Amene timamunyadila Lulu ndi voice yake yabwino let's gather here with some like, each like or comment i will come back to watch this masterpiece again ❤
Inuyo ndi amene mumatimvetsa kukoma komanso kutimphunzitsa ndi kutilimbikitsa ndi mayimbidwe anu abwino komanso machezedwe anu abwino GOD bless you Lulu and manthumera Band
The song is so beautiful,very beautiful Koma Pena tikumvera makanitu makamaka koyambililako it needs more balance,production yadumphako moto,koma guys mwakunga...🔥🔥🔥🔥
Amene timamunyadila Lulu ndi voice yake yabwino let's gather here with some like, each like or comment i will come back to watch this masterpiece again ❤
We here ❤
Amatha lulu
Anabwela kuzakhala uyu mpaseni plot
Amatha adawa
Tiyeni timupatse plot Lulu
My best musician ever💥💥lulu
Lulu the cool man with beautiful voice ❤️🔥❤️🔥💥
For the love of lulu being my favorite artist ❤🎉
I can see myself dancing the tango with special someone on this one, it's 🔥🔥🔥
My favorite 2 artist's in one song❤ much love from this side❤❤❤❤
Omwe tikuchoka ku mikozi let's gather here🔥
Inuyo ndi amene mumatimvetsa kukoma komanso kutimphunzitsa ndi kutilimbikitsa ndi mayimbidwe anu abwino komanso machezedwe anu abwino GOD bless you Lulu and manthumera Band
Nyimbo ya lulu sitiweluza 1st listening
This song is just a vibe 🔥🔥🔥🔥
I like how Lulu was changing styles
Hope ndinyimbo of the year😂 waiting patiently 🔥❤️
Team Lululu! Mwana Lululu.
It's Mathumela Babe. 🎉
Iyi yabwera munthawi yake
I love this song from 🇿🇲 (let's show love guys 🤩)
🔥🔥🔥…Ine ndikuona ngati Lulu pampandowo samafunapo… amafuna aime azivina zake zija!
Mwachidule azidikula
@@GP_memes36 Basitu lol
Ilove you guys,mwapha hits apa🔥🔥🔥
Nice one lulu... He's always been my favorite jxt that pakatipa don't know y... But now he's back. Kell Kay, machine 🔥
Nice one Lulu en Kell Kays❤❤❤
Bumuuu.. Machine Lulu, keep the fire burning bro
Lulu never disappoint. I much love from Canada 🇨🇦
Patiently waiting for this bomb🔥🔥🔥
Njovu zakumana, Malawi has talent, the kwambiri sisters ku backing vocals❤ 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
Kall kay he did it right 👍 there.. same one kiss my cmnt
Master piece ❤❤❤❤🔥🔥🔥🔥🔥💃💃💃💃
Team lulu ❤❤❤
My favourite 🔥🔥🔥 artist
Notify ikatuluka🥰🥳
Joyfully waiting for the song of the year🤗🔥💃
Another life 💝💝💝💝
Lulu ndi legend.
Koma the guy doesn't age ine lulu namudziwa 2003 ndili standard 3 wangonenepa basi.
I know from day one I saw this kuti ikhala hit,,, two legends meet beat yafapo 🥳🥳💥💥💥🥳 Moyo wina 🙌🙌🥰
Ndaikonda nyimboyi 🥳
Wapha aise🔥🔥🔥🔥🔥
Nyimbo yabwino singapose apa maka chorus mwaipha hvy hvy kell kay ulemu wakoso kachikrna 🔥🔥🔥
Nyimbo ndiya boh.. koma production nde sizinayendetu..... Zikuveka ngati mastering inavutirapo......
Ikuchita kukoma 😍😍😍 welcome Lulu
Ine kuonakuchedwa koma pot mbuye ndi okongola🔥🔥🔥
I like this man and his music , keep going boss
Tune chili super ichi!
💥💥💥💥💥💥💥💥💥
Song of the year ❤❤❤
My all time favorite Lulu, you never disappoint🔥🔥
Nyimbo yaikulu🔥🔥🔥
My best song from Lulu I love it
Here in USA I watch this always
Lulu voice ngati amaisita... My favourite artist in Malawi has done did it again 👏
I know you my brother Lulu always you give out good results you never disappoint 🙏
The song we eagerly waited for ❤. Now you should shoot a video for this
Chichewa ndachivutikila kuchimva ichi....nice nice
My all time favorite artist 🔥 ❤ 🔥
Kell kay fans let's gather here😎😎
Uyu bwanji sakufwifwa eehhh. Ndiwe dolo Lawrence 💥💥
My favourite artist 😊 Lulu sunapaleko aseh iweyo umatha keep de 🔥 burning
Ife pheee kudikila inu Mfumu💓💓
The song is so beautiful,very beautiful Koma Pena tikumvera makanitu makamaka koyambililako it needs more balance,production yadumphako moto,koma guys mwakunga...🔥🔥🔥🔥
Moyo wina,true story of my life..nyengo zomwe ndadusamo.
What a tune.... Lulu lyrics so.matured
Patiently waiting for the song
Hit lero ndinayilota🔥🔥🔥🔥
Top fans from mikozi let's gather here 2024 to support our brothers 🎉
We here🎉❤❤
Bwana Lulu inuyo ndakatundu .....mfana wanuyiso waikokela kutali much respect
Team Mathumela lets goooo
Nice tune, legendary
Patiently waiting 🥳
This will be my birthday song , coz in 14 that's my day
This is so amazing! Yovinika❤
Tikudikila katswiri kwambiri 🔥🔥
i love this song , ili pa repeat mbali yakuno, we need song like this
Anuwake a nyimbo 🔥
#Lulu💣
Mwaupha guys. Mwakumana anyamata a mkawale, anyamata a voice mbambande
Mumachedwa Pati kupanga collabo lulu and Kelly hit
Your voice is just awesome Lulu 🎉
With dat voice or tune pliz tipangile ya gospel..
Lulu pls u can stand up en dance cz yoh pampandopo sukufunapo😀😀...iyiyi mwapha ma guy 10/10
You are the best,nyimbo yomvera nthawi iliyonse❤️❤️❤️❤️❤️❤️
Shasha ka 3 million
Kawale boys 🎉🎉🎉🎉
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥hit mbambande
Lulu ndi Dolo kasanu ndi kanayi 🔥💪
Anamanyonyolo pamayimbidwe zakumana🔥🔥🎶🙌
Can't wait 🤩😁
Combination iyiyi🔥🔥🔥🔥
Lulu ndiwe dolo aseh🔥🔥 tazangisen show Ku chikwawa please
Biggie sakhumudwitsa🔥🔥🔥🔥
Wow great voices ikuvekaso mwawuzimu zimu nyimboyi
Waiting my best artist
Hit🎉🎉🎉 thanks my best musicians you made it
Ilibwino osati masewera❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤team lulu gather here 🔥🔥🔥
Kell Kay is powerful. Great master piece
Lulu amaganiza zoopsa pa nyimboyi koma production silibho koma akuluwa ndi legend
Exactly 🎉
Im speechless,but it's okay bcz Lulu always sanalepherepo
Production eeeeeh .
Koma chi lulu ndakatundu
Great song 🔥🔥
Mukapitiliza maimbidwe awawa! I swear mafanawa sangapezeso mpata!
Moyo wina on 🔥🔥🔥
Its a nice tune fada❤
It’s fire as expected!!! 🎉 Great job guys! It was worth the wait.
Akulu akulu nyimboyi aikutumula #LEGE NO DS OF THE SEEKER'S
Nice voice Lulu Always 🔥🔥🔥🔥🔥❤️
Nice tune guys 🔥💎
Intro ili mwala lulu🔥🔥
Waiting
🎉 lots of love and support from 🇲🇼✊
Kanyimbo kodekha. Very beautiful voices