Thanks for the true word of God.. We nid more pastors like u.. Who can stand n preach the true gospel of our Lord JESUS Christ.. May almighty GOD continue to use n bless u.. Yu r a blessing to us🙏🙏
Nkutheka kuti mwina inuyo mumanvera ulalikiwu muli kale ndi mbali yomwe mudasankha, ndiye mumangonva koma osanvetsetsa, kudzudzulana zikamalakwika nkofunika ndithu.
Each and everyone has got his or her own calling ... Ngati iweyo calling yako ndiimeneyo yoona zofooka zaanthu amulungu ... Mulungu akukhulukileni ndikukubweletsalani anthu amulungu onga awa Oti akuzuzuleni
Uyu munthu mubusa wakuyooya makola chomene and wakuyooya nkhana makola chomene, wakuyooya kose kose, not only shouting, wakuyooya naumo wawelengela mutu wa bible, am very happy with him, Pitilizani abusa osasiya osavela za anthu , And uyu kubusa nimunthu muwemi coz iye wakulalikila kumuzi not ivi wakupanga ma busa yanyake yanchuka aya chaa waka ma million mphaa vabweka utesi wekha , kwe uyu wakuyooya nkhana exactly umo chalo chilili pasono, wakuyenela kupephela nthena indeed, iye walinavo nachito vakutauni yyso or kuyenda malo uku na uko pitilizani basi iyaa , happy for you 😄
Kondwani Harawa I agree kwambiri. The reason why this world is finished is evident in such type of sermons. People prefer this preaching to tickle their ears. It’s mostly moralism and jokes. Sadly, most people think they are being fed spiritually. No wonder millions are headed for hell. The truth is supposed to pierce one’s heart not be anticipating laughter. The reason why this guy is trending is because he makes people laugh. Not that people are getting saved or knowing the truth. Ecclesiastes 7:4 The heart of the wise is in the house of mourning, but the heart of the fools is in the house of mirth.
🚨🚨 PHILL J - ZAKOMA PRODUCED BY MAGULU DOWNLOAD NOW ⚡🔥: malawitunes.com/track/BtKYGgtLuqZJ2AB GET THE BEST OF URBAN MALAWIAN MUSIC ON www.malawitunes.com TODAY!
POWERFUL MESSAGE MAY GOD CONTINUE BEING WITH YOU ALL THE TIME
Powerful message
Educative and edifying
Powerful message God continue bless you
powerful sms thnx 🙏 from north west klerksdorp
Thanks for the true word of God.. We nid more pastors like u.. Who can stand n preach the true gospel of our Lord JESUS Christ.. May almighty GOD continue to use n bless u.. Yu r a blessing to us🙏🙏
THATS TRUE
Unthenga waveka bwino kwambiri, Amen pastor
AMEN powerful massage ali ndi khutu Amve chimene nzimu anena
Powerful my pastor though ndamvera mochedwa 👏👏
Ndine Muslim koma akuluwa amandivetsa kukoma kwambiri ndimawu wawo👏🏻
Amen pastor and thanks,let God be God
Amen and amen point and powerful 🙏🙏🙏🔥🔥🔥
Powerful sermon
Amen powerful message
Aleluya and Amen and Amen 🙏 Kuna Mwari kudenga
Ali ndi makutu akumva wamva. Osamva ndi osamva basi. Amen
powerful massage
Amen mawu achilimbikiso
That's true man of god lm bresd here in cape town
Mumandidalitsa pastor ambuye akudalitseni
Koma mumandimasula mu zambili abusa olalika chilungamo🙏🙏
Amen abusa olalika chilungamo ngati awa palibeso
Amen PS Alexander
Kambri, chifukwa cha mtima wa nsanje, powerful
Powerful massage
Very powerful message
Am blessed
Kumva kukoma pastor ndi ulaliki wanu
Amenii abusa
Abusa awa palibesoi amalalika chilungamo 🙏🙏🙏
Watching you live from here at jcc, RSA,
One month ago here at website launch,,
May God keep blessing you.
Inu amene uthenga wa abusa a kambri umakuipilani musataye nthawi kuverera ife tiziverera tilipo
Powerful message
Powerful
Amen and amen
Chilungamo Nd mwano
Zachabe chabe ndipo zonsezi nzachabe
❤
Amen 🙏
Mumandisuntha kwambiri
🙏
Amen
Uthenga wabwino kwambiri
Amen amen abusa
Gud news
Mqaphunzitsa moyo wanga, ndasiya nsanje ineeeè
AMEN
Abusa mumakwana ndipo uthenga wanu umatiphunzitsa zambiri
This is my brother 😂😂
Chilungamo sashatila abusawa akutivetsa kukoma
Uthenga wabwino kwambiri. Kumalalikila zachilungamo Mulungu amasangalala. azitumiki ambiri ndiofuna kuziunjikila chuma sapembeza Mulungu mwini dziko lapansi ndikumwamba.
Your preaching is touching me more in my heart
Mbambande
Mlaka malilo
Kkkk, this is my brother wow
Praise lord
NDIKUKAIKA NGATI MUNTHU ANGAGONE KAPENA KUKHALA PA INTERNET ABUSAWA AKULALIKA
Kungokhalira kuzuzula pena muziphunzisa osamakhalira kuzuzula.
Nkutheka kuti mwina inuyo mumanvera ulalikiwu muli kale ndi mbali yomwe mudasankha, ndiye mumangonva koma osanvetsetsa, kudzudzulana zikamalakwika nkofunika ndithu.
@@twinktv6350 anthu akudana ndichilungamo ame
Pena umazalalikila mumisonkhano ya ndare munthu wa mulungu ndi ndale zikukumana pati
Poyamba mudziwe kuti ngati mukuti pa misonkhano ndekuti pamalopo pamasonkhana anthu nde mudziwenso kuti tikachotsapo ndalezo anthuwo ndi ake ndithu a Mulungu, pamenepo mpamene zimakumana, choncho ndale si cholepheletsa kuti anthu asalalikidwe. Nchifukwa chake olo pamaliro pamalalikidwa ndithu ngakhale wena akulira pomwepo kufuna kukumbutsana kuchita chifuniro cha Mulungu.
Koma lilipo siku limene muzaphunzisapo anthu za Yehova kuti amuziwe? Kungokhalira kunyoza anthu ndikumapempherera anthu zoipa zokha zokha. Ndikukayika ngati mbusa iwe unapitako ku bible koleji. Zimene umalalikila sizikuveka olo pang'ono.
Each and everyone has got his or her own calling ... Ngati iweyo calling yako ndiimeneyo yoona zofooka zaanthu amulungu ... Mulungu akukhulukileni ndikukubweletsalani anthu amulungu onga awa Oti akuzuzuleni
Sitikhalira kunyoza anthu ayi, munthu ukakhala kuti sukunvetsetsa umaona ndi mmene iweyo ukuganizira, vuto limeneri inuyo mulinalo. Kupemphelera anthu zoipa zokha zokha nde kofunika zedi cholinga choti asiye zoipazo azichita zabwino. Nanga kodi tingamapemphelerane kuti tisiye kuchita zabwino?, ayi ndithu, pakufunika kuti muthandizidwe ndithu mwapaderadera, chifukwa ngati mukuti simukunva chilichonse kuyambira kuwelenga Bible mpaka kumaliza ulaliki ndekuti pali vuto.
Uyu munthu mubusa wakuyooya makola chomene and wakuyooya nkhana makola chomene, wakuyooya kose kose, not only shouting, wakuyooya naumo wawelengela mutu wa bible, am very happy with him, Pitilizani abusa osasiya osavela za anthu , And uyu kubusa nimunthu muwemi coz iye wakulalikila kumuzi not ivi wakupanga ma busa yanyake yanchuka aya chaa waka ma million mphaa vabweka utesi wekha , kwe uyu wakuyooya nkhana exactly umo chalo chilili pasono, wakuyenela kupephela nthena indeed, iye walinavo nachito vakutauni yyso or kuyenda malo uku na uko pitilizani basi iyaa , happy for you 😄
Kondwani Harawa I agree kwambiri. The reason why this world is finished is evident in such type of sermons. People prefer this preaching to tickle their ears. It’s mostly moralism and jokes. Sadly, most people think they are being fed spiritually. No wonder millions are headed for hell.
The truth is supposed to pierce one’s heart not be anticipating laughter. The reason why this guy is trending is because he makes people laugh. Not that people are getting saved or knowing the truth.
Ecclesiastes 7:4
The heart of the wise is in the house of mourning, but the heart of the fools is in the house of mirth.
@@Kuwacha6075 me too l'm happy to him
🚨🚨 PHILL J - ZAKOMA
PRODUCED BY MAGULU
DOWNLOAD NOW ⚡🔥: malawitunes.com/track/BtKYGgtLuqZJ2AB
GET THE BEST OF URBAN MALAWIAN MUSIC ON www.malawitunes.com TODAY!
Powerful message amen
Powerful message
Powerful
Amen n amen
Amen and Amen
Is true
Amen
Amen
Amen
Powerful
Amen and Amen
Amen
Amen
Amen
Amen
Amen
Amen
Amen
Amen
amen
Amen
Amen
Amen