Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Olakwisa si pop young km mkazio cfkwa anamuputa dala yekha😂😂😂
Phyxix wapola kummenya mwanayi
Aaaa zaboxa zomwe wakamba pop young kupatura zomenyexo muve mfundo ya physics
Apa phyzo sanamenye nfanayu I think mwanayu akuyankhura izi chifukwa anamuthoka ma wise
🎉❤ nice video
😢Aaaaaa pop akukamba zoona
Phyzo osamamuseweresa azngogawa makofii bas
Wagena mwanayo
Kape ameneyo amafuna achindile zake
Akanamuheda akanafatu😂😂
😂😂😂😂 km bro 😅😂😂
Ine ndasankha kukhulupilira Phyzix ndipo ndi kuti very good very good
Pop young atha akuyankhula zoona, cz abale asikana mahule ngati amenewo angakane mwamuna, nde bozatu limenero, abale mwamuna ngati wamukana Singapange phokoso loti mupakana anthu kubwera kuzafusa ayi izi ndizabosa asikana amasiku ano amenewo ili nde ndiboza loone keratu.koma zomwe akunena pop izo ndikugwirizana nazo kuti sikanayo ndamene anabwera yekha kuzapereka moni asikanafetu timaterodi mwachidule musikanayo ndamene amafusira pop nde paja asikanafe sitimaloredwa kufusira mwamuna ndeno timangobwera ndimoni basi chilunga mwamunayo atifusire
Zitayeni izi tiyeni tilongosole zosaka ndalama.
PHYZIX IS MAN OF HUMANITY
Sindinatengepo mfundo apa😅😅😅
Akanamumenya km ah amadelera
Sasi 😂😂😂
What's the name of the background song that you put on the first part of the video?
Search .. nyimbo ya Sam Malvitha.. pa RUclips..
@@sammalvithacould you please place youtube link in response. I searched using what you gave koma sindina iwone. Would appreciate your response.
Phyizix akulowa khazandizawo frondokkis khala akulimbana mtcha hp sayitha kuvemekeza ndikwambuno? Mozambique,
Akanamkwapura kumene
Zoona xomwe akukamba Phixyxy
Akukamba chilungamo ndi Phyzx
Kd phyzx ndi Dan lu angawine ndan 😂
Amachezela limozi
Nice video
Tima artist tu timakonda kulandana akaz
Phizx azikula nae aaah
Iwe palibe voice apa
Phyizo akunena chilungamo
Nde onseo ndizitsilu
Pop amafunika kopondedwa
Kodi ndekuti phyzix ndekuti amatha kumenya kwambiri kumalawi kuno? Chifukwa akaka sikoyamba kunva nkhani ndeu
Vuto lokhala opanda management ndilimenelo umangopanga zinthu muchimbulimbuli,had it been kuti mafanayi akupangidwabe manage ndi Akometsi bwezi alibe well disciplined,..yekha waziwa kuti mkaziyo wapita ndi Artist nzake chomupangila approach ndichani? Phuma ngat ka mkodzo akuswani kutchuka musakutengere pamgong'o.
❤ nice video
Nice one video
Apa Mwafotokoz Moveka Bwin
Pop akunam
Phyzix salakwitsa mafana kudelera
Vuto loti pena palipose upeze upeze nkazi ndi limenelo
🎉
Akanamuponda amadelera popizo
Pop young ndi dolo
Motengela nd mbiri za achimwene aja tingot anamuswadi makofi
❤
pop ndamene walakwitsa coz zomwe wayakhula phyziks ndimalangizo abwino amene akusonyeza kut pop anapanga chinachake coz phyziks ofcoz mbili yake inaipakale kut amamenya oimba
Akanakamenya
Physics ndiolakwa mnyelo ndiwake?
Umakwana iweyo
😂😂😂😂
Kaya?
kk
Kumenyako very mistake ngat anatero
😂😂