COMRADE LWARA - KUMANGA ANTHU NGATI ACHINA KALIAT NDICHINTHU CHOWAWA KWAMBIRI.

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 23 окт 2024

Комментарии • 19

  • @SheenahMwalabu-iz3pr
    @SheenahMwalabu-iz3pr Час назад

    Hello mr Lwala. Sir plz musamasowe ngati ineyo l love to hear and listening to you everyday cz mumakamba ndikutitsegula mmaso and you are fun 😂😂❤❤ mudzitichezera daily sir. Long live ine mmakutsatani kwambiri kuyambira 2022 😊

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 5 часов назад +3

    Team yodziwa mpira siopa finalz Manganya akuopa finalz

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 5 часов назад +2

    Am waiting Bakili Muluzi TV atiuza znsezi madzulo pano dikirani

  • @BensonChilundu
    @BensonChilundu 6 часов назад +2

    Chipani chomwe chili m’boma chikamamanga anthu chotero dziwani kuti chipanicho ndi cholephera ndipo chituluka m’boma.Dziwani ichi,munthu ngati wapanga cholakwa m’nyumba ya munthu kenako mwini mkukupeza ndipo mwamwayi wapeza mpata wothawa ndipo kuti uli mkati mothawa kenako mkumva zoti akukutukwana yamba kuyenda.Mayi Kaliati tili nanu limodzi ndipo Mulungu yakha ndi yemwe akudziwa chilungamo chake.

  • @SifatiMoses
    @SifatiMoses 5 часов назад +2

    Chisiru manganya ndiyemwe akuyenda pasi pasi, chilungamo chikubwera palibe chisisi pansi pano.

  • @JosephHill-fy1bb
    @JosephHill-fy1bb 2 часа назад

    Next year, enanu muzidzati kumangidwa, kungolandila bail kenako rearrest pompo... Am seeing enanu mutalandidwa chuma chanu, kwangokhala ndi mira wanuyo basi...
    Am seeing enanu mukudzipha...

  • @InnocentNitamanMilanzi
    @InnocentNitamanMilanzi 2 часа назад

    Judge ameneyo akati asanene bwino
    Timuombera asamale

  • @FredKanyerere
    @FredKanyerere Час назад

    Zovetsa chisoni 😂😂😂 moti tizipita chitsogolo kma ayi.

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 6 часов назад +2

    Manganya ponyelera pako Kumene Uli plus yr boss

  • @MalvinMakolija
    @MalvinMakolija 2 часа назад

    Dziko lomvetsa chisoni kwambiri mmalo momathetsa mavuto okhuza mafuta bzy kumamanga Anthu zamanyazi😢😢 kwambiri mukuononga mbiri ya boma lanu inu a MCP samalani people they're very tired with you samalani samalani

  • @KalongaWhy
    @KalongaWhy 4 часа назад

    Mukuyankhura zachibwana pamenepo ndipamene mukana lusa kupita konko chimenecho chikanakhara choyamba kuyambisa mademo kupita kupolisi konko koma amalawi kaya zopusa zokhazokha

  • @MillieMalakam
    @MillieMalakam 6 часов назад +1

    Komano boma lamalawi lowola ndithu zimenezi nde tiziti chiyani

  • @SifatiMoses
    @SifatiMoses 5 часов назад

    Inu chakwera anangopezeka mwangozi kukhala president, munthu ngati amakanika kutsogolera m'pingo kuli bwanji kutsogolera dziko. Awa akanika angopakira azipita asadikile kuchoka mwa uyo uyo.

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 6 часов назад +1

    Mupite pa police po mukaotchepo, apólice wonso mupite mmanyumba mwawo muotche nyumba zawo ndikuphanso wana wao Ngati m'mene achitira Wanthu aku Maputo Moçambique apólice amocambique Ali Ndi Mantha panopa anayesesa kuitanisa herocopita Ku south Africa kuombera Wanthu Koma apólice amocambique agonja, Ndiye popeza Amalawi Ndi opusa Mantha,muzipenya Wanthu amocambique Ndi owopsya sangafane Ndi A Malawi ndinu ogona

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 5 часов назад

    Ma Corwards amcp ndimanganya apanga propaganda akuwonga ngati manganya angawine amfiti.

  • @ephraimphalawala4720
    @ephraimphalawala4720 6 часов назад +1

    They won't win Mcp, they are waiting time

  • @SimonBanda-b1f
    @SimonBanda-b1f 5 часов назад

    Apa tiwona ngati ma court aku malawi ndi a corruption dii.
    Gwirani amene anapha Chilima
    Leave this nonsense

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 5 часов назад

    Atimange osusa tonse asale MCP yokha yokha kulibe malo kupolisiko kodi sitikwanako

  • @marthaphiri3600
    @marthaphiri3600 6 часов назад

    Usi mu coward kuopa mzimai kkkkk