Big up guys. Koma work on sound. Piksy akumveka sharp koma ma host mukumveka ngati ma mic anu anali off so mukumvekera mwa piksy. Secondly try to arrange your stuff on the desk to look nice.
I personally didn't like your comment. We have to be positive for our guys. I'm sorry if you felt offended. 3 years ago you had this thought hope it's changed. Angozo more for and za bho zose ase.
Piksy my Favoured artist in Malawi #2 Kelly Kay
Sweet voice, and slang ya chichewa imakukhala kwambiri upitilize
great tingz
MALAWI MUZIK , MUMAICHUNA HEAVY big up d're wish u wu be there by de time I wu be making it tooo,,,,LOL
Big up to you guy🔥🔥🔥🔥
Advise him to focus also on internationally africa
I love his music!! Koma he's a bit cheeky. Za kuzimba saulura !
thank you so much ndakhala ndikusaka nyimbo zonse za adha awaa ndiye poti anena kuti zili ku reverbnation ayi zikomo ndakazipezadi.
Ku reverbnation nde ndikut plz
Katundu wabwino Piksy👏👏
Handsome guy
Big up guys. Koma work on sound. Piksy akumveka sharp koma ma host mukumveka ngati ma mic anu anali off so mukumvekera mwa piksy.
Secondly try to arrange your stuff on the desk to look nice.
❤❤❤❤
Mumayitha braz timasangalala nanu
Mumalakhula mosazibapa ngat enawa
My angoozo
Umatha big we asking for intern. collab
💖
piksy musician
KYC: are you married?
Piksy: tikhoza kunena choncho 😂 😂
Nice one
Iwe umakwana uli bho
Imagine! Mkazi wake ngati anaonela anazimvela chisoni kikkkk
Kuduwa ndichani
Pa interview olo madzi et kkk kma yaah
Kkkkkkk
Angozo ndi mtondo 🤓🤓🤓🤓🤓🤓🤓
Fuck the camera man... when Piksy was explaining issue yakhoti ndi ndifeyo he was busy showing us KYC and Amuna....
Demet!!
I personally didn't like your comment.
We have to be positive for our guys.
I'm sorry if you felt offended.
3 years ago you had this thought hope it's changed.
Angozo more for and za bho zose ase.
Zinthuzi nzabhobo komano zingoonekela mwaumphawi kunpanje eee kkkkk
Piksy amatha salimbana ndimunthu
et amino musomali kapena amino misonkhano
ArmStrong wansanje eti????
Anthu ochemwa
Ndainjoya mbiri Ya dhawa ndima3la badly level
Jay jay cee Beef
zinthu mbwee patebulo, umphawi, mukumveka ngat muli muzenje aaaa poor