U are a life saver brother ❤️ my question is Munthu ukadulidwa mwendomo kusonyeza kuti ndenthayo inali ku mwendo kokhako ngati mmene imakhalira cancer muja? Komaso akadula mwendomo ndenthayo imatheratu pompo? Anthu ena amati ukamamwa tea pafupi pafupi amayambitsa matenda a sugar ndizoona?
Upitilize kutiphunzitsa zamatenda ena chonde tikutseguka maso kwambiri. Don't translate into english sir, for what purples? Some body said that you should translate this teachings into english, don't do that otherwise you will leave many people behind, thanks
Talimbikitsika, continue
jazzakallah
Allah akudalitsen doc tikuphunzira ndithu Alhamdulillah
Thanks for the tips
Inutu allah azikudalitsani ndithu tikupindula mwaulele
Mumakwana big
Tathokoza kwambili boc taphuzila zambili ambuye akudaliseni🎉🎉🎉🎉
Mumakwana doctor
My favorite tsopano 😂❤
Wow mbambande brasa following
Thanks doctor
Thank you so much, tiuzeninso Za prostate cancer
Zikomo kwambiri 😊
Amwene mulungu akudalisen poyika proglame yi muchichewa ambr tu chingelezi sitimva koma amalawi ozikonda kukakamila zoti sizawo
❤❤❤❤
❤❤❤
Thanx mr boss man
Thank you Doctor, you are really awesome. Continue educating us about health. May God bless you keep you safe
Thanks bigy ndakumbuka pena pake l attended meeting on how we can ldentify kuti awa ali ndi shuga so ndinaiwla now wandikumbutsa
Nankha uli ndi bala kale ndiye akupeza kuti uli ndi shugar bala kuti lipole limatenga nthawi yoyitali bwanji
❤mandota is self-contained man
Bravo and jazaakumullah Khair
Mumakwana my favorite Doc
Koma muziyakhaso mafuso
❤sukulu yachipatala ikufunika tizingophuzila muchichewA
Create special group koma
Mr chikakuda i salute you for your program keep it up
Thank you for helping us may God bless you.
God bless you Dr timakunyadilani
This is so impressive Dr.
Nice explanation doctor keep doing it
You are helping us brother,may Allah bless you ❤
Zabwino zose taphuzila
Zikomo tasiwa
mutiphunzitse za high blood presure
Mwabwera inuyo 🫡🫡🫡🫡🫡
U are a life saver brother ❤️ my question is Munthu ukadulidwa mwendomo kusonyeza kuti ndenthayo inali ku mwendo kokhako ngati mmene imakhalira cancer muja?
Komaso akadula mwendomo ndenthayo imatheratu pompo?
Anthu ena amati ukamamwa tea pafupi pafupi amayambitsa matenda a sugar ndizoona?
Thank you so much
Create a special group for this please our doctor..timphunzre zambri kma takunyadrani😊
Next TB plz tinveso za imeneyi boss
Awesome, kudos to you doctor, may you explain also about heart attack 🎉🎉
This is great.
Thanks Doctor
Thanks alot
Katswiri 🙌🙌
Nice ❤
Ndikukaphunzola za medical
Thanks very much jomba we are proud of you 😊
Zikomo kwambr taphunzira nawo 🙏🙏
Kodi iwe dokotala che mandota, inu kodi apanso mundifuna kuti ine kuti ndikuchiteni inu subscribe?? Mukukhwanatu inu kwambiri.
Bwana inetu ndikufuna nambala yanu ngati zingatheke plz
0999374695
Kodi munthu ukukhala kut mphavu kuchipinda zikuchepa chimayambisa ndi chan nanga ungathane nalo bwanj vutoli
This is nice Doctor Koma if possible can you create another account so that we people can differentiate between Che mandota and Doctor
Bro tapangani account ya Dr chikakuda Ife tazolowela chemandota ukuku 😔
Doctor mutifotokozereso za then dad ya arthritis
Thanks
Nambala sikumaonekatu
0999374695
Tiphunzile bas zimenezi inuyo munabwela
Koma mandota udokotala wanu simungalowese majokosi😅😅😅
Number phone yanuyot Palibe kama ndimafuna thandizo lanu
❤
Tiyakheni ku WhatsApp Doc
Ndaphunzirapo ndithu ndakunyadilani kwambili Dr
Zikomo potipasa ma point osiyanasiyana kumbali ya mantenda ashuga lungu wapeupile
Thanks doctor ❤❤ pitilizani kutiphunzitsa
Ikhale BP
Ikhaledi BP enafe tikuzidadwatu
Upitilize kutiphunzitsa zamatenda ena chonde tikutseguka maso kwambiri.
Don't translate into english sir, for what purples?
Some body said that you should translate this teachings into english, don't do that otherwise you will leave many people behind, thanks
Number yanu bro mando ndili ndi vuto loiwala kawirikawiri
Kodi ine ndnava kut nicotine amapezekaso mumasamba atea nde mwat munthu osuta fodya amakhala pachiopsyezo chotenga matenda asugar nde ife amene timamwa teafe sitingakhale pachiopsezo chotenga matendawa
Number ine sindikuyiwona
0999374695
Dr. number yanu ija sindikuiona plz ndikufuna ya whatsapp
Thank u so much
Zikomo kwambr taphunzira nawo 🙏🙏
❤❤❤❤