Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Bambo analemera nazo nyimbo iziMwanaso akudya nazo bwinoMwana wakeso adzadyera momwemuBambo wanzeru adzisiyila ana ake poyambilaGreat!
That's sprit osati Ena amagonyozawa
Ndipo ife ana athu anangotengelako Asthma
Uli bho John .. I like the element of dancing you are featuring it's spicing and make u super
Mawu ngati Bambo weniweni eshhh zembani siyidzatha
And it will makes kut zembani isazathe
akumayesetsa mwanayu eti..keep up good dance
Mr zembani Ali ndi nyimbo zake, chonde muzimutsatira pofuna kudziwa osati kunyoza😂😂😂
Rasta wathu wathu uyuuuu opanda rocks😂😂😂😂😂Umakwana mtchana
Jonny u r great...like father like son zamphanvutu izi
Excilente music bradas nota 1000 tete anif
Chi m"malawi sichilemphela kumeza chifukwa pachina chilichonse azayamba kuyimba nyimbo zake akazamphya bwino bwino
Good job Mr Zembani 👏 Omar 4rm Mangochi bomamo
Muito obrigado ao malawi
mwana wa mkango ndi mkango amene
Hahahahah he is so funny.he can chase the crowd
Big up my bro
Soja ndi soja aiseee mmm kope ndi kope
Mmakwana Mr Zembani
Big up mr zembani
Nice
Mr Zembani has the energy
Keep fire burning
Anyway great
Uli bho mfana ajelasi onse ngwooo
He can dance,
The lad should not ride on Daddy's back. He should develop his own music & Brand
He has he's own songs
Ok. I didn't know
Komaso sizikugwirizana ife nde zimatikomela komaso nyimbozo ndizabambo ake not amkolo ake
True my bro, I was think so yooo 😂😂😂
Mwana wake omuuza zochita ndinu? Nafe tiyeni tipezere ana anthu zochita tisamalimbane ndi ana anzathu
Akukula ayambe kupeka zake nyimbo. Ayimba za madala ake mpaka liti??
Watch out for his own titled wanga
kkkkkkk chilungamo kaya iyyaaaaa
Ali nazo zake
Ndi madala anu?
Inu osapeka yanu bwanji
Bambo analemera nazo nyimbo izi
Mwanaso akudya nazo bwino
Mwana wakeso adzadyera momwemu
Bambo wanzeru adzisiyila ana ake poyambila
Great!
That's sprit osati Ena amagonyozawa
Ndipo ife ana athu anangotengelako Asthma
Uli bho John .. I like the element of dancing you are featuring it's spicing and make u super
Mawu ngati Bambo weniweni eshhh zembani siyidzatha
And it will makes kut zembani isazathe
akumayesetsa mwanayu eti..keep up good dance
Mr zembani Ali ndi nyimbo zake, chonde muzimutsatira pofuna kudziwa osati kunyoza😂😂😂
Rasta wathu wathu uyuuuu opanda rocks😂😂😂😂😂
Umakwana mtchana