My brother nepman mwatipezera mlamu wamwana kale ❤❤❤
Mlelemba akufunika naye kumusanjika manja mkumunenelera kuti sabalamakathendaaaa😂😂😂
😂😂😂 Week yamawa kuli nyekhwe. Mlelemba adzayankhe zomveka otherwise 😅🙌🏾
Enough it’s enough mai shokoshoko😂😂
nepman wagwa mu love tsopano❤😂😂
Nep man ndi katunduso
🎉🎉🎉eyooo tiyen tiyen
Mlelemba palije cha zeru chomene muthu ankhoza kuphuzirapo
Zoonad 😢
Mumakwana nonse 🎉🎉🎉
Nepman ka nyimbo Kali boh myitulusa liti
Madala ❤
Welcome back ladies+gentlemen Madam shokoshoko more fire
Ili bho kwambiri ngakhale mwachedwetsa kutipatsira😂😂
Nepman wagwa mchikondi😂😂😂
Prisca uli ndi m,nyumba mobeba komanso nep man nde mukkhalana heavy osaphwekesa
Kkkkk koma mai shokoshoko ndi mercy ndinu olongolora
Nepuman 🔥🔥🔥 wayaka moto
Pricica wagwa muchikondi ndi rasta 😂😂😂😂 kudya nawo za oyimba basi .
Mr kkkkk wachibwibwi kumamuchenjelela
Yankhani Funso Amulelemba akukufunsan kkk
Hahaha nepman ndi one
Mulelemba ndi pastor wama pastor 😂😂😂😂😂😂
Mmmmmm mandivesa kukoma ❤
Juma wayamba kundisangalasa bwanji 💐,,,Nepman iwe ndee wamuputa Mercy basiiii 😂😂😂
Kkkk azmai ndw mwati mudye zan2 oyimba eheeee
Salute
Muzitumiza mwansanga koma mumabebesa tikumaphuzira zambiri
Kani Pastor Mlelemba aliso ndiziwanda zovula vula? 🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Koma Nepman Ati ndi msamaria
Gyz munakhumudwisa fanzitu bczmwachizolowezi timadziwa kt friday to Saturday timaonera mdyangu bt thanks for ur coming back
Munachedwa bwanji 😂😂
Koma lelemba mupole Moto 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 babathena wanji mumutchulayo 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Km gyz Mulutilakwra Mmene tinayambira kupanga search aaaaaa but we proud u r back
Mai shoko shoko ndi 1 😂😂
Zomachedwa kutulusazo nde mulirapo tele
Nepman ndi Prisca mwandiwaza😊
Mayi chokochoko ndi one waya kkkkkkkkkkk 😂
Nep man be ready for chindeu ndi Franco 😂😂😂😂😂
Comedy ya mdangu yoyambira kumpanda kudzathera konko eeeeeeeesh
😂😂
Ine am waiting for the next episode 😂
A Nepman thumba LA chimanga mulitenga kt😅😅😅😅
Kodi munayi bisa Kuti mdyangu comedy yi😂😂😂😂
Koma shokoshoko ati majamping'i khaso akowo😂😂😂😂😂
Shoko.shoko amandisangalatsa ari ndi chikondi ❤kwabasi ndi Quan
Nep-Man 😂😂😂😂😂 bwinotu bwino 😊
Achedwetsadi😊 nice for bringing it
Kkkkkkkkkkk koma banja la Shoko-shoko
Nep man boot ngat yanga bola ndikaipezeko ku den isasowetu
Prisca's house is so smart
Kkkkk prophet wagwidwa 😂😂😂
Koma Queen kuyankhula uzidziwa paliponse kumangodulapo
Nepman phiradefiya mdyangu umakwana
Queen zovala zatheka njira dairy kusamuka😅😅😅
Koma chuma ndi machine eti akugogoda ndani chuchuchuchuma shoko shoko bwanjiso 😂😂😂😂😂 chuma tatu tu tu tu tu lukami😂
Bola lero munasowa abale😂mai shokoshoko simuzatheka😂
NepMan ulemu wanu .Pitilizani big man😂
kkkkkkkk sono iwe ukundiyang'ana choncho bwanjii 🤣🤣🤣🤣🤣🤣 shokoshoko kkkkk
Ndakunyadilani, koma please muzitumiza mwasanga. Mukumachedwesa
Ifeso tikudabwa akutumiza mochedwa loko mfumukazi sanatumizebe mpaka pano
Iyi mwapha guys 100%
Nepman mo fire🔥 🔥
Ndimaona ngati yathatu ine😂😂😂
Nepman anabwera😅😅😅😅 ft mercy
Koma mayi shocks ndikatundu kkkkkkkkkk
😂😂😂😂😂Nepman wapeza mukukhalanatu 😅😅😅😅
😂😂😂😂 Kma 😂😂😂 can't wait for another episode
Mwatitumozira mochedwa kwabas week ino chonde mutitumizire tinaisowa mdyangu
Lululuuuuu koma yah poloti iyi tikhonzekere kulelesa chindewu kuja mayi shoko shoko anyanyala apita kumudzi kumusiya mphwawo ashoko shoko sanasatire mbali inayi nep man akuhopera kwa prisika Kodi fulanko sazabwera ? Mayi n'dyangu akukayika za mwana waqueen akuti si wagani nawo amulelemba amakati kwa prisika? Kuja chuma wamusiya mercy m'malere kuchedze kwathera panjira tikati tisuzumire mwachidwi pa poloti iyi pazachitika chachikulu mpaka police idzabwera ❤❤❤❤❤❤ buuuuu
Ndichifukwa chake anayicha kuti mdyangu 😂😂😂
Ati chindeu 😅😅😅😅
Apa bola mwaitha mumatimvesa kukoma guyz pitilizani kubebesa
Muli bho koma mwayamba kuchedwesa
Koma chi bag cha queen
Munasowa guyz ndipo tinayamba kudandaulatu Ife
Koma akazatulukira Franco ndi Mwanawamkango kuzakhala zotani Chuma ndi Nepman......
Ife lachisanu pa times 9 koloko sitinaonele mwasitha nthawi??
Mlelemba aziona 😂😂😂
Chuma ndi member kkkkkkkk
Mdyangu more
Mwayamba kuchedwesatu sono 😢
Tina kusowani ma gyz
Mai shokoshoko akanabeleka wawo
😢😢😢😢😢😢 Queen iiiiiii
Sinthani #link yo nafe tipange download Miss-F-Suya
Mayi shokoshoko ndi kawawa
Contraceptive yomweo bas eish kwacahema tu😅😅😅
Ati anaphedwa bwanji
Ife tingoti pepani pokupatsirani mosemphana ndinthawi...Koma zikomo pitilizani kutsatira channel ichi kuti mupitilize kuphunzira,kudziwitsidwa ndikusangalala.❤❤❤❤❤❤
Zimatha
Mwatichedwetsera 😢
Nane ndimadabwatu
Ndimaona ngati yanthatu😅
Nep 😂😂😂
Kodi mwasitha tayamba kuwonela lelo ngati mfumkazi?ife last week timadikila 😊
Where have you been guys. We started to worry 😢. We are glad you're back.
😂😂😂, tavutikatu 😅
Koma Chakwela nde akutichedwetsatu
Mumakwana gys ❤❤❤😂😂😂😂
Mulelemba ndi Nepman ativuta
Nepman agwila
Priscila mugwiritse nepuman akusamala
Tinaisowatu kkkkkkk❤️😂😂😂😂😂
Chilungamo masiku ano muchedwa
😃😃😃😄
Nepboy wagwira msewu

NepMan ulemu wanu .
Pitilizani big man😂
kkkkkkkk sono iwe ukundiyang'ana choncho bwanjii 🤣🤣🤣🤣🤣🤣 shokoshoko kkkkk
Ndakunyadilani, koma please muzitumiza mwasanga. Mukumachedwesa
Ifeso tikudabwa akutumiza mochedwa loko mfumukazi sanatumizebe mpaka pano
Iyi mwapha guys 100%
Nepman mo fire🔥 🔥
Ndimaona ngati yathatu ine😂😂😂
Nepman anabwera😅😅😅😅 ft mercy
Koma mayi shocks ndikatundu kkkkkkkkkk
😂😂😂😂😂Nepman wapeza mukukhalanatu 😅😅😅😅
😂😂😂😂 Kma 😂😂😂 can't wait for another episode
Mwatitumozira mochedwa kwabas week ino chonde mutitumizire tinaisowa mdyangu
Lululuuuuu koma yah poloti iyi tikhonzekere kulelesa chindewu kuja mayi shoko shoko anyanyala apita kumudzi kumusiya mphwawo ashoko shoko sanasatire mbali inayi nep man akuhopera kwa prisika Kodi fulanko sazabwera ? Mayi n'dyangu akukayika za mwana waqueen akuti si wagani nawo amulelemba amakati kwa prisika? Kuja chuma wamusiya mercy m'malere kuchedze kwathera panjira tikati tisuzumire mwachidwi pa poloti iyi pazachitika chachikulu mpaka police idzabwera ❤❤❤❤❤❤ buuuuu
Ndichifukwa chake anayicha kuti mdyangu 😂😂😂
Ati chindeu 😅😅😅😅
Apa bola mwaitha mumatimvesa kukoma guyz pitilizani kubebesa
Muli bho koma mwayamba kuchedwesa
Koma chi bag cha queen
Munasowa guyz ndipo tinayamba kudandaulatu Ife
Koma akazatulukira Franco ndi Mwanawamkango kuzakhala zotani Chuma ndi Nepman......
Ife lachisanu pa times 9 koloko sitinaonele mwasitha nthawi??
Mlelemba aziona 😂😂😂
Chuma ndi member kkkkkkkk
Mdyangu more
Mwayamba kuchedwesatu sono 😢
Tina kusowani ma gyz
Mai shokoshoko akanabeleka wawo
😢😢😢😢😢😢 Queen iiiiiii
Sinthani #link yo nafe tipange download Miss-F-Suya
Mayi shokoshoko ndi kawawa
Contraceptive yomweo bas eish kwacahema tu😅😅😅
Ati anaphedwa bwanji
Ife tingoti pepani pokupatsirani mosemphana ndinthawi...
Koma zikomo pitilizani kutsatira channel ichi kuti mupitilize kuphunzira,kudziwitsidwa ndikusangalala.
❤❤❤❤❤❤