Tsono a UTM musatinyasepo manganya akufuna chipani chomwecho chkhale chake, Mtumbuka akufuna chkhale chake, kambala chkhale chakeso mapaz anu tangothetsan chpanicho bas!!!! Inuso a MBC mwapezaso zochta kuipitsa mbiri ya UTM bas chi TV chanucho adzkaonera yekha chakwera kukasya manyi anu nonse ma staff a mbc mmaombera mmanja zopusa, mafuta akusowa muzlimbikitsa munthu ku ma whistle stop,alimbikitsa bwanj ulimi chfetereza wakweza ndnu agalu nokhanokha
Tangovomerezani amutumbuka apo mungosokoneza zachipani nthawi yatha kale just let kabambe proceed komaso ku wina sizimatengera kuti unalimokale koma ku tchuka kwa munthu ndi ntchito zake for example kukula mutu sizelu
Komadi anapita ku school amtumbukawa kuberedwa mavoti onsewo kkkk mumschuluka matama kumawauza anthu za school yanu oxford ya chan steight to the point
Abusa omwe achita recommend pa MEC chair ndiwopusa and akudziwapo kanthu ineso ndi CCAP Christian koma chomwe mungadziwe a Malawi pano CCAP simpingo koma Business kuteroku azibusawa alandira ndalama mmene Malawi aliri pano sitikuyenbekeza kuti abusa omwe amadzitcha kuti ndi atumiki a Mulungu angamayikire kumbuyo zopusa zomwe Mec ikuchita
Apa ndi nthawi yoti mupite musogolo ndi chipani mwayamba kulimbana mesa usi amanenena koma inu kufuna ndalama ndi izo mwagwa nazo wanzeru ndani apa kkkkkk
Dr kabambe , seek thee first the political kingdom and the rest shall be given to thee
Vomelezani a Mtumbuka kuti mfundo mulibe and let's support Dr. Kabambe to promote our beloved party UTM
Titizalolaso zimenezo Dr Dalitso kambabe woyeeeeee❤❤❤❤❤❤❤
Tsono a UTM musatinyasepo manganya akufuna chipani chomwecho chkhale chake, Mtumbuka akufuna chkhale chake, kambala chkhale chakeso mapaz anu tangothetsan chpanicho bas!!!! Inuso a MBC mwapezaso zochta kuipitsa mbiri ya UTM bas chi TV chanucho adzkaonera yekha chakwera kukasya manyi anu nonse ma staff a mbc mmaombera mmanja zopusa, mafuta akusowa muzlimbikitsa munthu ku ma whistle stop,alimbikitsa bwanj ulimi chfetereza wakweza ndnu agalu nokhanokha
Vuto ndi boma likufuna kusokoneza chipani cha utm teroko akufuna ena apite ku court kuti apanga cancel conversion monga muja adachitira 2020,muchita mantha ndinkabambe
Kodi atumbuka experience alibe fundo alibe as well chikoka alibe ndiye njila zake ziti zingawinisile let's support to kabambe
Let's support the only true Malawi's coming president
Amutumbuka fundo nazo nazo mulimbe. Don't destroy the UTM. Fundo za akambambe
Kkkkkkk fundo zake izi ,,, achilima anali azanga , aa chipanichi tinayambisa ndine aaaaa ine ndimuthu wa business aaaaaa koma tamalakhulani zoveka
Maesa amati Mtumbuka ndiophunzira ndie umbuli akuchitawo bwanji ngati amakonda utm ampange support Kabambe
Angoomeleza...Mesa ankat azapangana support amene atawine...komaso ngat ayamba izo nde chipani chpasuka
Don't hate Kabambe, he is deserve to take this position
MBC ndiyandale yopoila. UTM more 🔥 🔥
Nkhani sikukhala mu ndale koma Fundo zomwe amauza anthu osati kunyozana,,Remember SKC anapeza ma vote 1 m+ kuposa zipani zina zakale
Inunso a HOT265 mukakakamira izizi zowonetseratu mbalizi, mufoila. Ine sindiyerekeza kuonera izi. Palibe chomwe tingatolepo
Koma mcp ikudabwitsa bwanj michael usi amaneneratu kuti UTM IKHALE MU ALLIANCE ...NDI MCP .NDE AKUFUNA KUGULISA CHIPANI NDI NDANI
Kodi zomwe amanena zija zoti omwe aluza akuyenera kupanga suport yemwe wawina,ndiye amafuna kuti awine iwo kuti anzawo awasapote
Mwachedwa achakwera,zilongezani,Chaka chamwa , chanu palibe
Tangovomerezani amutumbuka apo mungosokoneza zachipani nthawi yatha kale just let kabambe proceed komaso ku wina sizimatengera kuti unalimokale koma ku tchuka kwa munthu ndi ntchito zake for example kukula mutu sizelu
Kabambe woyeeeee....mcp, Kaya mbc zanu izooo
Vomelezani a Mtumbuka kuti munaluza anthu sanakufuneni, afuna Mr Kabambe
Exactly!!!
Takonda kabambe vomelezani bas Mr mtumbuka anthu sanakukondeni
😂😂😂 ndalama zobweleka sitipangila ndale apapa wabetsa basi ubweze katapila before kulandidwa chumachako 😂😂😂mtumbuka wayiwona kasongo mbonawewo mbona wewooooo😂😂😂😂🎉
Amtumbuka mfundo mulibe musiyeni nzanu wawina kababe oyeeeee
Atumbuka tikuvotelani inuyo kt mutchuke ndinu osangovomeleza bwanji aaa
komanso a mtumbuka and others were there during the whole process . osangomvomereZA bwanji ndi kuwona chitsogolo . amawina mmodzi basitu
Haha 😂 kabambe my vote!... Accept defeat isaaa
Mm!!amalawi nsanje cfukwa dzikolathu skutukuka
Prz vomerezAni bwanji munawavomer kuyima nawo ku koveshoni chifukwa chani? Kodi muganiza kuti muwina nose
Mwayambazi ndiye zofoila shupiti
Mukapanga zoti mukokane siziyenda
Tangovomelezani inu kuwina sawina awili mpando umozi iyaaaaa😂😂😂
Nkhani ndi yoti UTM ndi chipani champingo, ndiye ampingowo amayembekezera kuti amene atenge utsogoleri akhale wampingo womwewo ngati Chilima, ndichifukwa chake awa apita kukhothi
Mulungu salakwitsa tiyeni timbvomeleze, nde mukuthanthauza kuti akabambe anabera? Guys eishhhh
😂😂😂😂 kodi a mbc sikuzani chani 😂😂😂 mulila muona kabambe uja ndi machine
MBC mungoyalukatu zaziiii
MBC / MCP Sopano kupanga za AKABMBE. KKKKKKKK. MFITI.
Bola zikanakhalako ena 80 or 100 osati muma 20 onse orephela...there's catacombs played by Kabambe team
Dyera anyani a ku utm watola odutsa chikwama vomerezani mulungu ali ndi njira yake
Amtumbuka or manifest yawo or kamwana kakang'ono sikangawavotele
Ndipo aliyense anali ndi ma monitor ake kumenekuja nde mukati akuberani bwanji muzifunse mukuona ngati pa anthu 4 nonse mungawine koma mukanakhala inu kuwina aaaaa musatitopetse
Vomerezani a Mtumbuka Inu mfundo mulibe Kod a MCP mukulimbana ndi UTM why?? Amwaungulu mwadya zingati kuchokera ku MCP?? Mfundo zomwe akabambe alankhula amauza iweyo kapena ma deligates?? Iweyo Mwaungulu ndiwe mmodzi wa ma deligates a UTM?? Mtumbuka mfundo alibe kuyambitsa chipani sindiye kuti zukuyenereza kuwina mpando.
KABAMBE ANTHU A MCP SAKUGONA NAE TULO
Akaliyati muli ndi balance kwa god papa zanu sizingayende chifukwa mukuphatikiza Mulungu ndi timilungu . Repaint mama
Komadi anapita ku school amtumbukawa kuberedwa mavoti onsewo kkkk mumschuluka matama kumawauza anthu za school yanu oxford ya chan steight to the point
Kodi Mutumbuka nayoso amafunika kupita ku Meto limodzi ndi Manganya mumalo mogwirizana kuti mugwililane limodzi ntchito mwayamba zina .
Kodi mesa mumkalonjeza kuvomereza,
Zokha zokha zolowetsa mphepo zoipa ku chipani,
Vomerezani kuti nde mpikisano umenewo
Awa avomereze bas ma pule sangankhale awiri kuchipani loko atapangaso kena sangawinebe
Mtumbuka. Ndamene. Akutumidwa. Mcp kabambe moto bas
Ndipo atumbuka fundo zero percent tangovomerezani simukanawina inu
A mtumbuka musatichedwetsa olo kukuberaniko akuberani chani
Kuona fisi sikubadwa kale koma kuyenda usiku, komanso mlendo amadza ndi kalumo kakuthwa. Kalumoko ndikomwe kawathandiza akabambe nkotheka.
Zokhala kalezo. Zilibe ntchitooo
MBC ndi television 📺 ya nsete iyi
Mbc yadwala kuwina kwakabambe
Aaaa zikugwilzana bwanji MBC ikayima nawo kut ikwiye.
Kkkkkk. Olo atawapatsa 200 votes sangawinebe.
Kodi nanu adada Mtumbuka mwabwera litigation ku UTM kuti muyambe kusokoneza chipani
a Mwaungulu candidate amene mukufuna inuyo is no match to Kabambe. A Mtumbuka ndy mmmh kuumila too much simukanawina
Timakuonan ngt ochenjera apa mwayamva kuoneka kupusa
Chikangawayo akuti awonetsetse kut miyoyo yawanthu isinthe ifike pofinyika kwenikwrni
Yoooo shame on you apa NDE Zakeyu asangalalatu ( kumupatsa mpata manganya)
guys khani yayikulu ndi khalidwe kulemekeza omvutika thawi zina zimathandiza chomwe mungaziwe ndichoti akabambe samajama ya muthu koma kulemekeza aliyese ngakhale omvutika omwe kodi ndemukuganiza kt olo mutawina mungakhale awili mpando umudzi chenjezo likhale kwa inutso mcp
ABC kulizitsulu plus oweluzayo mbuzi komaso olengeza nkhani mukakayankhula take care one day u will fired
David became a Prime Minister in a foreign land, please go back and ref. history yazibweleza yokha.
Inu zimadziwika kuti DK awina even kuconvetion kuja amati akatchula dzina la DK horo imagwededzeka,,enawo akatchulidwa molalo ochuluka analibe.
The snake targeting the swallow of it's own tail😂
Asayakhe kumene mbudzi zimenezi abesa ndalama amenewo
Proper Ganda mmmmm ku Malawi yakula ndi sanje
kodi muzingokhalila milandu osati kutukula dziko lamalawi
A Mtumbuka mulibe mfundo inuuuuu.. Aaaaa tikufuna wamfundoyoooooo
Inu a mbc mulibe nzeru ndinuyo , mwasowa zochita campaign ndi pa tv pomwe zopusa eti
Kabambe yemweyo kuti wa!! Wa! Wa!! 😂😂😂🎉🎉🎉🎉
MBC namwe ndimwe vindere chomene
Abusa omwe achita recommend pa MEC chair ndiwopusa and akudziwapo kanthu ineso ndi CCAP Christian koma chomwe mungadziwe a Malawi pano CCAP simpingo koma Business kuteroku azibusawa alandira ndalama mmene Malawi aliri pano sitikuyenbekeza kuti abusa omwe amadzitcha kuti ndi atumiki a Mulungu angamayikire kumbuyo zopusa zomwe Mec ikuchita
Manga saw it coming, he said olimbilana mkazi sayendera limozi, UTM has shot itself on the foot
Kodi anthunu mmamverabe MBC? 😅😅
Koditu anthunu simukuona patali kuwina kwa akabambe mcp yanyasidwa kwambiri kmno avomere kuti xidawalaka basi.
DPP sizikuwakhudza angokambilana komweko
Ine ndimaona ngati munthu otchedwa kuti Mtumbukayo ndi ozindikilatu, koma kutengera zimene afotokoza apazi, ndaona kuti ndi mbatata yeniyeni
Atumbukadi ndizitsiru ndikangomva kom ndakhulupilila kkkkkk
Tumbuka vomelesani ndiyetu bdichisankhocho kabambe amasiwa ndare kuyambila kare
Kalikose muzingot DPP, pangan zanu, vuto ndilot DPP kuli anthu ambiri anfundo choncho amatenga utsogoleri kuchipani Zina zomwe alowa😂😂😂😂
MOTi a Mtumbuka ankaona kuti awina? mmm 😂😂😂😂
Maiyeni Kabambe nthawi yamukwanila
Learn to accept deafit and work together ngatidi Chilima anali nzanu
Km akunena zoona ndpo kabambe anabeladi ineyo kunalibeko kumeneko komaso mtumbuka simbale wanga komaso ineyo sine wachipan km kabambe wabera
Mwawuze achakwera wo mapwala awo
Apa ndi nthawi yoti mupite musogolo ndi chipani mwayamba kulimbana mesa usi amanenena koma inu kufuna ndalama ndi izo mwagwa nazo wanzeru ndani apa kkkkkk
Dziwani kuti ambiri omwe awina ku UTM m'mipando yochuluka ndi atsopano
Amtumbuka tidaku kondani,koma fundo mulibe
Nzeru ulibe chakwera coz msewu sitidya komanso fodya amafuna fertilizer ndiye aaaaa worst president of Malawi
Mbc yimangoziwa kupasula bSi
Iwo awona liti kuti wangobwera kumene
Mfundo alibe angovomereza basi
Mbc yambuli iyiiii ndipo felex njawala anachita bwino osayakha 4n yake
Dalitso Kabambe anawina bwinobwino
Kodi MBC inayamba liti kuuwulusa nkhani yazipani zosusa ?
Ndipodi Inu ayamba liti??
Ndipo vemerezani atumbuka fundo zanu zinalu zosagwira mtima atakupatsani 5 minutes kuti mutitakhule mbwerwra zokhazokha zolankhula olo atati akuberani mpaka 576 kukuberani? Ndizosatheka vomerezani basi
Kd Mary chilima akuyang'anila izizi
Eti inu or anakangolemba kalata kupanga congratulations kabambe basi onsewa sanakankhala ndi mphamvu
Ali ndi udindo wanji?
maryyo kut atañi? chipan chili mmanja mwaamalawi not mary ...
Alibe nzeru awa mbuzi iyi
Nkhani za pa MBC zofoira zenizeni
Delegate simumamudziwa inu amadana ndizopusa.