MBIRI ZA ANTHU OMWE ALUZA ZISANKHO🤔

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 9 сен 2024

Комментарии • 230

  • @jogechawa6192
    @jogechawa6192 Месяц назад +11

    Mumba is the future president

    • @Extratremendouszeus
      @Extratremendouszeus Месяц назад +2

      Waku MCP kwanu konkotu...osat dziko...ndiyamba awareness campaign kut anthu atsate zimenez😊

    • @stanleyzakeyo3138
      @stanleyzakeyo3138 Месяц назад

      ​@@Extratremendouszeuspp

    • @stanleyzakeyo3138
      @stanleyzakeyo3138 Месяц назад +1

    • @Okalekale
      @Okalekale Месяц назад

      ​​​@@ExtratremendouszeusTiyipatse mpata MCP or UTM,dziko zinaliononga mbava ndi okupha a UDF,DPP ndi PP,manyaka azipani,chomwe amadziwa ndikugawa dziko ndi kuba basi.Tinawayesa analephela mpaka kumaba ma votes,ngati akuba ma votes akukatani m'boma?,akukabansotu.Chitsiru cha nzika chokha,chimene sichimakonda dziko lake ndi chimene chingabweleze kuvotelanso mbava ndi ma murderers a DPP,UDF ndi PP.Maka maka uyu akumuti a dad uyu,ameneyi ndiye politician woyipa kwambiri,anangophunzira koma kuyendetsa dziko satha or pang'ono mapeto ake akupanga ndale zogawa anthu,mbuli yophunzira.Akuganiza or titagawana dziko alomwewo adzakhala ndi dziko lalikulu bwanji?.Bingu anali machine osati m'bale wakeyi,uyu ndi manyaka.

  • @GiftMathewe-fr3kn
    @GiftMathewe-fr3kn Месяц назад +15

    Ndichifukwa amati voti ndi muntima osadabwa ndimene zizakhalile 2025

    • @user-rz9rm4cb8x
      @user-rz9rm4cb8x Месяц назад +1

      Musiyeni chikangawa aziwona chaka chamawa ndalama akuononga zija azazkumbukila

  • @samchibenene4458
    @samchibenene4458 Месяц назад +5

    Well done zikhare Ng,oma you deserve what looking for 😂😂😂😂😂

  • @DolothyMussa
    @DolothyMussa Месяц назад +13

    Ndalama tizilandila koma vote ili mu mtima ndipo mcp sitikuyifuna mapeto ake tizazuzisa ana anthu sogolo

    • @EnockRabson
      @EnockRabson Месяц назад +1

      Awuzen aChing'omawo

    • @IshuBillalli
      @IshuBillalli Месяц назад +1

      Ndalama samakana koma kulandira koma povotapo ukuziwa wekha

    • @user-ol1hf7ru1v
      @user-ol1hf7ru1v Месяц назад +1

      Kwabasi

    • @JacobMalakini
      @JacobMalakini Месяц назад

      mufuna chan inu dpp nde yoola muti mulowela kuti kkkk zipani zosezo mesa zachoka ku mcp kholo lanu mukunama inu dziko si la dpp khalamba zikapume

  • @MaryChavula-jz3di
    @MaryChavula-jz3di Месяц назад +6

    Ndizomwe zitachitike 2025 mcp paulendo ndalama tidzilandila koma voti tilinayo kale feteleza otsikantengo ndiye voti yathui amalawi

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 Месяц назад +4

    Congratulations to mr zikhale ng'oma for the good race 😂😂😂

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 Месяц назад +13

    Koma Mumba congrants

  • @douglaskabekele7743
    @douglaskabekele7743 Месяц назад +4

    Chala Cha mulungu chikaloza wina sangachotse ..
    Congratulations all winners !!
    But please mumvetsetse kwambiri pewani zoyipa zomwe amapanga anzanu zomwe zakambidwa apa zimene zawapangitsa kuti lero agwe !!
    Mulungu sachedwa..safulumila..
    Once again congratulations all winners put your heaven God patsogolo..Amen

  • @Frederick-s4h
    @Frederick-s4h Месяц назад +5

    Mwaonatu Amcp zomwe zachitikazi bakilimuluzi tv yagwila tchito pasosho midia yatsegula m'maso athu ambili

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du Месяц назад +8

    Kunkuyu akanayesa mahule mwina akanawina sipaja iyeyo kunkuyu ndi hule mpaka kupha witika

    • @AllanChabwela
      @AllanChabwela Месяц назад

      😂😂😂

    • @spargomw
      @spargomw Месяц назад

      Kkkkkkkkkkkkkkk Koma ndaseka iiiiiiiiiiii anthu mumazama poganiza😂😂

    • @GloriaKaduya
      @GloriaKaduya Месяц назад

      Kodi nkhani zimene zija zinatha bwanji

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du Месяц назад +11

    Amkaka ndale dza usiku dzayenda bwanji😂😂😂

  • @Frederick-s4h
    @Frederick-s4h Месяц назад +4

    Mutengele phuzilo apapa amcp kuti 2025 mulipangozi yoopswa zd

    • @IshuBillalli
      @IshuBillalli Месяц назад

      Mwauze akhale osamala kwambiri chifukwa nthawi yoti angakonze zinthu yapita

  • @user-mi1fs2lv1h
    @user-mi1fs2lv1h Месяц назад +4

    Chakwera ayembekezelenso zonga izizi 2025
    Za muntima nzawekha

  • @kenmadan5350
    @kenmadan5350 Месяц назад +2

    A politician should be humble and reachable

  • @HawaSabit
    @HawaSabit Месяц назад +6

    Zoonad ndalama ndi khalidwe ziwiri zosiyana

  • @isaihmagani5697
    @isaihmagani5697 Месяц назад +5

    Congratulations Mkaka ku zikonda

  • @issahmmateyuh9817
    @issahmmateyuh9817 Месяц назад +4

    Zikhale ng'oma wachita bwino mbiri yambwino iposa chuma

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms Месяц назад +2

    Kunkuyu this is the time to get arrested and zikhale

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du Месяц назад +4

    Zikhale ng'oma nyama dzikuluzikulu mwangozidyela ndalama 😂😂😂

    • @user-wb3us4pg4b
      @user-wb3us4pg4b Месяц назад

      😂😂😂😂 nyama zazikulu Zagwa taedzeka❤

    • @Dysonkhofi
      @Dysonkhofi Месяц назад

      Akatero Ku undunako akaba kut abwezeretse.

    • @AllanWyson
      @AllanWyson Месяц назад

      Kkkkkkkkk nyama zikuluzikulu zagwa chagada uku😂😂😂😂😂

  • @JeffreyKambwemba-zs7wy
    @JeffreyKambwemba-zs7wy Месяц назад +2

    I even wish if this party was never exist in Malawi 🇲🇼 I hate azitsogoleli a chipani ichi cha M C P

    • @Eric-gb9ms
      @Eric-gb9ms Месяц назад

      Me too bro i hate them all

  • @user-hh4wn4vf9e
    @user-hh4wn4vf9e Месяц назад +7

    😂😂😂😂 zikhare wanya nayo 93 vote 😂😂😂😂

  • @user-cv3zw9ic6d
    @user-cv3zw9ic6d Месяц назад +2

    Kumkuyu galu mkaka galu zikhale ng'oma mwanya nao agalu ndi zomwe muzione 2025 agalu Inu paulendo

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e Месяц назад +4

    Mumba wazidzimusa anthu.

  • @YusufuUsumani
    @YusufuUsumani Месяц назад +3

    akabwela mudyereni, WA. MCP komaso osampasa voti yanu

    • @EllinaBitto
      @EllinaBitto Месяц назад

      Takumvani bwanaaaaa😂😂😂😂😂😂😂

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 Месяц назад +2

    Koma mulungu amamenyadi nkhondo a Mkaka mpaka kuluza Matama onse aja !! Madala nyama zikulu zikulu nkati zachisoni apapa apa mcp must b careful otherwise muzagwira chikolopa coz mwanyanya matama mizimu yakwiya basi.

  • @SautsoBandah-lf4so
    @SautsoBandah-lf4so Месяц назад +1

    New mcp president mumba

  • @AkiduMakwinja-x1h
    @AkiduMakwinja-x1h Месяц назад +2

    Congratulations kamajekete😂😂😂

  • @RobertWelosi
    @RobertWelosi 27 дней назад

    Nyama zikulu zikulu zikhale ng'oma 😊

  • @Frederick-s4h
    @Frederick-s4h Месяц назад +2

    Bakilimuluzi tv yataegula athuambili kuti ayone kutali mcp samala kumoto kutsogolo kwakwo

  • @lucasnyirongo2630
    @lucasnyirongo2630 Месяц назад +2

    Gotani fails to manage a small constituancey in mzimba ..she is very corrupt

    • @user-wg8tp8in1v
      @user-wg8tp8in1v Месяц назад

      Mmmmmm

    • @user-jn9tz3li3v
      @user-jn9tz3li3v Месяц назад

      MCP has made a mistake, Gotani Hara is not a leader but a confusionist. Her behaviour is very questionable. Chakwela will fail because of Gotani Hara.

  • @user-bf2ms9ss6d
    @user-bf2ms9ss6d Месяц назад +2

    Chisankho ndi muntima🙌🤣🤣🤣🤣

  • @user-wb5ym2qm6y
    @user-wb5ym2qm6y 29 дней назад

    It's true Mr Mkaka was not responding calls. I have great witness on this I once called him through our constituency but was quite. Even the whole community complains him of not responding calls

  • @LeviChakwira
    @LeviChakwira Месяц назад +4

    Chipani choipa ichi. Kupha chilima chifukwa cha udindo

    • @EllinaBitto
      @EllinaBitto Месяц назад

      😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢

  • @Frederick-s4h
    @Frederick-s4h Месяц назад +2

    Kkkkk ndasangala athuwa aluzanso covetion tidikilaso 2025 tidzaduleno mutu khuku yatabala pakhosi kuti kwiyoooo

  • @user-hq2io8nk7s
    @user-hq2io8nk7s Месяц назад +1

    Anthu omwe aluza asamalenso kudzaluza pa maprimary au mp.Makhalidwe awo ndi woipa komanso kudzikonda.Ndi amene amayipitsa mbiri yachipani ndi a president athu.

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 Месяц назад +1

    A mcp ndalamazo zibwere ife tikudikira tizidye koma vote yanga naaaa ineyo simuzayiwona ntharedi anthu oyipa inu shatapuuuuu.

  • @user-hq2io8nk7s
    @user-hq2io8nk7s Месяц назад +1

    Thumbs up for munthu wanzeru komanso wachilungamo Divason Kadzipachike

  • @Frederick-s4h
    @Frederick-s4h Месяц назад +2

    2025 tambalayo adzasamale asadzatuluke khola tidzamukazingila pachiwaya chapaseu

  • @AllanWilsonbanda
    @AllanWilsonbanda Месяц назад +2

    Mayi gotani hara one of them anthu amene adakoza chiwembu chokupha chilima zimene amkafuna zayamba kutheka kwatsala 2025

  • @EtinesChilaulo
    @EtinesChilaulo Месяц назад +2

    Komatu Bryan Banda amakhala serious

  • @spargomw
    @spargomw Месяц назад +2

    Yakwiya nd Mizimu.😂😂😂 Otumbwa onse out.

  • @user-rk3gq7gd8f
    @user-rk3gq7gd8f Месяц назад +2

    Abanda mumuuze chakwera ndi manganya zimene wawona zikhale nawoso amazing 2025

    • @PaulChaleka-lb4vx
      @PaulChaleka-lb4vx Месяц назад

      Exactly 2025 zomwe zamuchitikira zikhale ng'oma zidzamuchitikira chakwera

  • @imaculadaAndre-ns1py
    @imaculadaAndre-ns1py Месяц назад +2

    Kkkkkk😂😂😂😅mulungu simuthu

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn Месяц назад +2

    Musasiye gawani ndalamazo tizigula ufa anthu abwino inu

    • @Eric-gb9ms
      @Eric-gb9ms Месяц назад

      😂😂😂😂😂😂💐

  • @Frederick-s4h
    @Frederick-s4h Месяц назад +2

    Tikamadzadula mutu watambalayo pasadzapezekepo olila tidzamukakha

  • @RodwellChisambo
    @RodwellChisambo Месяц назад +2

    Bakili tv come on zikhale wagwa chagada😂😂

  • @MaryChavula-jz3di
    @MaryChavula-jz3di Месяц назад +5

    Ankaka zomwe zawachitikilazo ndi ndendende zidzachitikila mcp 2025 anatiphela chilima

  • @HandyChipeta
    @HandyChipeta Месяц назад

    We are proud of you wakwa Shumba!!

  • @MathiasJoseph-xv1hj
    @MathiasJoseph-xv1hj Месяц назад +2

    Kuluza kwa azibambo atatuwa asaa ndakondwa bwanj? Km

  • @LovelyCardGame-nx1gj
    @LovelyCardGame-nx1gj Месяц назад +1

    Brian watchutchutchu😂😂

  • @JoshuaNyirongo
    @JoshuaNyirongo Месяц назад +1

    Nyamayaikulu Zikhale zaivuta

  • @user-oc9vl9xz8e
    @user-oc9vl9xz8e Месяц назад

    Zakhala bwino Zikhale kuluza munthu wankhadza Mulungu wakwiyanaye anthu akamakudandaula umakhala wasoka Congratulations Chimwendo...

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg Месяц назад +2

    zíkhàlé kúmkuyu àchità bwino àluzà

  • @lawrentkaunda9316
    @lawrentkaunda9316 Месяц назад +1

    Mumba ndi machine

  • @JanaMdala
    @JanaMdala Месяц назад +1

    Azikhale ndi galu wamkulu waluza big up

  • @ChembeWaimba
    @ChembeWaimba Месяц назад +2

    Kuchosa MCP mu mboma ndakayika, chipani ndi chachikuru, komanso President Chakwera what a servant leadership mpaka kukhala limodzi ndi anthu usiku, this President may God bless

    • @user-uf4db7im7d
      @user-uf4db7im7d Месяц назад

      Mbolo yako galu iwe

    • @EllinaBitto
      @EllinaBitto Месяц назад

      Zoonadi ngati mmene anakakhalira kuchikangawa kuja usiku onse❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤ bomadi 2025 mcp❤❤❤❤❤❤❤❤

    • @Henry-vw2cz
      @Henry-vw2cz 29 дней назад

      Ndiwe chisilu chamunthu

  • @innocentmusuli7380
    @innocentmusuli7380 Месяц назад +1

    Kkkkkk amwano antuzu aluza nkulakwa kulankhula choncho

  • @EmsAdam-c1i
    @EmsAdam-c1i Месяц назад +1

    Kanyimbo kabakili muluzi TV sports sports😂😂😂 kamawaguguda muntima azikhale ng'oma achita bwino aluza anyera gede lero kkkkkk

  • @CathrineBizza
    @CathrineBizza Месяц назад +2

    Pepekale ywmweyo kkkkk wanyaaaa

  • @Aqiec09
    @Aqiec09 Месяц назад +1

    Cograts to mumba

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl Месяц назад +1

    Amalawi amcp adyeleni agalu awa osapasa vote

  • @GeorgeSmoke-xf2ks
    @GeorgeSmoke-xf2ks 29 дней назад

    Kuyankhula kumpoto kusiyana ndi mlomwe region,southern region ndiya mlomwe basi

  • @BlessingsMbulo-f8e
    @BlessingsMbulo-f8e 26 дней назад

    A Mumba is going forward 2025

  • @Frederick-s4h
    @Frederick-s4h Месяц назад +2

    Bakili muluzi anakoza timaivela deile patsalano pa 2025 kuka dulamutu tambala kut kwiyoookwiyooooooo kkkkkkk wina azalila

  • @user-jb8bc3qf3s
    @user-jb8bc3qf3s Месяц назад

    Please Mr President this is good convention

  • @user-hq2io8nk7s
    @user-hq2io8nk7s Месяц назад +1

    Kuba ndalama ndikumakapangira kampeni aaaaaaaah mwagwa nayo.

  • @MaryChavula-jz3di
    @MaryChavula-jz3di Месяц назад +1

    Mumba wayesetsa koma analowa chiani cholakwika umenewo ndi mpingo wa aflican wa magogo

  • @IshuBillalli
    @IshuBillalli Месяц назад

    Koma akuluakulu inuyo ndi nkhani zina koma ndikuyamikeni powauza chilungamo andalewa pena amanyanya auzeni zomwe sachitika lerori apa osati ndiolose ndikakutavune

  • @user-mf5ce9wj4m
    @user-mf5ce9wj4m Месяц назад

    Azikhale ntchito zawo zakhanza ndi chifukwa alephela anthu amawona

  • @giftkanjuchi-qm8hf
    @giftkanjuchi-qm8hf Месяц назад

    Kumakhara bwino ndi anthu. Amalawi azagamula wokha 2025 mmene chakwera wagwilira ntchito kuti apitilize kapena ai
    Once again amalawi will have a final say

  • @AlexHenere-r6l
    @AlexHenere-r6l Месяц назад +1

    Azikhale mlungu watimeyera kkkk
    Ndimmene tikaichotsere MCP tikakavota Chaka chamawa osakaika

  • @EagerChicken-qj6xu
    @EagerChicken-qj6xu Месяц назад +1

    Mkaka ndi munthu wodziwa kuyedzeka wazdziyedzeka yekha. Ndimo amachitila mulungu.

  • @Dysonkhofi
    @Dysonkhofi Месяц назад +1

    Ndalama zapita!
    Zikhale Chithyola.

  • @TiwongieChimphie
    @TiwongieChimphie Месяц назад +11

    Goodluck to all the winners

  • @tariroJinya
    @tariroJinya Месяц назад

    Brian let me tell this,ilike most bt politics is abad animal.ndale ndi kanyama kopsya

  • @SpencerKadewere-cd5ok
    @SpencerKadewere-cd5ok Месяц назад

    Ndalama akamapereka idyani basi vote ndi mumtima iyaaa

  • @SelinaGamaliyere-q8v
    @SelinaGamaliyere-q8v Месяц назад +1

    Ndipo ndasangalala pomva kuti kunkuyu.zikhale ndi chitchola anthu oyipa mtima anthu okupha tionana 2025 agalu inu

  • @watsonmhango8794
    @watsonmhango8794 Месяц назад +1

    Zimenezi zikupherezera zisankho za 2025 samalani a MCP

  • @user-lp8wj3vq4x
    @user-lp8wj3vq4x Месяц назад +1

    Atimes musamupope gotani inu sizimayi wabwino muona 2025 azaluza

  • @user-zm4jb5oq7b
    @user-zm4jb5oq7b Месяц назад +1

    Maliro ndi oika mawa ku city centre achipani cha MCP kozekani

  • @chrisboyce2
    @chrisboyce2 Месяц назад

    Zoona Brian Nkhalidwe ndi Chuma Ndipo Tidziyesetsa kukhala bwino ndi aliyense

  • @WilliamSaka-j6k
    @WilliamSaka-j6k Месяц назад +1

    Ankaka auyezeka Kaye udindo😅😅

  • @kambukuskylinerholdings7488
    @kambukuskylinerholdings7488 Месяц назад

    Why Brian is asking questions and he is busy on the phone, how can you hear to the guy replying

  • @user-bi5lg8mg9y
    @user-bi5lg8mg9y Месяц назад +1

    Mr Bakili TV repeats again Pepekale ka volume🤸‍♂️😂

  • @GiftJulius-gx2kb
    @GiftJulius-gx2kb Месяц назад +1

    Zikhale kkkkkkkkk kunyelela kukamwa

  • @ErickTym-u2m
    @ErickTym-u2m Месяц назад +1

    Ng'oma ndalamazo ukanabwezetsanso ma jecket ako ma suite kupangitsa ung'onoung'ono sorry zimachitika kkkkk

  • @KunyengaMoyo
    @KunyengaMoyo Месяц назад +1

    Kunkuyu ndi kamajekete agwa nayoo 🤣🤣🤣🤣

  • @user-wb5ym2qm6y
    @user-wb5ym2qm6y 29 дней назад

    Deligates are delicates kkkkkkkkkkkk they don't know what they do

  • @user-rk3gq7gd8f
    @user-rk3gq7gd8f Месяц назад +1

    Amalawi sapanganika amakhala anasakhakale wawo

  • @chinsisingondo4834
    @chinsisingondo4834 Месяц назад +1

    A Nkaka taedzeka kaye

  • @MathiasJoseph-xv1hj
    @MathiasJoseph-xv1hj Месяц назад +1

    Km ndasangalala heveee kuluza kwa azibambo atatuwa makamaka ndunaziwiliz ndakondwaatu

  • @MerienohawaiBro
    @MerienohawaiBro Месяц назад +1

    😂😂😂 Esther nchekachilenje😆😆😆😆😆😆

  • @user-cp4qt9hs8w
    @user-cp4qt9hs8w Месяц назад

    Eeee zikhale adzilingalila kt tidamphelanji chilima iye amayesa kt adzamusankha mchakwela azawo apanga kampeni osati kusaka ntanyiwa

  • @munashemoyo4190
    @munashemoyo4190 Месяц назад +1

    Ine Bola kamayekete waluza ndakondwa bas 😅

  • @isaacthawani5442
    @isaacthawani5442 Месяц назад +1

    Kunkuyu zimu wa witika wamukana😂

  • @Michael-mb2sy
    @Michael-mb2sy Месяц назад

    Mumba is real the next president

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi8897 Месяц назад

    Any failure is a preamble to success

  • @GraceKuchombo
    @GraceKuchombo Месяц назад

    Nkaka wachita bwino waluza munthu oipa ameneyo

  • @SithembilePhiri
    @SithembilePhiri Месяц назад +1

    Wanya nayo😂 zikhale

  • @user-vm7iz6oz6r
    @user-vm7iz6oz6r Месяц назад +1

    Ndiye muona aphanakoso