Osakakamiza anthu kuti alembese ndi cholinga choti azavote, ma service aboma pano anasiya kugwira ntchito kwa anthu osauka, mwa chisanzo, osauka kupita ku chipatala amamuwuza kuti mankhwala kulibe pita ukazigulire wekha, walakwilidwa kupita ku police amati galimoto ilibe mafuta panga hire galimoto, kupita ku immigration kukapangisa passport uli ndi R50, 000, amafinya ma form ako ndikuwasekera mu Drower kukalonjelera amati kulibe data, ngati ukufuna upereke two hundred thousand kwacha, ngati ulibe siupangiridwa passport, ndiye pamenepo pali chifukwa choti ukavotere?
Kabambe mbuzi yamunthu anali kuti chamasiye sichilimba usachenjele ngati wanzeru ukudya zachilima Garu iwe ma vote unaba koma kwachakwera sungamake chakwera ndi mamunatu si joice Banda munamuoezera uja bomaa ndilomweli ndipo sitikusintha

Ana mwachepa mwachuluka dyela, simungakwanitse kusintha zinthu thawi yathelani,kaya pakampeni muznena fundo zanji kaya
Zaziii
Olephera savomereza 😅😅
Achakwera alibe zelu ndi cabinet yawo yose chifukwa akuzuzisa athu osauka
Muthesa nthawiyanji now its five years?.