Nkhanga Zaona president Chakwera wagendedwa ku Chikwawa anthu mpaka windo laphwanyika

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 17 сен 2024

Комментарии • 58

  • @AckimChione
    @AckimChione 5 дней назад +6

    Very good people from chikwawa

  • @AbudulJohn
    @AbudulJohn 5 дней назад +8

    amuchepesaso akanamuswa mutu chifukwa chake angoyenda yenda kuthawa ku state house kumagona muliyenda amumenyeso kwasala kwa Chikwewo kumeneko akamuswaso

  • @ThivadoartistDyson
    @ThivadoartistDyson 5 дней назад +6

    Ndipo tangoyambapo ngat ndikufa tifela mbendela yathu ndipo zitsilu zonse zomwe zili kumbali ya mcp kwinaku zikuvutika nd njala,kukwela kwakatundu ,kutsika kwa kwacha tifa tifela inu ndi ana anu pakut simukudziwa zomwe mukuchita..💪💪💪💪 oyeee vilva never change, Malawi ndi wathu.

  • @MustafaMakumba
    @MustafaMakumba 3 дня назад +1

    Sunati chikangawa mumakwana chikwawa people ❤❤❤❤❤

  • @EnockGispo
    @EnockGispo 5 дней назад +2

    Apm ma vote

  • @misoMoyo
    @misoMoyo 5 дней назад +2

    Wina akuti Radio yabodza mukutiuza kuti sanagendedwe or bwanji wa MCP iwe komweko sanati Chikangawa amugenda pang,Ono kodi amaboma ena simungaonere apanga anzanuzo

  • @JibraanSharief-ol1yn
    @JibraanSharief-ol1yn 5 дней назад +2

    Akanamuswa mutu garu

  • @Chayibujackison
    @Chayibujackison 5 дней назад +3

    Comrad ntanyiwa yomweyo mawulem

    • @innocentkhwamba856
      @innocentkhwamba856 5 дней назад +1

      Awuzen zowona zokhazokha mmatikwanira mmalawi muno🎉 paribeso wina

  • @user-gk4nu4xr8r
    @user-gk4nu4xr8r 5 дней назад +1

    Chakwela delivery 🎉🎉🎉🎉🎉🎉

  • @MaryTSwachi
    @MaryTSwachi 5 дней назад +1

    Watikwana ndithu sitikumufuna wakuphayi Kodi akutivuta bwanji? Wadyerayi

  • @PeterFrancis-q6h
    @PeterFrancis-q6h 2 дня назад

    Wopusa iwe Muthu wosayamika

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 3 дня назад

    Mbuzi zambili chifukwa apasidwa ndalama zokuba .
    ..kuyimbili mfiti mmanja ....amalawife ndi anthu opusa zedi nanga mmene zavutila mmalawi muno ndiye zisilu zina zizikati chakwera mpaka 2030 .....zisilu za anthu umphawi uli thooo kupusa kwenikweni

  • @MussaChilembwe
    @MussaChilembwe 5 дней назад +1

    Zakhala bwino pamenepo azikapanga kwawo ku kasiyako muthu oyipa ameneyo

  • @kondwanivyalema9449
    @kondwanivyalema9449 4 дня назад +2

    Kkk chikadafa chi Mr chakangawa 😂 chimunthu chonumkha choyipa

  • @CharityKangulero
    @CharityKangulero 5 дней назад +1

    Umakwana tanyuwa zaona 😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @PrinceThom-pe6ie
    @PrinceThom-pe6ie 5 дней назад +1

    Sopano inu agaru a mcp mumati mthanyiwa ndi wabodza ndiye izi zakuti chikangawa wagendedwa ndi zabozanso?

  • @JibraanSharief-ol1yn
    @JibraanSharief-ol1yn 5 дней назад +1

    Akanamupha garu wa chikangawa

  • @JibraanSharief-ol1yn
    @JibraanSharief-ol1yn 5 дней назад +1

    Mboli yamake garu

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe 5 дней назад +2

    Kkkk chikangawayo akadzapitanso ku lower states.anthu adzamutumizila ng"ona pampanfo wake mgalimoto .asamalen

  • @JibraanSharief-ol1yn
    @JibraanSharief-ol1yn 5 дней назад +1

  • @DoreenLivata
    @DoreenLivata 4 дня назад

    Mr ntanyiwa mbambande

  • @pidona825
    @pidona825 5 дней назад +1

    But u mtanyiwa I always pray for you

  • @HlamuChavalala
    @HlamuChavalala 3 часа назад

    Koma tingoti usamalekwambili Ngati ukugendedwa apolisi alipompo uzifuse ukaluza udzafika podzikweza wekha ntendele wamuntima ulibe undikile udzaone anthu odalitsidwa akulamulila chilichonse chimalola chifukwa Mulungu amalisekelela dziko m'dalitso satsazila Mumufuse Mulungu zadalitso wanu musakakamile dalitso wayena mupululitsa athundinjala thawi ya Bingu and pm chilichonse chimalola olomikhaka imatheka usiye usakakamile olo group lanulo palibe muthuolimbitsa ntima olommodzi olozomwe mumakamba mudzizibweleza kuvela ndibwelela asakugendeni bwanji mutho akumadya chitedze pomwe inu

  • @AlexChikoti-y3s
    @AlexChikoti-y3s 4 дня назад +1

    ❤❤🔥🔥🔥

  • @MussaChilembwe
    @MussaChilembwe 5 дней назад +1

    anakangomupha basi kuti dziko rathu likhare bwino osati izi manyakawa

  • @babranzima8120
    @babranzima8120 5 дней назад +1

    Amalawi afika potopa😂😂😂

  • @DavidKantukule
    @DavidKantukule 4 дня назад

    Go on Mtanyiwa 😂

  • @AllieKaisi-je6rm
    @AllieKaisi-je6rm 4 дня назад

    Osapita kumaliro kwa sadic Mia lero kupita kukaona ng'ombe kkkk

  • @MaryTSwachi
    @MaryTSwachi 5 дней назад +1

    Amuchita bwino Kodi kunja kuno kulibe afiti? Osamupha bwanji iye wapha anzake

  • @GanizaniBonongwe
    @GanizaniBonongwe 3 дня назад

    Kkkkkk koma yah ziliko chaka chino

  • @Chayibujackison
    @Chayibujackison 5 дней назад +1

    ❤❤❤

  • @VincentKautale
    @VincentKautale 15 часов назад

    Haaaa za ziiiii zenizeni

  • @LongTeez
    @LongTeez 5 дней назад +1

    Agofa tatopa Naye

  • @FatimaLesson
    @FatimaLesson 4 дня назад

    😂😂😂 Galu ameneuja sadati

  • @Thewarrior7093
    @Thewarrior7093 4 дня назад

    Angoni simukutithandiza ayi , galu ameneyi amadutsa mbali yanuyo daily koma osamuthira miyala ayi?

  • @FarzanaStembridge
    @FarzanaStembridge 4 дня назад

    Akanapheratu

  • @user-ve2ts3yr2n
    @user-ve2ts3yr2n 4 дня назад

    Uyutu atuwuze kumene kuli chilima wathu

  • @PeaceIslsm
    @PeaceIslsm 5 дней назад +1

    Kkkkkkk😂🤣😂

  • @Danp-q4n
    @Danp-q4n 19 часов назад

    Nzoona 😂

  • @Kaliwo
    @Kaliwo 3 дня назад

    Zavuta

  • @RabeccaChiumia
    @RabeccaChiumia 5 дней назад +1

    😂😂😂😂😂😂😂

  • @NoliaGama
    @NoliaGama 4 дня назад

    Anthu amafika potopa

  • @user-gk4nu4xr8r
    @user-gk4nu4xr8r 5 дней назад

    Radio njaboza iyi 😂😂😂😂😂

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 5 дней назад

    Lower shire ulendo unonso ma mp onse akhala a congress chifukwa dpp inatha sitikukufunani anthu alomwe inu

  • @captainmdima1102
    @captainmdima1102 5 дней назад

    A ntanyiwa kuchulusa maboza aa za zii kma 2025 mcp boma kale

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 5 дней назад

    Sikoyamba president kugendedwa even peter wakoyo anagendedwaso komwe kwawo ,bakili muluzi amamugendaso ku karonga dairy koma panthawi ya mavoti amawinanso nde iwe chitsiru ntanyiwa usatipusise ndi maboza akowo, ndikuwonanso kut pano zokamba zambiri zikukuvuta masiku ano chifukwa chakwera akupanga zitukuko pena paliponse wagwa nayo ukhala nkayidi mpaka kale ,mcp yipitilila kulamulila

    • @ReginaMulipa
      @ReginaMulipa 5 дней назад

      Pakholo pamako plz uone comment yangayi napakunya kuzaza sisi ponyera eti osakameta uko bwanji nyani

    • @user-dh1oi8mb4v
      @user-dh1oi8mb4v 4 дня назад

      Ndipo zilibwino kwabasi iwowo angatinamize ife kuti abweletsa mafuta Ali juice was mzimbe chamba

  • @Ramosfresh
    @Ramosfresh 5 дней назад

    Kape iwe ntanyiwa