Wow! This is the divine definition of grace to individual staff at immigration. Review yourself and stop maladministration. The spirit has spoken. Thank you pastor Kambwiri
Anthu amenewa uthenga aumve ndithu.Ma past port athu ali mmanja mwa ma Burundi,Ma Nigeria ndi Amwenye pomwe ife anuwake timavutika kuti tipeze passport.
uthenga si waku maliro okha, tili nawo ma videos ambiri koma sitimatha kutumiza kamba ka kuwonongeka kwa zipangizo zathu zogwiritsa ntchito. pang'ono ndi pang'ono tayambapo kuzitolera ndipo Ambuye atithandiza.
Immigration ya malawi ntchito ya NRB mumaidziwa koma chipangisireni chitupa changa sitinafunsidwepo mpaka pano from 2018 ndimafunsidwa ndikapita Zambia Mozambique Tanzania 😂😢😅😅
Please continue organizing this program frequently as very helpful to such.God bless you Rev.Kambiri
Kupezeka ku immigration ndi chisomo cha Mulungu zoonadi
Mulungu adasankhadi inu kuti mupezeke pa maudindo muli nawowo. A big Amen
Maybe they can stop corruption. The one who organized this program may God bless him or her abundantly.
This is beautiful may God bless immigration office for honoring God words
Good initiative by Immigration Department. May good Lord bless you. Zikungofunika kulapa basi, mgt Pampanga mbali yake.
Amvekere Amen ngati za nzeru mbava zachabechabe izo ndipo alape anthu amenewo
May God bless you pastor powerful message wakhutu wamva
Wow! This is the divine definition of grace to individual staff at immigration. Review yourself and stop maladministration. The spirit has spoken. Thank you pastor Kambwiri
God continue talking to us through the ones you have chosen
So that we can know why we are in our positions
Amen
Amen Amen Amen.
Mwina asinthe mchitidwe wa corruption. Abusa mudziwayendera kawiri kawiri.
Sipangakhale kusintha because pamwambapo pali mbava yeni-yeni Shakwera ndi afalisi azinzake
Amen, thank you for the word of encouragement Abusa. God bless you
I always agree with this man.He knows how put sense into people mind.
Mau a Mulungu sasankha Malo. God is everywhere!!
Mbava za kuba MULUNGU awakanthe onse awa fire 🔥🔥🔥🔥 pano tilibe mtendere ndipo zoonadi akayamkhadi
To God be glory, ndadalitsika nawo uthengau ndipo wandikhudza
Amen Abusa awuzeni kwambili ave masozi ya anthu ili pamutu wawo
Tadalitsika kwambiri Pastor
More blessings to you pastor
Best place to preach, next time to our Parliament
Amen
May I have it please
Amen man of God 🙏🙏🙏🙏🙏
Amen man of God
Munasowatu a Rev
Amen tadalitsika nawo
Ndizoonadi abusa amthu anenewa amati zuza ndi tauzika kudedza mulungu atithandize awakhululukike ambili akulila😢😢
lapan anyamata Inu aku immigration mukuba kwambiri tikamapangitsa ma passport
Amen 🙏
Anthu amenewa uthenga aumve ndithu.Ma past port athu ali mmanja mwa ma Burundi,Ma Nigeria ndi Amwenye pomwe ife anuwake timavutika kuti tipeze passport.
Ma uthenga akumveka ndithu 😊
Km musiye kuba anthu inuuu aku immigration
Awa akufunikadi mapemphero,mbava zotheratu
Thus Great
Zinyengo ameneo zili mitu bibi
😂
Powerful 🤝
Preach on man of God
Anthu akatangale opondeleza ngati awa until they change that God has nothing to do with them
Abusa next week pitani ku STATE HOUSE,,kwaphulika zimimba kumeneko...
mwina angasiyeko chinyengo
Will the corruption stop????
Anthu awa eeeeeeh ambuye awayendere
Powerful
Kukonda ndalama a immigration
Ada awo anadya 100pin yanga...maofesara achinyengo😅
Mulungu alemekezeke
Amen 🇿🇲🇿🇲🇿🇲
Mrs luhanga ndakuonani number yanu bwanji
Mukayankha pa maso ps mulungu ndalama mutazisiya pansi pano
Apitekoso ku police (road traffic)
Abusa musataye thawi ndi athu amenewo muchedwa nazo, zonsezo ndi mbamva zotheratu,funso nkumati mwasakha bwanji kulalikira office ya athu akubayo Bola munakapita kumamizi kulalikira km naizi Mmmmmm mbamva
Ma officers chinyengo awa alibzyoli anyenga okha okha mwina kumaalalikira Daily
Abusa zilingati mukulalika palibe coz muli pakati pa nkhosa zosochela😂😂😂
Abusa nthuwa Alape kaye katangale amanyanyila kwambili alape ndithu
Mukafikeso ku Ma Court...kuli mamafia kumeneko.
That is a very corrupt ministry in Malawi government plz from there kambiri go to traffic department
Mpaka mmaoffesi?
Athokeni ngamo agalu amenewa akutilangadi passport ya 90pin kudisha 300,pin mulungu awaonedi
Mwina angalapeko anthu ozunza awa
Ingakhale mukuwalakhula choncho,sakumva kanthu ai ndithu"moti enawo angokutukwanani,angoti Galu iwe mumtimamo. tikakudyera kuti.
komatu simukuwoneka abusa kapena Maliro achepa dera lanu..ulaliki wanu umatitsitsimutsa ndipo umatisintha..kapena 2024 Mwabwera ndi zina..😂😂
uthenga si waku maliro okha, tili nawo ma videos ambiri koma sitimatha kutumiza kamba ka kuwonongeka kwa zipangizo zathu zogwiritsa ntchito. pang'ono ndi pang'ono tayambapo kuzitolera ndipo Ambuye atithandiza.
Kumapetoko munakawapemphelela
Madalayo wosapanga retire bwanji akapume
Pomaliza chopereka abusa,,,
Please stop corruption
Ulaliki wabwino aRev gulu lozuza limenelo
Immigration ya malawi ntchito ya NRB mumaidziwa koma chipangisireni chitupa changa sitinafunsidwepo mpaka pano from 2018 ndimafunsidwa ndikapita Zambia Mozambique Tanzania 😂😢😅😅
Anthu awa amakhalangati anachoka direct kumwamba kuti azagwire ntchito ku immigration
Anthu opanda chisoni amenewa kuteroko lero lomwe lino amubera wina ndalama kulephera kugwira ntchito mwachilungamo too much corruption
Anthu a corruption awa
Pastor you are preaching to evil people. Ndinakanika ulendo wanga opita ku UK chifukwa cha asatana ameneo.
Amen
Amen man of GOD
Amen 🙏 🙏
Amen ❤
Amen
amen
Amen
Amen Amen
Amen