AMIPINGO ZAWAVUTA MWA NYOO!!!

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 17 янв 2025

Комментарии • 55

  • @Elias-q7n6b
    @Elias-q7n6b 22 дня назад

    Mr Susa tithokoze pa mawu amene mwapeleka ku Malawi mulingu akudalitseni ndine Elias

  • @mathewssimbi3052
    @mathewssimbi3052 22 дня назад +1

    Azitumikiwa achokera Ku Church yathu ya Chimwendo Evangelical Banda

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 22 дня назад

    Muft wake uti mumadziwa Muft koma mukupembedza chbwana anthu inu ilove Muft Merk from Zimbabwe

  • @DjshukulanGift
    @DjshukulanGift 22 дня назад +1

    Mcp ndiyopusa malo mothan ndimavuto omwe Ali Malawi muno akulimban ndikumagula athu kt azimubakila ,mmm

    • @Stretor
      @Stretor 22 дня назад

      Ndipo MCP ndiyonvesa chisoni kwambili

  • @LucyKulemeka
    @LucyKulemeka 22 дня назад +1

    Ngati akulephera kudzifotokoza bwino ndiye kuti ndi azibusa azikwanje amenewa

  • @AllanBiseck
    @AllanBiseck 22 дня назад +3

    Mbuzi zawanthu zikukanika kutchula mipingo imene akuchokera ,why? Angowatola awa agalu

  • @ImedKunje
    @ImedKunje 22 дня назад +1

    Izizi ndizitsilu zapochela ife tilipa mbuyo pa nsusa

  • @chrismatemba556
    @chrismatemba556 22 дня назад +1

    Kutiyesa kuti ndife opusa.😅. You have been given money, just eat it and enjoy yourselves.

  • @Dalsonchimlomo
    @Dalsonchimlomo 22 дня назад

    Msusa ndi mtsogoleri wamulungu enawa ndi adyera obisa chilungamo chifkwa chofuna ndalama kuchokera kwa andale ndipo kwa ife loport lija ndilosaveka pokhapokha atayankha mmafuso omwe tili nawo okhudza ngozi ija.

  • @CatherineMsaya
    @CatherineMsaya 22 дня назад +4

    Abusa a zikwanje asatinamize msusa is true man of God chilima he can not die like that mind you fake pastors we want to know actually what happened to chilima and others to die it was not accident cooked plan

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 22 дня назад +1

    Si atsogoleri ampingo amenewo koma otumidwa ndi satana mizimo yoipa yawakuta anthu amenewo apanga musokhano watola nkhani anamuvula zovala chilima ndi ndani ma walakwa chani bishop? Anaswiswiri nose anthu akumudima inu

  • @AndersonBishop-i2t
    @AndersonBishop-i2t 22 дня назад

    Sheikh palibepo pamenepo ndi anthu azikwanje amenewo ndiposo machende awo

  • @francistsutsu4811
    @francistsutsu4811 20 дней назад

    Ndiye akatolikawo akufuna kuti utsogoleri uchokere ku mpingo kwawo?

  • @JafarWiati
    @JafarWiati 22 дня назад

    Azibusa ake ometa mmbali ngati anyamula tebulo 😂😂😂😂

    • @Stretor
      @Stretor 22 дня назад

      😂😂😂😂😂 kuonaso bwino akuyankha mozemba kwambili

  • @mcrayansimwaka8890
    @mcrayansimwaka8890 22 дня назад

    Ngati akuzikayikira kuzitchura okha, angakhere asogoleri . Asasambawa palibe alankhula apa

  • @LucyKulemeka
    @LucyKulemeka 22 дня назад

    Azibusa ometa m, mbali azikwanje mukulowera kuti😂?

  • @JulioChiwalo-t4f
    @JulioChiwalo-t4f 22 дня назад +1

    Kuzibisa kokhako ndi uthenga wokwanira kwa a Malawi kuti amipingo amenewa akufuna ndalama ku MCP

  • @chisomositima665
    @chisomositima665 22 дня назад

    Ma kolalala mungopatsa aliyenxe et

  • @SinoliaEphraim
    @SinoliaEphraim 22 дня назад

    Anthu opanda mipingo Amenewa opemphapempha antsusa sanalakwe

  • @KelvinBandah-o5v
    @KelvinBandah-o5v 22 дня назад +1

    Don't think we stupid chakwera learn from others you may have power today but time will be gone malawians you are persecuting today will be essential on 16 September 2025

  • @PatrickMaluwah-bx9or
    @PatrickMaluwah-bx9or 22 дня назад

    If they were really men of God they would have introduced themselves .

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o 22 дня назад

    Asusawo analakwa chifukwa iwowo ngati akuziwapo kanthu akadanena chifukwa ofufuzawo anapeleka mpata kuti yose amene akuziwapo kanthu abwele azatiuze lelo lipoti latuluka akuti sakukhutila iwl anali kuti ndiye koskoneako koma ndi abusa

  • @MustafaJafali-c3q
    @MustafaJafali-c3q 22 дня назад +1

    Msusa sanalakwe

  • @YusufLiffah
    @YusufLiffah 22 дня назад +1

    😂😂😂

  • @EdwinZiwa-x2g
    @EdwinZiwa-x2g 22 дня назад +1

    Koma azibambo inu muli ndi mzelu koma mapazi amanu nonse agalu inu

  • @Khadija-q9r
    @Khadija-q9r 22 дня назад

    😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂akuti azibusa osaziwika

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf 22 дня назад +1

    azibusa ake siawa ndi ajera okha okha

  • @patriciajangaza675
    @patriciajangaza675 22 дня назад

    Abusa a pansi anyanja inu zopusa

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 22 дня назад +1

    Athu amenewo ndi mbuzi zawathu asusa bwanji akunena zoonadi osati makape enawa akuyakhurazo chakwera wakupasani ndlama kuti mumuteteze thawi ndi nyengo ikwana pompa mcp ndichipani chakupha

    • @Patrickmanyozoproperties
      @Patrickmanyozoproperties 22 дня назад +1

      Koma azibusa enawa eeee moto uliko kumwamba kubitsa chilungamo chifukwa Cha ndalama kkkkk mulungu akukuonani

  • @MphatsoLuka-gn3lr
    @MphatsoLuka-gn3lr 22 дня назад

    Chakwela anachokela koko ku church chili MA anati osakhulupilila azibusa

  • @FrankNedson
    @FrankNedson 22 дня назад

    Koma akt ndi Abusa munthu wameta mmbali aaaaaaaa Koma dziko lathu likulamulidwadi ndi satana Chakwera ndi amzake

    • @JafarWiati
      @JafarWiati 22 дня назад

      Eti eti kumeta ngati wanyamula tebulo😂😂😂😂

  • @thomasmkwinda
    @thomasmkwinda 22 дня назад

    Azibusa opepela

  • @SilaimanLoja
    @SilaimanLoja 22 дня назад

    Mwanya ndalama inu

  • @Wezzie-j2v
    @Wezzie-j2v 22 дня назад

    Makape azibusa awa mbuzi

  • @StalnLossan
    @StalnLossan 22 дня назад

    Azibusa adyera

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 22 дня назад

    Akulu akulu anyamata azikwanje awa. MCP ikungodzipanga decampaign chifukwa chiani? Anapha Chilima adadzichotsera mavoti, panonso atuma abusa azikwanje kuti anyoze ma bishop akuyiwala kuti kutukwana awa ndikudzichotsera mavotinso

  • @HenryMziwanizga-p1d
    @HenryMziwanizga-p1d 22 дня назад

    Azibusa wogulidwa inu chokani afiti inu mukubisalila mumpingo basi

  • @PAULMABVUTO-r9d
    @PAULMABVUTO-r9d 22 дня назад +1

    Machede awo asatinyanse tikadalilabe pano

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 22 дня назад +1

    Chakwera ndi amene warephera ngwirizano wake ndi chirima ndiye ndiye mbuzi zina zikumuyikira crocodile kumbuyo nonse muzayakha

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 22 дня назад

    M'busa ometa mbali koma satan chita manyazi agaru nonse

  • @AlexKaunda-w7l
    @AlexKaunda-w7l 22 дня назад

    Abusa opusa

  • @LevisonDaka-f5x
    @LevisonDaka-f5x 22 дня назад

    You remember what was the report from Malawi defense Valentino phiri he said it was not easy to go and search but look at the picture there's no more trees let's us say the truth this is was planned move

  • @Mrjafman
    @Mrjafman 22 дня назад

    Ghost pastors

  • @MikeMuwalo-h1r
    @MikeMuwalo-h1r 22 дня назад

    Inuso munali gulu lopeleka Chilima kut aphedwe azibusa onse omwe muli apa mukuzitcha kut okhudzidwanu

  • @bisweckchimphamba8497
    @bisweckchimphamba8497 22 дня назад

    False prophets

  • @BlessChilita
    @BlessChilita 22 дня назад +1

    Akatolika sakukondwera ndi a Chakwera chifukwa ndi assembly's

    • @petrokagona1708
      @petrokagona1708 22 дня назад

      Anavula zovala anthu aja pa ngozi ya ndege, ndi ndegeyo? Pamenepo simumafotokozapo bwino bwanji?

    • @EnockMasiye-e4j
      @EnockMasiye-e4j 22 дня назад

      Iwe umuuwuze chakwera wakoyo abwerese black box

    • @BlessChilita
      @BlessChilita 22 дня назад

      @EnockMasiye-e4j chilungamo kuwawa

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms 22 дня назад

    Azibusa amene akusutsana nd msuna ndaye ndiwakupha