Ku Malawi konse nyimbo iyi Ili pa number 1 . Azimayi akuwoneka achilengedwe ndipo ndi 100% mmene tikuyenela kuwoneka munthu wokhulupilira. Ambuye akudalitseni mochuluka azimayi
Nyimbo iyi imandikumbutsa nthawi imene ndinaluza azibale anga 5 pakamodzi ndipo moyo unali owawa koma nyimbo iyi imasisimura ndikulimbitsa moyo wanga 😭
Such a powerful message God bless you all 🙏🙏
yah zoondi
Ku Malawi konse nyimbo iyi Ili pa number 1 .
Azimayi akuwoneka achilengedwe ndipo ndi 100% mmene tikuyenela kuwoneka munthu wokhulupilira.
Ambuye akudalitseni mochuluka azimayi
This song make me to put God first in my problemes in my everyday life
I'm always encouraged each time I listen to this song 🙏🙏🙏 I'm humbled, from Zambia
Praise the lord ❤❤❤❤❤ all the time, good job
iam muslim but ilike dis song ..😍😍😍😍
Very sweet piece of song keep it up mponela ccap women
Proudly presebeterian..... Good work azimayi 🥰🥰🥰
God bless you all for this kind of powerful gospel music🙏🙏🇿🇲
I'm very excited about this opportunity to listen to music 🎶 . This is wonderful to me.
Tikakhala paulendo nyimbo yomwe ndimakonda kuvera ndimeneyi ❤❤❤❤❤ mwina kutheka mwachitira mdara 😅😅😅
Ukamadutsa muchikangawamo driver Kuzaika pamenepa nonse kukhala chete ngati mu kugona koma Ayi ndinthu
Zili bwino azimayi thanks so much ambuye mwina mwachitira dara kuti ndikuziwen
These woman deserve a reward 👌 🆗️.
You look soo lovely my mother in Jesus..wish u a good hope always
Zoonadi ambuye mwachitira dala kuti ndikudziweni I like it
Ayi kuimba kosangalatsa azimai keep it up mwativesa kukoma ambuye akhale nanu
Powerful messages womens❤❤❤❤ keep it up
My God bless u all keep fire Bunning
This song inspires me a lot. Glory be to God
Pastor Emmanuel sends compliments of the day.
ndikuziweni ine ambuye amen ❤❤❤❤
Amen, mwina mkuthekadi ambuye achitila dala kuti ndaziwe
To God be the glory..blessings shall ever flow to your gospels 🎉
Nice song I really enjoyed
God bless you all & His holy Church, in Jesus' name. Amen.
Let God's will be done and am speechless
Proud of you our ladies. Keep it up
Amen powerful message 💪
Wow keep it up🎉
Kwambilitu ndipo osatinso masewera,osatsutsana ndi chilengedwe cha Mulungu
A very good song and indeed we have to remember God always
Mponela ccap keep it up 🔥 burning
Hi
kwaya ya kwanthu ku mpotsi more fire..Ambuye apitilize kudalitseni
Amen mwandisuntha ndinyimbo yabwino
Death is very cruel, this man gone but the legacy continue. Rest well Athot Manje.
every Sunday i watch it
Hallelujah 🎉🎉
Ambuye mwandileka dala ndikudziweni ineyo amen
Nice song like it 🙏🙏🙏🙏
Very powerful azimai
In everything put God first God bless you.
Thanks may God bless you 4:14
Nyimbo iyi imandikumbutsa nthawi imene ndinaluza azibale anga 5 pakamodzi ndipo moyo unali owawa koma nyimbo iyi imasisimura ndikulimbitsa moyo wanga 😭
Sorry sorry 😢😢😢
Imatilimbikitsadi ndipomwe timadziwa Kuti Mulungu salakwitsa brother
Zikomo ambuye akudatsen azimay alwathu mponera timakunyadiran akudatsen amen😅
God bless those woman's 🙏🙏🙏🙏
Pure Gospel
Nice one🎉🎉
Good songs
I love this song
Emen and emen ❤❤
Amen nice song
The music that can change our lives. Keep it up
Mwina mkutheka Ambuye mwachitila dala😢
thanks 😅
Aiboooh
Your music revives me a lot keep up with good work of God
Naice
Nice song endeed
zili bwino kobasi🙏🙏🙏🙏🙏
I love this song❤❤❤❤ mumaswa sound zedi azimai athu pitilizani zedi mumatitsisimusa ndithu
Beautiful🎉
Amen, God bless all of you
❤Amen Mavuto aabanja
Powerful...Mwina nkutheka Ambuye mwachitila dala kuti ndikudziweni ineyo.
Keep it up
Sure mavuto asandichedwetse haaa
Powerful song 🙏 amen
Nice song amen 🙏🙏🙏
Pure art
Glory be to God amen.❤
Hallelujah
Good song indeed
Praise the lord
good song
Nice song
Lovely.
Nice song 💯 amen 🙏🙏🙏
Nice
Awesome
amene
Eeeee komadi nyimbo ili bwino kwambili iyi
Good
Nyimbo iyi imanisuntha
Makhadzi
Azimai mumaimba bwino pitilizani kufalisa mau amulungu
Nyimbo yabwino kwambiri yotsitsimutsa yobvinika
Mmatidalisa
Osanama zilibwino
Naikonda imenei
Zoonadi nyengo zina Mulungu amazilora dala kuti timudziwe
Ndikuimvera apapa zamphamvu
Zoonadi timudziwe yesu
Kwa iye kudzilemekezeka nthawi zonse
Komaso Ambuye dalitsani Banja ilo
Glorry to GOD
amen amen
Nyimbozi zindikumbutsa Amai anga. Anakonda kuyimba mu Msamaria Choir ku Petauke RCZ ku ZAMBIA.
Zauzimu zenizen
Amen 🙏 🙏
❤❤❤
Nkasa uli pa business yosaoda km ifeyo tizingomvelanao nyimbozi km siticopekanazo tikudziwa zodzapanga 2025 muzaona bachitani matamao
🎉
Mbambande pitilizani
Zikutheka