MFUMUKAZI COMEDY SERIES..30/08/23..FLORA SUYA +265883106798

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 1 окт 2024

Комментарии • 93

  • @SharonJalamu-g9m
    @SharonJalamu-g9m Год назад +3

    Farayih anankodza ai ndthu asasowe pano ndiyemwe akubhebetsa I love you farayih

  • @HusseinMm-z3j
    @HusseinMm-z3j Год назад +2

    Eeeee falayi anadza eeee akut stock taking

  • @patricksinyala1345
    @patricksinyala1345 Год назад +3

    🤣🤣🤣 Koma amaliro ndi mwanawao eishiii

  • @PaulNdalama
    @PaulNdalama Год назад +1

    Jemason wabudula mmemo wagulu

  • @clesheinvestments
    @clesheinvestments Год назад

    Farai sadzatheka.
    Mfumukazi anadya Mfulumira pothamangitsa Giring'ande lero ndi izi mukulira.
    Ndiye Namoyo ndi Tambwali otha ntchito wadya Mpunga wa ulele.
    Mukuitha Guys

  • @JohnChibalo-wf8gr
    @JohnChibalo-wf8gr Год назад +1

    Lululuuuuuu moto buuuuuu chiphwanya kumulesa padera kunjoya chiphwanya ndiiwe wachibwana kobasi amfumu kadzi mamvera mvera lero ndiidzi mukungodyeredwa mpunga cholinga muthandizidwe nzeru naye namoyo amamuhopera Shoprite farayi kuyipasa moto buuuuuu ❤❤❤❤.

  • @SharonJalamu-g9m
    @SharonJalamu-g9m Год назад +1

    Farayih sakuchoka agreeng'ande apo ndie mukunama farayih sanasale madzi amodz 😅😅😅 Moto kut bhuuuui

  • @blessmax5148
    @blessmax5148 Год назад

    A geling'ande a shoprite asabwerere athu aphuzile kulemekeza aliyese aliyese ndiwofunuka paziko pano

  • @giftblack7690
    @giftblack7690 Год назад +1

    😂😂😂😂 padela yamuwawatu ana achoka nde jemasoniso kumatulukila wasokoneza ma program Kwambili 😂😂😂😂😂

  • @ChifundoChikakwiya-kf1is
    @ChifundoChikakwiya-kf1is Год назад +2

    Nice content guys we are supporting you right behind you

  • @mrscharleswebster6192
    @mrscharleswebster6192 Год назад +1

    Kkkkkkkk ndinaziwa kut amaliro ndi mwanawawo zithera ma speed😂😂

  • @ethelsawerengera2140
    @ethelsawerengera2140 Год назад +1

    Farai asachoke akubebetsa onse mfumukazi namoyo onse mpakampaka 🔥🔥🔥🔥🔥

  • @Fanzo-h2l
    @Fanzo-h2l Год назад +1

    Abale munthu akuganizidwayo gilin'ande komadi sananame kuti love is blind eti mumandimvetsa kukoma anthu Inu pitilizani namoyo atengana ndi Giling'ande keep it up

  • @GOEMENGONDWE
    @GOEMENGONDWE Год назад

    Padera kungoyamba motomoto 🎉🎉🎉 Basi😅😅😅😅😅

  • @MaureenMangani
    @MaureenMangani Год назад +1

    Nagama bwanji kulibe sindikumuona

  • @ethelsawerengera2140
    @ethelsawerengera2140 Год назад +1

    Banja ilinso nde likubebetsa bwanji ndaseka 😂😂😂😂😂😂

  • @Martha1436
    @Martha1436 2 месяца назад

    Amfumukazi avala Juzi ya Pilira wantchito wa amai a Sikono. 😊

  • @SquareBoma-vl2rj
    @SquareBoma-vl2rj Год назад +1

    Kawawa!!! Farsi umakwanira, Amfumukazi mwadekhatu 😂😂😂😂😂😂

  • @KenedyJolamu
    @KenedyJolamu Год назад +1

    Kkkkkkk eish koma shop rite 😅😅😅😅😅😅

  • @preciousmatenje1425
    @preciousmatenje1425 Год назад +1

    Kkkkkkkkk osakhala ndi thinking

  • @mussachitambi
    @mussachitambi Год назад

    Mfumu mkazi Mr Shoprite koma musanale namoyo akulanda

  • @yassinrashid7012
    @yassinrashid7012 Год назад

    Padera akufuna kunamiziranso kukomoka yeti😅😅

  • @EsnartJosiah-r2x
    @EsnartJosiah-r2x Год назад +1

    Koma farayi umaipasa Moto kkkkkkkk

  • @HassanBandah-l4t
    @HassanBandah-l4t Год назад

    Pabwalo tapasowa pangani zoti tikamve watch out

  • @franciscoduartie5762
    @franciscoduartie5762 Год назад

    Duncen kuyiuza wise mdala yake😂

  • @KondwaniChinawa
    @KondwaniChinawa Год назад

    Kod farai.. Ndi pricess chitsulo?

  • @NelsonNgoma-iu4jw
    @NelsonNgoma-iu4jw Год назад

    Koma falai kukaniza namoyo kuti asagule sugar koma zina

  • @KennedyPhiri-fb6zc
    @KennedyPhiri-fb6zc Год назад +1

    Mumacedwetsa kuchotsa commend

  • @JamesWandari
    @JamesWandari 4 месяца назад

    Chimphwanyakusokoneza game

  • @khanawesaulo
    @khanawesaulo Год назад +1

    Nie

  • @AliceDandaula-ug8rj
    @AliceDandaula-ug8rj Год назад

    Namoyo mulilise mfumu kazi wataya yekha makina

  • @abrahamnkosi4160
    @abrahamnkosi4160 Год назад

    😂😂😂😂 koma farai anakonza,,,, watching from Eastern Cape tsitsikamma storms river south Africa

  • @JamesImran
    @JamesImran Год назад +1

    ❤️❤️🥰🥰🥰🥰🤣🤣❤️ mukutiyimirila ma gyz

  • @harrisonnavayah6480
    @harrisonnavayah6480 Год назад

    Falai kuno kumudzi upole faya

  • @bernadettechoma
    @bernadettechoma Год назад

    Ati komatu iwe ndikuwsa😅😅😅😅

  • @hamiltonlemilton7322
    @hamiltonlemilton7322 Год назад

    Jemason ofunika mpini 😂😂😂😂😂

  • @maliyadaitoni
    @maliyadaitoni Год назад

    Koma namoyo kwauza zochita mfumukazi kk

  • @IshmaelAnad-zd6zi
    @IshmaelAnad-zd6zi 11 месяцев назад

    Mutu mene wachepelamo 😆😆😆😆😆

  • @moosathomas6440
    @moosathomas6440 Год назад +1

    Koma ndanken ndi bambo ako mumatengetsana😂😂

  • @benjulius6070
    @benjulius6070 Год назад

    😂😂😂😂😂😂

  • @estherkauyange6548
    @estherkauyange6548 11 месяцев назад

    Kkkkkk chipwanya kusokoneza

  • @ApsChap
    @ApsChap Год назад +1

    Mr shoprite kkk

  • @erastokawina4550
    @erastokawina4550 Год назад

    Watching from Cape town 😂😂 koma kwabeba mpaka namoyo ndi fumukazi kupelekezana😂😂😂

  • @RabeccaSaka-y3q
    @RabeccaSaka-y3q Год назад

    Padera afera mmanja mwa anthu

  • @madalitsomakawa9708
    @madalitsomakawa9708 Год назад +2

    Kodi Farai ndi ndani in real world?

    • @SquareBoma-vl2rj
      @SquareBoma-vl2rj Год назад +1

      In real world she is Gospel Musician Princess Goldenvoice Chitsulo

  • @JustenChikanda
    @JustenChikanda Год назад

    Afumukazi ayilira ya gili

  • @JayMilazi-fv6px
    @JayMilazi-fv6px Год назад

    Koma Namoyo uli busy kumudyera mzako mpunga😂😂😂😂😂 komanso padela katundu yonseyo ukufuna kutenga ulere😅😅😅😅😅

  • @SquareBoma-vl2rj
    @SquareBoma-vl2rj Год назад

    Komatu Banja lanu a Padela mmmm munakumana ma actors okhaokha eeeee keep fire burning guys, mumakwanira!!

  • @FrancisKamwendo-k7j
    @FrancisKamwendo-k7j Год назад

    Koma mfumukazi mumatimvesa kukoma koma jemason ndi gututu amaphula ma scandal okuba mowa Kwa namoyo 😂😂😂😂😂

  • @SharonJalamu-g9m
    @SharonJalamu-g9m Год назад +1

    ❤😂😂😂😂😂

  • @EvelynSimino
    @EvelynSimino Год назад

    ndimakuko ndaninose

  • @madalitsosandram1576
    @madalitsosandram1576 Год назад

    Farai Sali bho😮

  • @harrisonnavayah6480
    @harrisonnavayah6480 Год назад

    Fumukazi nsanje

  • @yusufqassim2020
    @yusufqassim2020 Год назад

    aha😂

  • @GOEMENGONDWE
    @GOEMENGONDWE Год назад

    A mfumukazi si nsanje koma ndalama yawavuta😂😂🎉🎉🎉

  • @AleksaWilliams
    @AleksaWilliams Год назад +1

    Nice

  • @abdulboniface9832
    @abdulboniface9832 Год назад

    Namoyo uli bho

  • @abdulboniface9832
    @abdulboniface9832 Год назад

    Namoyo uli bho

  • @mackgozambia
    @mackgozambia Год назад

    Watching from Katete Zambia

  • @HappinessMkwinda-fz2wn
    @HappinessMkwinda-fz2wn Год назад

    Farai😂🙄

  • @ziyamikanmakowa5981
    @ziyamikanmakowa5981 Год назад

    Amfumu KAZI mmathamangisa agilingande mukuwafuns

  • @ChristinaKumwenda-d3l
    @ChristinaKumwenda-d3l Год назад

    Kkkkk afumukaz ayamba jeras 😂😂😂

  • @mussaganeti
    @mussaganeti Год назад

    mayi padela amakwana 😂😂😂😂😂amfumu ayambaso sanje. kkkkkkk

  • @cathychimombo6884
    @cathychimombo6884 Год назад

    amfumu kazi tsopano zayamba kuwawa tsopano

  • @sostenkasandala3505
    @sostenkasandala3505 Год назад

    Jamason waisokoneza game ija kuno

  • @DuncanSimbeye-t4y
    @DuncanSimbeye-t4y Год назад

    Thinking kabwasite😂😂😂😂

  • @kondwaninyangulu5563
    @kondwaninyangulu5563 Год назад

    kkk ntoliro mulungu anayika kale mchele

  • @sidreckrashid9327
    @sidreckrashid9327 Год назад

    Watching from Taiwan, my warm heart of africa

  • @harrisonnavayah6480
    @harrisonnavayah6480 Год назад

    Me konda this comedy

  • @lhordgowello688
    @lhordgowello688 Год назад

    Kkkkkkkkkkkkk koma paderaaaaaa umakwana

  • @user-oi9on5dy3hlixy
    @user-oi9on5dy3hlixy Год назад

    😂😂😂😂km falai

  • @MuhammadKayipa
    @MuhammadKayipa Год назад

    Padela ndi jamasoni ndi one

  • @MalitaBanda
    @MalitaBanda Год назад

    Ayamba jealous amfumukaz 😂😂😂😊

  • @DennnisGogoda
    @DennnisGogoda Год назад

    Farayi tamusiye Namoyoyo abale 😂

  • @anniewhite3497
    @anniewhite3497 Год назад

    Mutimvesa kukoma😂

  • @MzatiYouthOrganization
    @MzatiYouthOrganization Год назад

    😂😂😂

  • @franciscoalexandre4168
    @franciscoalexandre4168 Год назад

    Namoyo ndiwe okongola❤

  • @lydiakamanga
    @lydiakamanga Год назад

    Koma farai😂😂😂😂😂

  • @LaikaMakalani-ur2wg
    @LaikaMakalani-ur2wg Год назад

    Mfumukazzi wayaluka

  • @Pungwe123
    @Pungwe123  Год назад

    Deal ndi mai padera😂

  • @EdwardHamilton-k8f
    @EdwardHamilton-k8f Год назад +2

    Farai is very clever indeed, u have been hiding your talent for many years.God bless you

  • @GiftAli-d7k
    @GiftAli-d7k Год назад

    Kkkk km apadela

  • @andreguvermane7434
    @andreguvermane7434 Год назад

    Pasela wavuta

  • @YusufRahimu-be9hu
    @YusufRahimu-be9hu Год назад

    Padera ❤😂😂

  • @EnochRickson
    @EnochRickson Год назад

    Mumatha ma guyz

  • @tawongakakusa3437
    @tawongakakusa3437 Год назад

    Farai ndi Namayo adziwana liti?

  • @mavutojackson9264
    @mavutojackson9264 Год назад +1

    Kkkkkkk

  • @hestonsailesinjolomole2318
    @hestonsailesinjolomole2318 Год назад

    Farai wow very talented