Joseph Nkasa - Chakwela Delivery (official music Audio)

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 30 ноя 2024

Комментарии • 49

  • @pattingosi6770
    @pattingosi6770 16 дней назад

    Chakwera..chakwera..chakwera🥰🥰😍😍

  • @cstvinmw7187
    @cstvinmw7187 3 месяца назад +2


    Mkuluyi amatha kulemba nyimbo

  • @RichardMdala-ml4hx
    @RichardMdala-ml4hx Месяц назад +1

    I just like the talent, not the politics. The guys has talent.

  • @rajivjere110
    @rajivjere110 2 месяца назад

    Osaspa mtima kwambiri. The song is on point 🔥🔥🔥

  • @SelemaniMatola-x8c
    @SelemaniMatola-x8c 3 месяца назад +1

    I don't want to comment much on political songs but about this guy he is always singing praising every leader who is in power.

  • @ronaldchilinda2855
    @ronaldchilinda2855 3 месяца назад +2

    Chakwera bomaaaaaa 🎉

  • @alicklabu2494
    @alicklabu2494 3 месяца назад

    nyimbo iyi yamenyedwa bwino heavy ndipo ndiyekhayo yemwe sadziwa nyimbo ndiyemwe angayankhule mwano... more fire mkasa

  • @NellieMsonthi
    @NellieMsonthi 15 дней назад

    zili choncho eti a nkasa ai zikomo tainvera nawo nyimboi

  • @GeoffreyChibowa
    @GeoffreyChibowa Месяц назад

    ☑️☑️☑️

  • @WaliaCon
    @WaliaCon 2 месяца назад

    Machine abwera Ku MCP ❤❤❤❤ watipeza basi

    • @PrinceBlessings-bv5bs
      @PrinceBlessings-bv5bs 2 месяца назад

      😂😂😂😂 akugwira ntchito yake uyu.. apa Ali ku aford

  • @thomaskalima7379
    @thomaskalima7379 3 месяца назад

    Nkasa ndi machine 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @edwinshaba3730
    @edwinshaba3730 3 месяца назад

    Boma ndilomweli basi❤❤❤

  • @thumbikokaira6743
    @thumbikokaira6743 3 месяца назад

    Dolo kwambiri 🔥🔥🔥

  • @StevePemphokwenda
    @StevePemphokwenda 3 месяца назад

    Nkasa pa repeat bwaaa❤❤❤❤

  • @PeterMahwayo-eo4ef
    @PeterMahwayo-eo4ef Месяц назад

    BOMA NDILOMWERI

  • @kennethmoyo8672
    @kennethmoyo8672 3 месяца назад

    Kuyambila lero nyimbo za mkasa sizavelatso ndi galu wen wen dyela pa drama chisilu uyu ndichifukwa may ake amagona nyumba ya uzuh galu wamuthu😢😢

  • @EvanceJimmy-e6c
    @EvanceJimmy-e6c 3 месяца назад

    DPP my vote koma Mkasa mkatundu. Amakwapula akafuna kukwapula nyimbo

  • @GeoffreyChilombo-yz4yh
    @GeoffreyChilombo-yz4yh 3 месяца назад

    ine ndi wa DPP 💙 💙 koma nyimbo iyiyi 💥💥💥

  • @Frederick-s4h
    @Frederick-s4h 3 месяца назад +2

    Ndikudziwa kwambili kut ndiwe kapolo watumiki aumbava km Joseph nksa udzachita manyazi zd mukagwetsedwa 2025 ukumutembelela tambala wakuda uku

  • @ShearstonNyirenda
    @ShearstonNyirenda 3 месяца назад

    Yomweyo vote tanga chakwera

  • @FysonKashon
    @FysonKashon 2 месяца назад

    ❤❤❤❤❤

  • @Frederick-s4h
    @Frederick-s4h 3 месяца назад +1

    Galu weniweni uyu

  • @PATREQUEChissime-j7p
    @PATREQUEChissime-j7p 3 месяца назад

    Uzafela kusata nkasa ,wasala iwe wasala iwe akuchotse nyesi Ili padazilo waukape iwe

  • @danielzitande5231
    @danielzitande5231 3 месяца назад

    Mkasa ndi nali mbali yako koma apa mmmmmm ndiwe oipa

  • @edwinshaba3730
    @edwinshaba3730 3 месяца назад

    Boma ilooo

  • @PreviousStanley
    @PreviousStanley 2 месяца назад +1

    .inuso mutamuza Kuti akuyimbireni nyimbo akuyimbireni ndinthu awatu ndioyimba amankhalaso akusaka ndalama

  • @chifundo-f1w
    @chifundo-f1w 3 месяца назад

    Amuzachosanso Mano ena uyu

  • @jonesnezara4294
    @jonesnezara4294 3 месяца назад

    Mesa ndi mkasa yomweyi ananenesa kuti kusapota ndikuyimbira andale ndikomwe kwansaukisa ndikumuphera sogolo, ndipo sazayimbiso nyimbo yochemelera kapena kusapota wandale. Nkhaniyo anainena PA cruise 5 ndi Joab chakhaza

  • @DavyChirwa-k9x
    @DavyChirwa-k9x 3 месяца назад

    pakukhalira pako Joseph

  • @HassanAllie-z8l
    @HassanAllie-z8l 3 месяца назад +1

    Nosenu amene mukuti mkasa wayimba bwino ndinu makape limozi ndi family yanu

  • @charleskayamba-s7c
    @charleskayamba-s7c 3 месяца назад

    chakwela yemweyo

  • @BiquitoniNsandamila
    @BiquitoniNsandamila 3 месяца назад

    Nkasa amayesetsa kuyamikila kuti asinthe phungu mbambande

  • @ConradccjSokoSoko
    @ConradccjSokoSoko 3 месяца назад

    Awinasonso❤

  • @CHARLESMWANZA-s5v
    @CHARLESMWANZA-s5v 3 месяца назад

    Chisiru ichi

  • @DanMhone-iw6xg
    @DanMhone-iw6xg 3 месяца назад

    Kachisilu aka sikamaziwa chimene chimafuna mkowona chili chosawuka kunthupi nd kuzimu komwe

  • @emmanuelmwanza-p4r
    @emmanuelmwanza-p4r 3 месяца назад

    Joseph nkasa ndi oiyamba dolo katatu nyimbo yokoma yodzadza ndi mfundo komaso zitukuko zomwe zachitika kutsutsana naye mkungotaya Nthawi chifukwa zomwe akunenena zilipo pa ground,

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 2 месяца назад

    😂😂😂😂😂😂😂😂 hule mu nyimbo...
    Sasankha mbali😂😂

  • @WakatMakwinja
    @WakatMakwinja 3 месяца назад +1

    Umphawi siwabwino, munthu umasanduka chitsiru poyerayera. Nyimbo zonse zija kudzi fufuta nkusiya iyi yopanda ndi tune yomwe
    Hmmm umphawi sizinthu, kwasala mupeka yotukwana makolo amanu!

  • @AllanGonthi
    @AllanGonthi 3 месяца назад

    Mose wa lero ija mudaikwapula man mukadasiira yomwe ija basi

  • @MosesShaibu-ee8hn
    @MosesShaibu-ee8hn 3 месяца назад

    Ukungo funandalamaiwe ukuwona ngati zikuyendele?

  • @ChisomoPhillip
    @ChisomoPhillip 3 месяца назад

    Dolo

  • @bestonlamson213
    @bestonlamson213 3 месяца назад

    Ngti kuli chidzete ndiye ichi basi ati nchiyani tsono

  • @davidmagwira6988
    @davidmagwira6988 3 месяца назад

    Yudasi😂

  • @MichaelMbona-ch2kc
    @MichaelMbona-ch2kc 3 месяца назад

    Waukape iwe

  • @HalimaMtewa
    @HalimaMtewa 3 месяца назад

    True lies

  • @GeorgeGeorge-vp4cs
    @GeorgeGeorge-vp4cs 3 месяца назад +1

    Nonsense again

  • @PATREQUEChissime-j7p
    @PATREQUEChissime-j7p 3 месяца назад

    Uzafela kusata nkasa ,wasala iwe wasala iwe akuchotse nyesi Ili padazilo waukape iwe

    • @juniormkandawire
      @juniormkandawire 3 месяца назад +1

      Akanayimba za DPP bwenzi Machende ali lende lende kusekelela