Awayana😂😂 do not say kuti anthu sadawerenge ayi. Dzithu zina oro mutadzikhothetsa bwanji koma idzi ndi dza straight forward. Ngati kuli chibazi idyani chabe koma ft p nt play with chilungamo
We respect you, Times reporters but you are going overboard by pretending as if you don't know the realities of the accident. We said ife Kuti these investigators are prone to manipulation and here you are with half baked report. Anthu amakagula fertilizer Ku butchare nde angakapeze ofufuza achilungamo andege?
Mmm koma Mw pena pake muzikhala serious muuza bwanji asilikali kut azilondela chi wood cha ndege yet munakanika kuuza asilikaliwo kut afufuze ndege idakali yamoyo that nonsense ife si a Mw a 1964
Podeman next time osazaika chithuzi cha brain PA program yoti brain yo sanakhale nawo chifukwa anthu ambiri akangoona pic ya brain nkhaniyo amaidutsa osatsekula chifukwa salankhula bwino
MCP inapha chilima ndianthu ena Aja basi palibeso wa MCP akunena zolongosokapo apa
Mcp you know the truth
Ndege Inyamuka Bwanji Opanda Black Box Ndi Transponder? Report Yabidza Limenelo
Kodi akamati yopanda zipangizo inabwela choncho ndengeyo ,anachotsa black box ndani
Dziko lapansi ndila chabe tiyeni tiyang'ane kwa mulungu basi chifukwa wina aliyense akungolankhula chabe zomwe akumva mmutu mwake
Report labodza limenelija bwana.
1.Flight recoder adachotseranji?
2.Ngozi yanji yomamuvura munthu dzovala,nsapato,sokosi,tayi,jombo?
3.Chifukwa chani pa ulendowo panalibe wa mcp?
4.Kodi ubale wa Chilima ndi Chakwera udali bwino kapena ayi?
5.President adatiwuza kuti ndege idabwezedwa ku Mzuzu chifukwa cha nyengo sinali bwino lero Report likuti ndege sidafike ku Mzuzu ndipo munalibe communication.
Nthawi ikufika mudzakagwira murder a Chakwera.
Awayana😂😂 do not say kuti anthu sadawerenge ayi.
Dzithu zina oro mutadzikhothetsa bwanji koma idzi ndi dza straight forward.
Ngati kuli chibazi idyani chabe koma ft p nt play with chilungamo
Zoona
We respect you, Times reporters but you are going overboard by pretending as if you don't know the realities of the accident. We said ife Kuti these investigators are prone to manipulation and here you are with half baked report. Anthu amakagula fertilizer Ku butchare nde angakapeze ofufuza achilungamo andege?
Ndege inali ndichina chilichonse choyenerera tisamanamizane.ndikugwirizana ndizoti ku army kuli madolo a engineering.
THE MALAWIANS WANT TO KNOW WHAT OR WHO REMOVED CHILLIMA'S CLOTHES??. WHY CHILLIMA. WAS FOUND
NAKED????
Palibe chomwe mukukamba chanzeru pamenepo muthu munapha bas
ngati mwasowa nkhani zokamba musamabwele pano ndi nkhani zoposazo. ife chomww tikudziwa ndi chakuti a chilima anachita kuphedwa
Mmm koma Mw pena pake muzikhala serious muuza bwanji asilikali kut azilondela chi wood cha ndege yet munakanika kuuza asilikaliwo kut afufuze ndege idakali yamoyo that nonsense ife si a Mw a 1964
Komanso anamulora bwanji wachiwiri kukwera ndege imeneyiii?
A Kamkwatira,musamanamizane ndege ija anakwerapo Mnangagwa.sakweze visiting predident ndege yoperewera zipango .chilungamo ndichofunika.Ndege imene ija pachilungamo pake inali yoyenera pamseu.zipangizo zinachotsedwa .anthu aja anachita kuphedwa..pamene amkaimitsa kufufuza mkuti asanamaliza kuchotsa zinthuzo ndi kupha anthuwo.
Kwenzaramba is talking sense,
Kunkuyu! Chilima munamuyedzeka , ndale mumapanga usiku
Bodza kwambirii kunkuyu
From Mr Jokes
From mr jokes
Lipoti lochita kukakamiza kuti lituluke
A Times nanunso zikuoneka ngati mwayamba kubakila B oma mafunso ndiyambili opanda mayanko
Anthu opusa inu munagudwa ndi chikangawa
Malawians knows truth no matter what chakwela can say to Malawians but we know chakwela is killer
Iwe ukumkuyo ndiwe mbuzi ya munthu 😢😢😢😢
Nde choonongera ndalama za ife osaukafe ndi chani if you know that iwo angotiuza za technical
Times timakudalilani komatu apa mukuwoneka kuti simukuyankhula zotipatsa chilimbikiso why??? Koma ndalama why???
Podeman next time osazaika chithuzi cha brain PA program yoti brain yo sanakhale nawo chifukwa anthu ambiri akangoona pic ya brain nkhaniyo amaidutsa osatsekula chifukwa salankhula bwino
Zamanyi bs akupha inu 2025 mudzakafela ku prison agalu inu
no media house is asking about zovala zinavuka zija
Akuwuza ana? Ifetu sitinalezere ngati ngati mwadyapo zanu izo
So you mean times is the best for commenting repots
Ndege 11 kikiki kunkuyu, iwe mumafufuza Chilima ndi torches
Kudikila ndege ya ku Zambia
Aaa kunkuyu
Black box transponder zinapita kuti ngati mu ndege mulibe
Eee komatu anthu ndiotsekuka mmitu eee this tym around
People say you have started showing side
Ndie kuti zija akunena anthu zija ndizoona kuti Bryian komanso Kamkwatira mukulandira ndalama kuchokera ku boma.Nkhani ya ndege ife tikudziwa kuti mcp inachita kupha anthu aja.
Kumkuyu akudifenda boma ndicholinga choti lisapeze mabvuto
Ndege 11 koma nankha mumagalira za ku Zambia bwanji?
Kodi akamati yopanda zipangizo inabwela choncho ndengeyo ,anachotsa black box ndani?
Osamapita mmbali pokamba nkaniyi HIT THE NAIL ON THE HEAD period
Fuso ndilakuti black box anachosa ndani chifukwa ndege iliyose mumankhala black box
Times ndi manyaka
Sad
Ma bans basi a times muzikala ndimanyazi mwamva
From Mr Jokes