New track from Joseph mkasa OWINA ANAWINA KALE

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 15 сен 2024

Комментарии • 49

  • @ManuelMalunga-fl3vq
    @ManuelMalunga-fl3vq Год назад

    This is really educative and master class keep it up our on Minister wa amphawi umatha zedi koopsa ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @ManuelMalunga-fl3vq
    @ManuelMalunga-fl3vq Год назад

    Nkasa he's Legend ❤❤❤❤❤❤

  • @davidmaulana9277
    @davidmaulana9277 4 года назад +4

    Nkasa alibe size pa Malawi kumbali ya nyimbo kapena Luso

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 2 месяца назад

    Tikananvera zamunyimbo iyi ntbawi imeneija panopa Malawi Ali pabwino zinthu zikutchipa Chilima ndi anthu Ena ajaaa alipo komanso Malawi atatukuka koopsa Zedi Komanso njala kulibeko

  • @brightkumandamwale7662
    @brightkumandamwale7662 4 года назад +2

    Song of the month. Very true big up mkasa

  • @lonelykasinja9043
    @lonelykasinja9043 4 года назад +3

    Weather they give u money or not but the massage is good to every Malawian, we struggle to get chitukuko in the communities, nde tidziphwanyeso chifukwa cha anthu andale🙄🙄🙄🙄

  • @gadaffi.y.chimbeta5858
    @gadaffi.y.chimbeta5858 4 года назад +1

    Owina wawina kale basi 😆😆😆😆 we proud with u mkasa, away from Japan

  • @ruthmalunga2147
    @ruthmalunga2147 4 года назад

    Nkasa your the best owina anawinadi kale kwinaku anthu angozivutitsa basi, kodi ngati anthu akuononga choncho kuwapasa mpando sazagulitsayi Malawi yense? Nkasa your the best kuononga zinthu sikungapangiseyi kuti awine chisankho Ndipo ulamuliro sumafunayi mphamvu koma nzeru basi. Owina anawina kale

    • @ManuelMalunga-fl3vq
      @ManuelMalunga-fl3vq Год назад

      Ndi awa akuononga dzikoli brother Sinanga anachita kulowa mwaupo momgolanda Boma brother

  • @yusufbalakasi419
    @yusufbalakasi419 2 года назад

    Ndiwebwanabasi lusoulinalo

  • @johnthomas4284
    @johnthomas4284 4 года назад +1

    Very nice song i like it

  • @stephanongalaukabandasteph2807
    @stephanongalaukabandasteph2807 4 года назад +1

    from cape town ngati tikuphwanyadi misewu ndiye phindu ndichiyani anthu ndiwolemera kale

  • @tobiasnyirenda2023
    @tobiasnyirenda2023 4 года назад +2

    Zopusa, Nkasa dyera basi. Akawina Chakwera adzaimba yina, angofuna kudya nawo. I know this guy. Am following from Stuttgart, Germany..

    • @brucewarchild2156
      @brucewarchild2156 4 года назад

      Uli kwa Adolf how can you follow what Malawi is going thru... Via Facebook?

    • @ManuelMalunga-fl3vq
      @ManuelMalunga-fl3vq Год назад

      Ndiopepera uyu mutayeni yekha akuti Ali Ku Germany simisala imeneyi aaaa

  • @stephanongalaukabandasteph2807
    @stephanongalaukabandasteph2807 4 года назад +2

    ngati uli pachibwezi akukuomba makofi kodi ungapitirize kumanga naye banja?

  • @frankmazibuko1023
    @frankmazibuko1023 4 года назад +2

    Vuto ankasa mulibe mbali mumangoti uku chakoma uko chakoma

  • @giftchale672
    @giftchale672 4 года назад +3

    Very true mkasa

  • @beinhardkausiwa7107
    @beinhardkausiwa7107 4 года назад +1

    Mwaonongeranji zitukuko ZANU zomwe?????owina anawina kale bas ndipo yehova kumwamba anasainila kalekale

  • @blazeafrica6429
    @blazeafrica6429 4 года назад +2

    Amudyesa bazi ameneyo mkasa

    • @daviebanda7477
      @daviebanda7477 4 года назад +1

      From America akunena zoona kuononga dziko lanu lomwe

    • @blazeafrica6429
      @blazeafrica6429 4 года назад

      Malawi ndichoncho

    • @RiteRoderick
      @RiteRoderick 2 месяца назад

      Akunena Chilungamo kaaah Makani anu odana ndi Chilungamowo ndiizi Malawi wathapo Chilima kuphedwa

  • @fanizochataika9768
    @fanizochataika9768 4 года назад +1

    Mkasa amudyetsa CHIOBAMA UYU, alira pompano awa

    • @ManuelMalunga-fl3vq
      @ManuelMalunga-fl3vq Год назад

      Inu panopa Ndie how do you feel? Munthu Wina wawina Ndie mukukayamba kuphwanya Zinthu Kumeneko ndikukoza or kuononga? You need to think twice before you vommit that nonsense okay

  • @Littlefair7
    @Littlefair7 4 года назад +1

    Owina awoneka pa 19 osati za tippex

  • @chesterphiri7523
    @chesterphiri7523 4 года назад

    Can you sing this now Mkasa????? Umphawi siwabwino ayi

  • @alickwilsonthom7007
    @alickwilsonthom7007 4 года назад

    Zoonadi Phungu wa Osauka

  • @rakiticnicco6483
    @rakiticnicco6483 3 года назад

    Dada mumantha

  • @bestonjoseph2193
    @bestonjoseph2193 3 года назад +1

    Ankasa mwafa nayo 🤣🤣🤣🤣

  • @patrickmagombo4921
    @patrickmagombo4921 4 года назад

    Mkasa ndi mambala

  • @emmanuelmagreta4191
    @emmanuelmagreta4191 4 года назад +2

    😂😂😂😂 auze ase

  • @warrenmwambazi8342
    @warrenmwambazi8342 4 года назад +3

    True

  • @Emmanuel-gs1vk
    @Emmanuel-gs1vk 3 года назад

    Mphungu Joseph nkhasa Striked again

  • @adamchilombo4852
    @adamchilombo4852 3 года назад

    Kkkkkk

  • @brucewarchild2156
    @brucewarchild2156 4 года назад

    Kkkkkkkkkk nkasa sadzatha basi kkkkkkk

  • @manzykawika8988
    @manzykawika8988 4 года назад +2

    Kkkkk aaaaa

  • @charlesrichard8667
    @charlesrichard8667 4 года назад +1

    I mean really?

  • @zionsdaughter2391
    @zionsdaughter2391 4 года назад

    Ine ndikanakhala mkasa nkana deleter video iyi🤣🤣🤣

  • @dennnisjames6489
    @dennnisjames6489 4 года назад +2

    Galu

  • @moosathompas9987
    @moosathompas9987 4 года назад +3

    I like the beat but I don't like the message who else agree with me

    • @brucewarchild2156
      @brucewarchild2156 4 года назад +1

      You don't like to be told the truth even when you are wrong then you got a problem