mukuyimba bobo gys
mukuyimba bwino koma stop behaving like The Great Angels choir because they dance nanga achikunja...they dress into stunning dresses to show off the fresh...Please don't follow them...chifukwa alandiliratu kale photo yawo...mpaseni Ulemu Mulungu...
Amen
anthu amulungu inu ndisaname nyimbo zanu zindisangalasa makamaka nyimbo yoti akanapanda mbuye ija imadisuntha
Amen