Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
🎉
The upcoming president of Malawi. Bravo Fredo, tiri nganganga pambuyo pako
Fredo ndiye atsogoleri achinyamata amene dzikoli likufuna bravo
MCP inapha agogo ako yoh yoh kabwezele man
Osawopa, fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
chilima anamwalira let's move on muyambe mfundo za UTM yopanda chilima
Komans sitikudyaa katatu just a reminder, 😂😂😂 Mcp yapano olo chitukuko chake chitii sikungoba dollar bas ena mpaka akudya chitedze mmalawi mommuno nde muzit Mcp Mcp.
Osaopa ,osatopa ,osafowoka
Muchedwa nazo zimezo kambani fundo zomwe muzapangile amalawi mukazalowa muboma
Mumuuze tanthauzo la aruta continua kuti nichani kumalawi kulibe nkhondo mawu amenewo ni wa samola Mozambique
Komatu mupepela nazo ndale za malirozo aaaah 🚮 Inu muzakhala basi ntchito kufukula maliro kuti muzapeze ma voti... Let me tell you, zokha mukuononga mbiri ya CHAKWERA kuti wapha Chilima, inu muzaluza zisankho momvesa chisoni. Iwe fredokiss olo bambo Ako sananenepo mabodza akowo. Nenani manifesto osati kupaka anzanu ufiti pomwe afiti owophya ndinu a UTM
Tabula lassa
Ndali zimene ukubwera nazo fredo kiss zauchitsilu ndiwe mwana bambo ako sanakhalepo prensdent mumalawi ndiye kuti uziwe anthu sazavotela utm kamba kutchula maliro koma uziwe ndiwe mwana ndali wayiyamba kumene
Inu ambambo anu adakhalako tsogoleli wadziko
Kachitsiru aka kungot boma nalo Lili weak akaka kamafunika kukatchingila njila zonse zimene kamapangila ndalama
Zosantheka
Mm
galu uyu palibe mfundo apa
Amkatamba
🎉
The upcoming president of Malawi. Bravo Fredo, tiri nganganga pambuyo pako
Fredo ndiye atsogoleri achinyamata amene dzikoli likufuna bravo
MCP inapha agogo ako yoh yoh kabwezele man
Osawopa, fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
chilima anamwalira let's move on muyambe mfundo za UTM yopanda chilima
Komans sitikudyaa katatu just a reminder, 😂😂😂 Mcp yapano olo chitukuko chake chitii sikungoba dollar bas ena mpaka akudya chitedze mmalawi mommuno nde muzit Mcp Mcp.
Osaopa ,osatopa ,osafowoka
Muchedwa nazo zimezo kambani fundo zomwe muzapangile amalawi mukazalowa muboma
Mumuuze tanthauzo la aruta continua kuti nichani kumalawi kulibe nkhondo mawu amenewo ni wa samola Mozambique
Komatu mupepela nazo ndale za malirozo aaaah 🚮
Inu muzakhala basi ntchito kufukula maliro kuti muzapeze ma voti... Let me tell you, zokha mukuononga mbiri ya CHAKWERA kuti wapha Chilima, inu muzaluza zisankho momvesa chisoni. Iwe fredokiss olo bambo Ako sananenepo mabodza akowo. Nenani manifesto osati kupaka anzanu ufiti pomwe afiti owophya ndinu a UTM