@@ExcitedBreakingWaves-oh3zb dzana mumalilatu ku Lilongwe, anyamata ataletsa mademo. Dzulo pa 21 Lilongwe yakanaso nyasi, no mademo ku Lilongwe. Munya muona
CHAKWERA ALI NDIKUTHEKERA KUTUMIKILA SATANA OSATI MULUNGU AMENE MWADYA NDALAMA ZA CHAKWERA DZIWANI KUTI MWAKITSA TSAYA LA SATANA NOSE MAZIMBUSA NOSE MABUNGWE AMENE WALANDILA NDALAMA KUCHOKERA KWA CHAKWERA SIMWANASO WA MULUNGU AI AMEN
Sorry for mcp...darkness has started enveloping you.
Inali demonstration yabwino kwambiri chifukwa kupempha Kuma DC boma limakaniza.
MCP ndi ma minister amazitenga ngati NDI madolo
Ndilande siyigawa maswiti
Investigation must start from what happened in LL
Ndirande keep it up menyani onse akutizunzawa
Good Ndix, tsikulina muzagende Chimwendo Banda ndi Kabwira Jess.
Amuchita bwino,anakamukangatha zenzeni.. well-done ndilande people
Zili bwino chisakuwaweni a mcp,
Mwaonongo nokha
Mukuzala nansongole
Bravooooooooooooo zikufunika ndizimenezo .
MCP osangosanzika bwanji Kuti mwalephera. kweni kweni mukufuna chani kakakaaaaaaaaaa MCP.
Tulani pansi maudindo mwalephera
Vithireni machaka za mcp
Moto moto ndirande Ineyo ndi kuidziwa ndirande, safuna kulandira sweet amene sanagwirire ntchito safuna zopusa woyee ndirande MCP inakuphelani munthu wanu.
Ndirande sisungaaa kape ulemu wanu Comrades
Well done boys of ndirande.
@@ExcitedBreakingWaves-oh3zb dzana mumalilatu ku Lilongwe, anyamata ataletsa mademo. Dzulo pa 21 Lilongwe yakanaso nyasi, no mademo ku Lilongwe. Munya muona
Mr Savimbi Mchinji good
ayambe Kaye kufufuza zikwanje za ku Lilongwe
Ndilande kwanthu muzipereka odi kuti mukulowa.....uremu wanu anthu amu Ghetto.......... komatu osamatiseweresa......viva ndilande......kwanthu kwa uremu
More fire 🔥 🔥🔥🔥🔥🔥Ndilande siphwekesa
Don't apply selective justice apa
Mwachita bwino big more fire comrade zimenezo ndizimene zikufunika basi mcp ndichipani chakhaza
Waona iye kuti atha kuzuzula ndizo zaku ndilandezo koma aja azikwanje aja ayi.muva kuwawa
Joice Banda, Bakili Muluzi and Peter Mutharika to condemn these violences.
My home town ndix ndirande Soweto
That's good 👍
Musamanyengelele nyansi
Anthu aku ndirande ndakupasani ulemu ndipo mwachita bwino. Ngati apolisi amange munthu mupwanye mapolisi wose. Akayembe kaye kukamanga anthu azikwanje
amaona ngati yakulilongweija siimatiwawa😢😢😢
Mwachita bwino,imeneyo nde ndi Dix V iwe umatiii😂😅😊
Police ikangomanga anthu ku ndilande tiontcha police station yawo
Kuwaotchera kumene.
Akamange kaye Akazikwanje awo Aja Ku LL.
NDIX BT TOWN sisunga zitsiru
Ndirande sisewera 💪💪💪💪💪
Asala apule agendedweso
Amaziwa phavu amenewo mwachita bwino a kwa sundwe amaziwona ngat alipo okha
Apolice agwile kaye akulilongwe
Mcp just think.... Anthu akugona ndi njala midzimu kudya chitedze.... Yambani mwakonza mavuto amenewo akuchitani bwino.... Ukafesa chitedze umakololanso chitedze more fire ndilande pple
Zonsezi chifukwa cha ulamuliro oipa wa Chakwera tayambani mwafufuza azikwanje aja
Wasala Richard chimwendo banda muphulise mimbayakeyija
Amafuna kumangq ayambe Kaye aku Lilongwe aja amayenda ndi zikwanje
I surport the point Malawi wawola.MCP kumangowagenda
Awachita bwino bwanji sakuzuzula dzaku Lilongwe
MANGANI KAYE ANTHU AJA ANAYENDA NDI ZIKWANJE KU LILONGWE AJA NDI PAMENE MUMANGE ANTHU AKU NDILANDE
Munganamugwila,kumudula mutu live 😅😅😅😅
Imve tikudikila kuno kumachinga abwele I 😂😂😂😂😂😂
Amange kaye anyamata azikwanje
Kafukufukuyo ayambe kaye kwa azikwanje aja
😂😂😂😂😂 chikangawa party wakupha
Ifeso kuno kumangochi tidzakugendani achakwela ndizadula mbolo imeneyo
Very good
Amuchita bwino kuyelekedwa
Minister My Friend Kunkuyu think of u ,ur Kids en ur family after ur MCP party loses
Ndilande keep it up
Ine zandikomelatu kwambiri
Ndirarende woyeee😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 mcp tikuyikanaaa ife
Bravo NDIX.
CHAKWERA ALI NDIKUTHEKERA KUTUMIKILA SATANA OSATI MULUNGU AMENE MWADYA NDALAMA ZA CHAKWERA DZIWANI KUTI MWAKITSA TSAYA LA SATANA NOSE MAZIMBUSA NOSE MABUNGWE AMENE WALANDILA NDALAMA KUCHOKERA KWA CHAKWERA SIMWANASO WA MULUNGU AI AMEN
Mwamuchita bwino ameneyo anthu akatopa ndi chocho
Amenyedwe agalu amenewa
100% awachita bwino amaonangati zikoli ndilawo agaluachabe chabe
Kwasala ku Bangwe pa Wiving myala tasunga kale tikudzidikira zisru zimenezi maka Chimwendo Banda
Woooza
Ku Lilongwe sanafufuze za anyamata a zikwanje. ndye azifufuza za chitsiruchi
Kkkk boma ndilomwelidie
Ndirande my Ndirande
Wayenda tchibiyatchibiya😅
Mcp will learn in a hard way
Mayizi zosangalatsa miyala ili ponseponse amenewo kwanuko athamangitseni kwathuso miyala ilipo tidzathamangiso anuwo
Munakangowaphela komko zisiru zimenezi
Ndipo tiye nawoni, tiwathile miyala anyapapi..
Kkkkk koma cadet uli pa ntchito. Zithuzi izi ndizakumozambiki
Muli ndinchitodi nanu,mukukana zoti agendedwa mwina ndibambo anu,,,
Mozambique yaku chipinda kwako? Kodi simukufuna kuvomereza kuti zinthu sizikuyenda bwino bwanji mdzikoli
@IvyMkhura koma dpp palibe chomwe ingabweletse chachilendo. Mesa munkati Malawi ioneka ngati Singapore, zinathela kuti? Kkkkkk. Kamagwelu wanuyo palibe chomwe angachite.
Awa alephela usogoleli
Anthu akundilande mwachita bwino
Nice
Mwawachita bwino ndipo or mukanawapha
Ayambe kufufudza za kulilongwe kuja kaya mbuzi za policezo
Kulilongwe mcp akumagenda athu osalakwa nde apapa asadabwe
Mwachita bwino kundirandeko ine chimwemwe chokha chokha
I condem such act koma zinalibho coz kubwezela
Mwalakwisa kuwasiya mukanaswa mitu yawo amaziyesa madolo ku lilongwe tiwonana
Kkkkk km zooona kwambili mcp yagwakale bs
Mufufuze kqye zandege, kenako za mafuta
Ndi okhaokha a MCP amenewo
Akanangomupha galu ameneyi
Nziko lamalawi tikugawana zigowo lilogwe tingani chakwera usapiteso kumangochi kwatupere ndi adadi kupoto afrod chigawo chapakati kabambe
Apolice mugwire azikwanje aku LL aja sizokonderazo
Mwachita bwino akutamika agalu amenewa
Kkkkk azigendwedwa kumene
Ndipo muwawonetse mbwadza angayambe. Kudelela kabambe woyeee
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Awa chita bwino
Mukanamuphulisa dadzi lekero, wasala mkulu wakeyo anthu azamugendaso
ANTHU INU MCP OSADZITENGA NGATI MACHANCHA AI MUKUNAMA KWAMBILI TIKUTI MANGANI ANTHU AJA ANALEPHWRETSA MODEMO MUMZINDA WA LILONGWE POYAMBA MUSANAYAMBE ZAKU NDILANDE NGATI IZI NSIMUCHITA PASAPEZEKE WINA WAKE WA POLICE AKULOWA MUNO MUNDILANDE AI
Ajosefe mwambe awachita bwino atizolowela agaluamenewa
Zili bwino
Koma awawa ofunika kwagenda
Mwati watani?
Kunkuyu anayeneleka kuphedwa kuti adziwe uchitsiru wawo
Ndilande mwachita bwino tatopa tsopano boma lanji lasava zonena anthu komaso chimwendo banda osamale tikukuonanitu
Ndilande sisunga kape
Mukayambe mwamanga azikwanje aja kaye. Uchisiru wanu uwonekera pamenepo kuti chilungamo chikhala bwanji
Mukuti Moses Kunkuyu watani
Mwina ndikulota
Zilibwino asamationjeze
Athu atopa.......... Mcp......musamale.....athu akutikitani mwa nyooooo simunati
Mcp sitikuyifuna ife
Awachita bwino
Simar yafuwa
Ghetto sisunga kpe chimne mungaxwe ife sitidya ndale timadya thukuta lathu chutipweteka nchimodz ndalama sikukhazikika musatitole kufasa
Agweye azikwanje aja