JOSEPH MKASA KACHIKENA KU CONVENTION YA MCP

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 30 ноя 2024

Комментарии • 126

  • @timothyganizani6541
    @timothyganizani6541 3 месяца назад +2

    Mkasa kufika poyamikira ndiye kuti ziribwino👍

  • @ShuaibuBanda-g6v
    @ShuaibuBanda-g6v 3 месяца назад +1

    Big up big chakwela 2030 woooooooo

  • @DuncanThambala
    @DuncanThambala 3 месяца назад +5

    Mkasa zowonad kuyimba nyimbo yoyamikira munthu wakuphayu Chakwera, ah ndiwe wosapanganika wandikhumudwitsa

  • @CosmasChikwindi
    @CosmasChikwindi 3 месяца назад +6

    Zotinyozera oimba ayi zithe guys, oimba alingati wailesi amagulisa uthenga ulionse omwe ungawapeze and nkhani ndindalama so please musamude Nkasa please

    • @TakondwaSaidi
      @TakondwaSaidi 3 месяца назад

      Kd nawe ndani waimbira kut😂😂nawe

    • @EdwardZuze-r7w
      @EdwardZuze-r7w 3 месяца назад

      Zomwe akupanga kaya ndi makobili akundikhumudwitsa kwambiri, ndipo aaaaa oyomba inu musamangoyamikira ndi zolakwika zomwe,
      tamadzudzulani zolakwika zomwe zili mu dziko muno.

  • @GeraldKapalamula-e1u
    @GeraldKapalamula-e1u 3 месяца назад +4

    Nyimbo ya bwino ,yopatsa chilimbikitso, mumatha Mr mkasa👍👍👍

  • @ApocheC.
    @ApocheC. 3 месяца назад

    😂😂😂😂😂 Nkasa ndi mbuzi wandikhumudwisa 🙌🙌

    • @ApocheC.
      @ApocheC. 3 месяца назад

      nyimboyi zoti ndi Nkasa sindikukhulupilira

  • @EzekielZulu-c9c
    @EzekielZulu-c9c 3 месяца назад

    I like your confidence veterans from my childwood

  • @DixonChimanya
    @DixonChimanya 3 месяца назад +6

    Nkasa wadya chibazi
    Ndiye ndiwe kampetu

  • @ShuaibuBanda-g6v
    @ShuaibuBanda-g6v 3 месяца назад

    He just say what is on ground big up chakwela

  • @DavyChirwa-k9x
    @DavyChirwa-k9x 3 месяца назад +1

    😢koma nde padafupidwatu..

  • @JustinWodala-d6p
    @JustinWodala-d6p 3 месяца назад +4

    Ndiwe chisiru kwabwsi mkansa kaya kusapita ku school kaya

    • @MercyChimaliro-fi6mv
      @MercyChimaliro-fi6mv 3 месяца назад

      Kkkkkkkkk

    • @EdwardZuze-r7w
      @EdwardZuze-r7w 3 месяца назад

      @@MercyChimaliro-fi6mv Komaditu apa ndiye akuonetsa umbuli.
      dpp, anali komweko, pano ndi wa MCP, iazabwera ena, azadumphila kumeneko, kupoila

  • @monicagondwe228
    @monicagondwe228 3 месяца назад +3

    Panga zomwezo umadyera mommo mphwanga 😂

  • @JUSTINMOKELI
    @JUSTINMOKELI 3 месяца назад +4

    Mkasa dyela ndilomwe lachuluka ndikukumbuka unayimbatu nyimbo yomwe athu anatsitsira mpweya dziko la 🇲🇼

  • @Kamatuwajr
    @Kamatuwajr 3 месяца назад

    Chikachepa Ponya Mkamwa Akakhala Galu Kuyang'ana Ndikwake😂😂

  • @KingfrahMachado
    @KingfrahMachado 3 месяца назад +2

    Munthu wadyela galu kwabas nang Chakwela wakoyo ndindani nonse matako amakolo anu Chikangawa 😅😅😅😅😅😅

  • @MayesoKulea-sh8xd
    @MayesoKulea-sh8xd 3 месяца назад

    Nkasa kuswa kuswa 🔥❤️ nice song 💗

  • @CassimMbalaka
    @CassimMbalaka 3 месяца назад +6

    Woyimba wopanda tsogolo kape uyu

  • @ChristopherSekantole
    @ChristopherSekantole 3 месяца назад

    Ndiomeo, Ndiomeo!!!! Ndiye angasiye kukuntha choncho. Umaimbira amene amatuluka muboma

  • @yasitafuphiri-nw2he
    @yasitafuphiri-nw2he 3 месяца назад +1

    Kudya zamuzinda mkuchenjera ,mkasa apa waing'alulatu😂😂😂

  • @MzikaPhiri
    @MzikaPhiri 3 месяца назад

    Nyimbo yasowa DJ ingoika Yoswa ndi Muthalika basi kkkkkk

  • @MarkMailosi
    @MarkMailosi 3 месяца назад +2

    Mkasa iyeyo bolatu zilowe 😅

  • @williamsalexmbonga
    @williamsalexmbonga 3 месяца назад

    Boma ndilomweli nthuni zinazo zikuchedwetsani chabe Dr Laz M Chakwela anabwela kudzakhala

  • @charleslimbani8590
    @charleslimbani8590 3 месяца назад

    Umadyera momooo palibe angakuuzee wayiziii......wina akutukwana koma iweyo zako zalowaaa ndaziona akukupatsa pa manjaaa 😂😂😂

  • @chesterphiri7523
    @chesterphiri7523 3 месяца назад +1

    Mkasa tsopano 😂😂😂😂

  • @MaryTchapo-py4hh
    @MaryTchapo-py4hh 3 месяца назад +2

    Chitukuko chake chit?bola akupatse ndalamazo

  • @masianobrighton
    @masianobrighton 3 месяца назад

    Kaya wina afune wina asafune mtsinje umapita kotsetseleka inu ngati simukuona ubwino wa boma ili khalani ku udani konko
    Anthu anapha njanji kuti sigula ma truck azipangira business ya transport kugulisa ma kampani aboma kuti atsegule awo
    Kutenga Malawi ngati mgodi wao ndiye uyu akubwezeresa zithu kwa eni ake amalawi
    Miseu kumangopanga yosalimba cholinga chaka chilichonse azigwiramo ntchito azilemera okha taonani miseu yomwe aika ma slab pamenepo atambalali omanga zosalimba mungakondwe naye? Nyumba za police zasopano pomwe ena amangomanga papepala iyaaa tiyeni tizionanso munthu saipa zonse koma zabwino tizinena miseu yolimba ma bridge ndiye mukufuna chanino

  • @LewisSimfukwe-kw2mn
    @LewisSimfukwe-kw2mn 3 месяца назад

    Nkasa al8be vuto! Ngati anamupanga hire he has to do the best kuti awese yambiri! Oimba ali ngat ma lawyer, can be hired like a tax kaya mupita ndi mkazi ku lodge or konyamula katundu wakuba they dont mind

  • @RitaBan-t7c
    @RitaBan-t7c 3 месяца назад

    Mukalandira mukawamangile amai anu aja nyumba paja munazolowera kudya zopatsidwa zakuba usiku wa bhooo

  • @MaryTchapo-py4hh
    @MaryTchapo-py4hh 3 месяца назад +2

    Nyau singasowe uku

  • @stephenkbanda598
    @stephenkbanda598 3 месяца назад

    🤣🤣🤣 ine chiphwete kkkkk

  • @masianobrighton
    @masianobrighton 3 месяца назад

    Ndale sitichitira pa social media ndale ndi pa ground adyera onse achoke kumipandoko kubwere ma servant munthu ikakhala nyumba momwe muli moto mpomwe umaziwa chomwe chayatsa Motowo koma ukakhala kunja umangona utsi basi

  • @EdwardZuze-r7w
    @EdwardZuze-r7w 3 месяца назад

    Komatu muyaluka nazo izi, osamangodya makobili omwe munapangawo ndi ma banja anu bwanji, za ndale abwere uyu muli konko, akadzabweranso uyo, mukapedzeka mukuymba nyimbo kumeneko zochemelera ndi zopoila zomwe

  • @Dinalamakanjira
    @Dinalamakanjira 3 месяца назад +7

    Ichi ndi chitsilu

  • @KenChitete-pg3ws
    @KenChitete-pg3ws 3 месяца назад

    Joseph nkasa ndi wathayimingi kwambili akuonela patali,,akudziwa chipani chowina masakho a 2025 MCP ndiyimene idza wine

  • @JulietKapata
    @JulietKapata 3 месяца назад

    Eyadi ntchito zabwinod zomwe akugwira zokupha😢😢

  • @JoelMwenegamba
    @JoelMwenegamba 3 месяца назад

    Ife mutiyikile nyimbo ya yosha ufumu ukuyenera.

  • @ShukuraniTonex
    @ShukuraniTonex 3 месяца назад +1

    Koma mkasa 😅😅😅😅😅😅

  • @YusufJames-f5f
    @YusufJames-f5f 3 месяца назад +1

    Ndalama ndiopsa

  • @LikangaManuel-sk8yp
    @LikangaManuel-sk8yp 3 месяца назад

    Nyawu kaye kunyada koma utangopwasamuka nganyadile bwanji

  • @khadjahmustafa365
    @khadjahmustafa365 3 месяца назад

    😂😂😂😂😂 makanja zikuvuta kumufupa kwaje

  • @chipilirolackson530
    @chipilirolackson530 3 месяца назад

    talented

  • @juliochiwalo
    @juliochiwalo 3 месяца назад +1

    Nkasa idya nao ndalama za magazizo mbale thesa umphawi wako

  • @DavieChiwale
    @DavieChiwale 3 месяца назад

    Nkasa Joseph ndi we chitsiru mphawi galu wachabechabe ngati iwe

  • @AubreyChiyaya-ty8ge
    @AubreyChiyaya-ty8ge 3 месяца назад

    Uphawi ukukupangitsa uchitsilu mkasa

  • @MadalitsoMagalasi
    @MadalitsoMagalasi 3 месяца назад

    Kmatu Mkasa umaimba eeeeeeeee

  • @VenançioZocueza
    @VenançioZocueza 3 месяца назад

    Gwape iwe dyera lako silingapulumutse malawi.

  • @ThokiezMw
    @ThokiezMw 3 месяца назад +3

    Mkasa ulibe mantha kwa tcheya uli komko 😂

  • @KapundaVictor
    @KapundaVictor 3 месяца назад

    Gule

  • @DesireMjojo
    @DesireMjojo 3 месяца назад

    Uyimbenso ija yokuti ,azimayi kuvulidwa mahafu Panja kuja komesa hall.

  • @EnerstManess
    @EnerstManess 3 месяца назад +3

    Nkaza mboloyako wava

  • @LAKISSONEBINGOLOSSEMACUNHA
    @LAKISSONEBINGOLOSSEMACUNHA 3 месяца назад

    Nthawi yakwana Ndalama zikhweke

  • @JessicaPerry-u1q
    @JessicaPerry-u1q 3 месяца назад

    Lewis Christopher Martinez Kevin Jackson Larry

  • @thumbikokaira6743
    @thumbikokaira6743 3 месяца назад +1

    nyimbo iyi wapha 🔥🔥🔥🔥🔥

  • @jomochirwa
    @jomochirwa 3 месяца назад

    Komatu mkasa munthu uyu mulungu adamudalitsatu nzeru zopeka nyimbo.

  • @FunnyKalimwayi
    @FunnyKalimwayi 3 месяца назад +1

    kukamwa kwa madam ngati akunyela

    • @finchiadriano
      @finchiadriano 3 месяца назад

      Ulindi lawyer, kapena ulibe

    • @MangulenjeTwangu
      @MangulenjeTwangu 3 месяца назад

      Kayatu fusen ameneyo

    • @GiftKumbweza
      @GiftKumbweza 3 месяца назад

      Olo chidanicho,ukanyoze mayi wamkulu ngati ameneyo.Zina kumachitako manyazi ai😮

    • @williamsalexmbonga
      @williamsalexmbonga 3 месяца назад

      Tigaileni picture ya makolo anu big tiwaoneko

  • @MarriamBakalie
    @MarriamBakalie 3 месяца назад +1

    Ulemu wanu bwana nkasa podyela sitisankha 😂😂 aiwala mwano wako tiye nawoo 😂😂😂kma abale MCP muli makape eti

  • @LAKISSONEBINGOLOSSEMACUNHA
    @LAKISSONEBINGOLOSSEMACUNHA 3 месяца назад

    Oyimba ndi hule

  • @francismungu7749
    @francismungu7749 3 месяца назад

    Ayi guys umphawi siwabwino. Ampasa zake mkasa zili pabwino. Koma osaiwala mawa

  • @KenChitete-pg3ws
    @KenChitete-pg3ws 3 месяца назад

    Chibanzi nchofinika aliyense amalemela ndi chibanzicho

  • @JorgeSacuate
    @JorgeSacuate 3 месяца назад

    Paliso oyimba ena ndi zitsiru. Malo mopita kukapepha ndalama Kwa Satanic chakwera akufuna ayambe watiyika ife athu pamoto Kaya. Joseph mkasa utukanisa Makolo ako ndi abale ako. Chitsiru iwe tiwonana 2025. Uzathawira ziko Lina iwe

  • @PaxNkhomaPaul
    @PaxNkhomaPaul 3 месяца назад

    Koma yah. Kufunika kadema kaja uyu

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg 3 месяца назад

    Komatu Mkasa dyera lizakuphesa

  • @BLazymusicproduction-ee6ec
    @BLazymusicproduction-ee6ec 2 месяца назад

    Chakwera 2025 awinanso
    Ufune usafune mcp boma

  • @TRIPLE-w1s
    @TRIPLE-w1s 3 месяца назад

    Kasa ndiwe opusa kwambili

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 3 месяца назад

    Watha bas 😂😂😂😂😂

  • @SalatielMgadamika-i9m
    @SalatielMgadamika-i9m 3 месяца назад

    ADPP ndinu zitsilu komaso ndinu malova ambili ofunika ukupatsani madzi kuti musambe mmaso chifukwA mwina muli mtulo simukuchiwona chitukuko chahcakwela

  • @Okalekale
    @Okalekale 3 месяца назад

    Onse amene m'matinChakwera anapha Chilima fotokozani tsatane tsatane kuti anapanga bwanji chifukwa sindinvetsetsa kuti ngati anaphedwa,anaphedwa bwanji,sinditha kulumikiza bwino-bwino,mwina sinditha kuganiza ndi ine.Kapena anapangana ndi pilot?,ndiye pilot yo anali wa suicide,kupha Chilima ndi ena onse pamodzi iye yemwe?.Tatiuzeniko anthu anzeru zawo kuti anawapha bwanji anthu aja?.Ndikaonetsetsa imfa iyi ndiyosiyana ndi m'mene anaphedwela anthu ndi boma ma boma a zipani zina,zimachita kudziwikilatu kuti aphedwa ndi boma.

  • @PaulChaleka-lb4vx
    @PaulChaleka-lb4vx 3 месяца назад

    A Malawi kumangoombera manja zilizonse

  • @MaxonKambazithe
    @MaxonKambazithe 3 месяца назад

    Nkasa ndiwe mfiti uziona galu wamunthu uzingodya ndalamazo

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 3 месяца назад

    Nkasa ndiwe galu kwambili umbuli ndimavutodi

  • @AlufeyoBanda-cv2we
    @AlufeyoBanda-cv2we 3 месяца назад

    Uyu ndi oimbatu akuyenera kudyera pakamwa basi zandale sizikumukhudza ndiye osamunyoza iyayi

  • @ShamilahSaizi
    @ShamilahSaizi 3 месяца назад +1

    Chizereza chimunthu ichi

    • @fannyzimba149
      @fannyzimba149 3 месяца назад

      Kkkkk chindere ichi wanthu njala ili thooo uyu ninyimbwa

  • @VitumbikoKumwenda-sd1uo
    @VitumbikoKumwenda-sd1uo 3 месяца назад

    Nkasa ndi munthu wadyera

  • @EnipherAyami
    @EnipherAyami 3 месяца назад +1

    Koma chimenechi ndichitsiru

  • @FrancisKatunga-u5f
    @FrancisKatunga-u5f 3 месяца назад

    nanuso network ku tripah kkkkkkkk

  • @KylaAdams-m5c
    @KylaAdams-m5c 3 месяца назад

    Muvotelana nokha mmene mukudyela ndalama zanthu za tax

  • @DesmondTaulaye
    @DesmondTaulaye 3 месяца назад

    Simupanga post zithu molongosoka zimangojama

  • @MosesMillionnkhoma
    @MosesMillionnkhoma 3 месяца назад

    Mpaka mbunda😂

  • @LikangaManuel-sk8yp
    @LikangaManuel-sk8yp 3 месяца назад

    Uyu wadyela galu kwabasi

  • @tamalangoma2765
    @tamalangoma2765 3 месяца назад

    That background tune is so annoying @makosana

  • @JafaliAjusa-zg2xi
    @JafaliAjusa-zg2xi 3 месяца назад

    Kupempha chikulu achisilu

  • @MangulenjeTwangu
    @MangulenjeTwangu 3 месяца назад

    Bola ndalama bas

  • @ColetteMalunga
    @ColetteMalunga 3 месяца назад

    Politics, dirty game . Nyau mu hall 😂

  • @VioletChandire
    @VioletChandire 3 месяца назад

    Vuto ndi umphawii

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo 3 месяца назад

    Wadya manyi

  • @AfickGeorge
    @AfickGeorge 3 месяца назад +1

    Nkasa ndiwe chibakha

  • @GeoffreyKatsache
    @GeoffreyKatsache 3 месяца назад

    Chitsiru inchi man

  • @TRIPLE-w1s
    @TRIPLE-w1s 3 месяца назад

    Zopisa

  • @Jasper-xk9iv
    @Jasper-xk9iv 3 месяца назад

    Koma nkasa udzafa choima

  • @JustinWodala-d6p
    @JustinWodala-d6p 3 месяца назад

    Joseph mkansa uzafa ngat galu

  • @luciarashid1961
    @luciarashid1961 3 месяца назад

    😢😢

  • @martinjonam8237
    @martinjonam8237 3 месяца назад

    Komatu amadya zaketu

  • @ShalifuKachigwe
    @ShalifuKachigwe 3 месяца назад

    Uzathera manja iwe

  • @TakondwaSaidi
    @TakondwaSaidi 3 месяца назад

    zamanyazi mkasa

  • @moseskavalo3304
    @moseskavalo3304 3 месяца назад

    Chakwera be careful, you are not surrounded by good people

  • @FlechaChipeta
    @FlechaChipeta 3 месяца назад

    Kasa panyopako mbuzi iwe

  • @finchiadriano
    @finchiadriano 3 месяца назад

    Mkasa wagogoda nyimbo yomalizilayo

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo 3 месяца назад

    Panyapake galuyu

  • @MWAZANGATIPATRICKPAUL
    @MWAZANGATIPATRICKPAUL 3 месяца назад

    umphawa umapatsa uchitsiru

  • @MusheyCassimuCassimu
    @MusheyCassimuCassimu 3 месяца назад

    Nkasa pamtumbo