So very creative and relevant especially now that people are busy with campaigns. It's brief but covering the subject enough. Che Mandota in his cunning ways knows very well what exactly the Shado MP wants to hear, and he quickly cultivates MP's trust.
Achisi uluani kuti Amandota akunama I think in Malawi 🇲🇼 🤔 😕 masakho siworandira ndalama kapena kupepha ndalama anthu kwa Ma MPS but deliver what very will do it in future l mean the MPS, Che Mandota you need to educated people through this comedy .
So very creative and relevant especially now that people are busy with campaigns. It's brief but covering the subject enough. Che Mandota in his cunning ways knows very well what exactly the Shado MP wants to hear, and he quickly cultivates MP's trust.
A Chisi mumakwana 😂😂😂😂a shadoro omwewo 😂😂😂😂😂😂
Mandota sizimuthera 😆🤣 cha chisi nacho😆🤣 aemupi, ashadolo
Ache madota muli bwino ndine sosten chinkumbi ku Zambia l love you guys god bless
Koma iweyo Che Mandota ndiwadyera kwambiri iiiiiiiiii ay
Bwezi mwapeza Shado wina osati uyu nanu chemandota uyu akuphanitu
Kkkķkkk mandota udzafela maja mwa anthu utabwali🤗🤗🤗🤗🤗😍😍
🤣🤣🤣🤣🤣 a shadow adyeredwa iyi nde ndi wake up call kwa ma mp onse adzidziwa kut kumudz kuli anthu ngat chemandota 🤣🤣🤣
Kkkkk mandota vuzoolo zmunanve.. A shado akuvuzatu kuti samaliro sili pati... Zono muthu iwe mukuvuzazo kut maliro akutii shimenecho shilungamo... 😮😮😮😮😮
Mumakwana team ndoxy ulemu wanu wherever you are
Iyiyi ndi massive ma guy😂😂😂😂
Apa actor wafa chifukwa chofuna kudyelera yekha🤣🤣🤣🤣🤣
Ndalama nzakuno😃😃😃😃
Akuti adali athupi ndiye bokosi lawo lifunika extra large 😀
Kkkkkkk mugwire mwendo muli speed umu
😂😂😂 Ndimapangira kuti anthu akanva kumudzi kuja Muluza Mavote
Mwagula foni yabwinotu mr Mandota
😂😂😂😂😂😂 koma abale akut ina ija tinadya tonse
So creative 🔥🔥🔥🔥
Kufaliyament tukalowa ndimapazi😳😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 Sofutatu😂😂😂 mumakwana guys 🔥🔥🔥🔥🔥✊✊✊✊
Mwejo..walume. Kusakombola.
🤣🤣🤣biliati mvura anafa 2005 ifenso lero chisi iweyo umakwana...mandota ndikhuluku kobasi
Ilibwino kwambiri zikumachitika. Anthu ena samafuna kumathandiza azawo
Abwenze bas ndalamazo 😂😂😂😂❤
Keep it up brother watching from mangamba chikuluma❤
Amandota madya ndalama za ligili😄😄😄
More love from Zed🇿🇲🇿🇲🇿🇲
I loves you Che Mandota
Kkkkkkk Mandota upole moto wamfa. Akupatsa kwawo kuwatawatu....
To be frank, Chemandota ndi osalakwa a Shadolo amafunika kuwadyera.
Prof. keep it up!
M mmm unabwera iweo kuzakhala😅😅😅
Kkkkkk mandoda ameneyo wadya ndalama 😂😂
Che Mandota sudzatheka ndipo iweyo unadza sure
🤣🤣🤣🤣 achisi akuti gwilani miyendo muli speed umu 🤣🤣🤣🤣
Ili bwino kwabasi❤
Achisi number 1 Muthu AFA bwanji kawili😂😂.
😂😂😂😂
Mandota xanaime bwino eeee kkkkkkk 😂😂😂😂
Mfula,,,, Mumatha guys 🤣🤣😂😂 Mandota tayipangeniso post video ya vacancy, please.
Kkkķk aah mandota ndiwakuba mmmmh
Mandota unazaaaaa iweyo
v
continue with good work madala 🔥🔥🔥🥳
Abiliyati mfula🤣🤣🤣🤣
Kkkkkk mandota kukonda kupag plan wekha iwe, taona ashadolo akufuna kukumangitsa
Che mandota kukhomelera chisi 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 akupanga za ena
😂😂😂😂 Chisi waononga chilichonse!
😂😂😂 komatu achisi ndi mandota simuzatheka inuu😂😂😂😂😂😂😂😂
Billiati Mvula anafa thwu sauzande andi faifi, afa bwanji kawiri munthu Billiati uyu😂😂😂😂😂😂😂 Mandota udzafera m'manja mwa anthu iwe😂😂😂
Achisi uluani kuti Amandota akunama
I think in Malawi 🇲🇼 🤔 😕 masakho siworandira ndalama kapena kupepha ndalama anthu kwa Ma MPS but deliver what very will do it in future l mean the MPS, Che Mandota you need to educated people through this comedy .
Kkkkkkk Chisi amvekere mayee!!!! Mandota kuba 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
😂😂 mkwana guys keep it up.Achisi mudzibwelabwela ndi Ashadolo
Am waiting tsiku lina kunte azakhala momwemo
Yaaaaa ndagwilozan nazo kwambili
Kkkk madota chipongwe
Guys inuyo mumakwana heavy
Iwe anakoza 😂😂😂
Hehehe he akadye ku chipala ngati wadwala
Muli speed umu😂😂😂😂😂
Chisi ndiwe number one
Achisi inuyo ndi one😂😂😂😂😂😂 Ndrama ya Ligili wadya yekha mandota....We Loves You Che Mandota🎉 Akita Wafaaa😂
😂😂😂😂😂Ligili tu
Koma ine akitayo ndimafuna asamafe nanga izingothela amaili atawapweteka nawoso pena aziwinako 😂
😂😂😂😂😂 maliro? Kwachitika maliro 😂😂
Nkhani yabwino kwambili ma guys
Chemandota imeneyo phone kkķkkk😂😂😂😂😂😂😂
Iyi nde ndaimva kukoma
Inu ndadolo Che mandota komanso mzanu waligili yo kkkkk Achisi mumakwana
Koma mandota susazantheka😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂🙌🙌🙌
Mandota ndiwe mbava kwambili
Kuva kukoma ndi mandota always ❤
Koma Kankhani ndiwe actor wokwiya...you just act naturally..😂😂😂
🤣🤣🤣 Macholowe Mandota🙌
Kkk
Nice work guys
Ndikhale oyamba ine
Mali mapu wo
Keep it up 😅😅😅😅
Chala man
Kkkkkkkk mkwapuleni basi
Mandota sadzatheka guys😅😅😅keep up the good work ha ha ha chisi naye ndi nkhani zinasotu😂😂
Mmmmm akadyera ameno
👍👍
Kkkkkkkkkkk ndalama za ligili
Talented 🎉
Ndipo mandota sachedwa kugwidwa kkkk 😅😂
Biliati Mvula afa bwanji kawili 😂
Mandota akujowawajowa ku mowa😂😂😂
Mumakwana crew ya mandota
Km mmmmm actor safa
😂😂😂 iyiyi yandiwaza 🔥🔥
Zakhalirana Masaka tu, a shadoro!
Ashodolo😅😅😅 shadow
Mmwejo dolo
Achisi abudula ndiwo za gulu kkkk
Brilliant guys
Mandota 🔥🔥
Mandota anakonza 😂😂😂anyway big up
Amangedwe basi
Sikiliteti wasowatu 😂😂this is nice keep on going
Mandota umakwana
Chilungamu chimafunikadi abele
Mandota sudzatheka umenyedwapot apa😂😂😂
Kkkkkkk mandota umbava bas
Ashadorooo omwewoo kkkkkk
Mandota ŵakusokonasya kwabasi
Tamuchose ntumbukayo sakufikapo aaaaaaa
Kuyankhula kwa bwanji uku @ Frank😳
😂😂 afa kawili nawe😢😢😢
natumiza msg ku innobuild anangoona sanayankhe
Tinadziwa sizitha bwino🤣🤣🤣🤣
Imalakwa owezi
Ashadolo😅😅😅
Ili bhoo kwambili
Koma mandota iwe nditambwali😂😂😂😂😂😂😂