ANEBA ATHU AKUTISEKA KOMASO KUTIPOSA MUZOCHITIKA IFEDI NDI A NTHABWALA KUYAMBA NDI PRESIDENT

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 25 окт 2024

Комментарии • 62

  • @jamessheki4293
    @jamessheki4293 3 дня назад +6

    Chitsiru china ku Zambia nkumayimba nyimbo kuyamikira Malawi shame 😢

  • @IsmaelBilal-lh1pi
    @IsmaelBilal-lh1pi 3 дня назад +12

    Achakwera alibe mphavu zoposa Chimwendo Banda....Chakwera amawuzidwa zochita😢

  • @gmxplayboy6559
    @gmxplayboy6559 3 дня назад +9

    Kodi ku Malawi kuno kuli President? Chakwera adakanika kutsogolera mpingo ndiye angakwanitse kutsogolera dziko? Chakwera akumayendera nzeru za Chimwendo Banda

  • @BrightMajor-h8l
    @BrightMajor-h8l 3 дня назад +5

    Maiko osiyana mapresidentnso osiyana, wina ochangamuka wina opepela ogwa ndondoli

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 3 дня назад +1

    Zimene zikuchitika kumalawi Kuno kuziganizila zikuwawisa Mutu And chakwera zot ndi Muthu ndakaika

  • @abrahammkandawire4039
    @abrahammkandawire4039 3 дня назад +1

    Simungafananize NDI Chakwera akuluwa uyu ngwa nzeru wathuyu alibe nzeru

  • @misoMoyo
    @misoMoyo 3 дня назад +1

    Chakwera akuopa Chimwendo sangapangei chili Chonse Pano pule ndi Chimwendo 😊

  • @FlossyAtupeleNyasulu
    @FlossyAtupeleNyasulu 3 дня назад +1

    Well done president Hichilema

  • @FrankWines
    @FrankWines 2 дня назад

    🎉Mmesa anawasankha ndi Iyeyo alephera bwanji kuwachotsa, zowasankha ngati Alinazo zowacbotsanso Alinazo koma vuto a adyera mbale imodzi

  • @RosinaPatel
    @RosinaPatel 3 дня назад +1

    Sangamakane..awa ndi ma real politician

  • @andiwochishadreck3753
    @andiwochishadreck3753 3 дня назад +1

    Congratulations 🎊

  • @JonesBenNgaiyaye
    @JonesBenNgaiyaye 3 дня назад +1

    He knows nothing about administration more especially inthe running of this country,but God is watching panda pusha

  • @Dauson-j5i
    @Dauson-j5i 3 дня назад

    Umenewo ndiwo usogoleri kuganizira kuti anthu ambiri asabvutike chifukwa cha anthu ochepa well done apule akuzambia

  • @SteveNdhlovu-r2x
    @SteveNdhlovu-r2x 2 дня назад

    Kuno acb inatha nthawi ija anagwila mayi chizuma MOTi anthu aku acb akulandila ndalama zaulele. Misonkho yathu kumangowonongeka zovuta kwambiri

  • @JamiesonKaunda
    @JamiesonKaunda 9 часов назад

    Ndi chinyengo cha majajinso chinamuika chakwera pa mpando chifukwa popanda majaji chakwera sakanakhala pa mpando amalawi tikuvutika chifukwa cha chinyengo cha majaji

  • @PollyLysonLutepo
    @PollyLysonLutepo 2 дня назад

    President Chilema Siwa Chinyengo, Ndichochifulwa wachotsa ma Judge a Chinyengo.
    Wathuyu ndi ntchito yake. Sangachotse omwe akumubakira akaba.

  • @HajaSande
    @HajaSande 3 дня назад +1

    Ndiyekuti majajiwo alimbali yaboma zachinyengozo zikukuza boma

  • @TayibuUmalikauta
    @TayibuUmalikauta 2 дня назад

    Indedi tilibe nsogoleri ife oganiza bwino amaganiza mopelewela ndithu simukunama

  • @ElatonGwaza-k4h
    @ElatonGwaza-k4h 3 дня назад

    Kuno kumalawi aliyese ndiwakuba ndiye amawopa kuyaluka

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule 3 дня назад +1

    Good

  • @ellensambo6323
    @ellensambo6323 3 дня назад +1

    Zovuta 😢 bolani aneba zawo zikuyenda

  • @Alice-z7t4z
    @Alice-z7t4z 3 дня назад +1

    Chakwera sangapange zimenezo amamvera chimwendo

  • @Thewarrior7093
    @Thewarrior7093 3 дня назад

    Chakwera ndi president opusa ogunata alibe luntha ndi nzeru za utsogoleri. Mulungu amulange galu ameneyi he doesn't deserve to rule this country.

  • @MichaelMagombo
    @MichaelMagombo 3 дня назад

    Chakwera sangakwantse kuchosa munthu chifukwa pa anthu omwe akuba mubomamu iyeyo ali pa number 1

  • @emmanuelalbertbotolo
    @emmanuelalbertbotolo 3 дня назад +1

    Chakwera ndiwachingo mwino ndiye achotsa bwanji ena iye zikunkhuza

  • @MarkoSimon-q3b
    @MarkoSimon-q3b 3 дня назад +1

    Apulezident. Athu. Akuopa. Kuti. Adzawa ulula. Kuti. Nawonso. Ndi skatangale bola. Kungo. Khala. Chete.

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 3 дня назад +3

    Zochita mu dziko lathu utha kutopa ndiwe olankhurawe

  • @dinchisale
    @dinchisale 3 дня назад +1

    Prezident wathu Dr. Chakwera alibe maganizidwe a tsogolo LA dziko lino posaonetsa mphanvu zakuchita zinthu posatira malamulo oyendetsera dziko lino, komanso ndimunthu yemwe Ali ndi mtima osawerengeta kuti Malawi Ali pansi pa ulamuliro wa democracy, komanso Ali ndi moyo wodelera malamulo oyendetsera dziko lino

  • @MichaelMagombo
    @MichaelMagombo 3 дня назад

    Ku Zambia achotsa ma Judge pamene ku Malawi akufuna atapha waulula chinyengowo

  • @chrisboyce2
    @chrisboyce2 3 дня назад

    Chimwendo Banda kms Puppet wake Chakwera ndi omwe atiwonongera Dziko lanthu labwino bwinoli ( Mulungu akulangeni pansi pompano Mr Chimwendo band a kms iwe Chakwera afiti osekelera)

  • @JohnWame-u3l
    @JohnWame-u3l 3 дня назад +1

    Ndi mbavatu osewo akaba winayo amadyera limodzi

  • @PromiseNduna
    @PromiseNduna 3 дня назад

    Chakwera akuopa kuikapo mulomo chifukwa akudziwa naye zake ziululika

  • @ChimwemweSauka
    @ChimwemweSauka 3 дня назад

    Chakwera sukuziwa kanthu pa kuyendetsa ziko,ubweleraso ku chipiku azikapakira Nima mu shelfu

  • @WysonAdamu
    @WysonAdamu 3 дня назад

    Koditu dziko lanthu lamalawi likuyendesedwa ndi anthu amisala onkhaonkha

  • @SteveNdhlovu-r2x
    @SteveNdhlovu-r2x 2 дня назад

    Hakainde wakhala ku opposition kwa zaka zambiri. Iyi ndi term yake yoyamba koma Ali ndimaganizo otukula dziko lawo. A pule athuwa sangachite manyazi?

  • @Henry-vw2cz
    @Henry-vw2cz 3 дня назад

    Chakwela chomwe amadziwa ndi kuba ndi kupha

  • @IBRAHIMCHIPASULA
    @IBRAHIMCHIPASULA 3 дня назад

    Malawi ndi dziko lovetsa chisoni

  • @kantayeniphiri4016
    @kantayeniphiri4016 3 дня назад

    Always aMalawi mumayamikira zobwera shupit

    • @cwsteve8233
      @cwsteve8233 3 дня назад

      That unpatriotic man, you sounds to be behind those schemes.

  • @mabvutomichaelpanagona1949
    @mabvutomichaelpanagona1949 3 дня назад

    Achakwela ndi achitsiru palibe chimene akuchita chifukwa nayeso ndi wakuba akuopa kuti amuulula ndichifukwa akungokhala duu

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili День назад

    Hakainde ali ndi maso mphenya uyuyu chakwera full of curruption its like mulibe president mudziko

  • @InnocentHassan-m3r
    @InnocentHassan-m3r 3 дня назад

    Atsogoleri am'zeru okonda dziko lawo,,,,chakwela ndiwakubaso nde zikhoza kum'vuta

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 3 дня назад

    Chakwera osafanizila ndi H.H waku Zambia ai. Malawi ndi yopoila kwambiri. Zambia kuli utsogoleri osati ku Malawi.

  • @InnocentEdasi
    @InnocentEdasi 3 дня назад

    Mwachakwela mulibe utsogoleli

  • @HajaSande
    @HajaSande 3 дня назад +1

    Khoswe akakala pasuko sapheka

  • @LeyvanSamuel-pe5tc
    @LeyvanSamuel-pe5tc 3 дня назад

    Kuno sizingatheke akuyambisa katangale ndi president yemweyo. Akakhala pakhate sapheka

  • @RodgersPhiri-ju1eo
    @RodgersPhiri-ju1eo 2 дня назад

    Iwenso machende ako wasowa zochita kodi pitala wanuyonso nkhalamba ija analephela ma chende amako bussy kumangokhalila ndale basi nchifukwa chake mukudya ziteze agalunu

  • @DigleDafter
    @DigleDafter 3 дня назад

    Kodi president ndi chakwera or chimwendo Malawi kuvusa chisoni neba wathu uyu kuchita chiganizo mwasanga osati disotuzu osachitapo kathu zochita kuoneka kuti uyu ndewaba koma kusakha kukhala chete

  • @WanangwaMfune
    @WanangwaMfune 3 дня назад

    Nanga kuno zikhala bwanji?

  • @UmariBashiri
    @UmariBashiri 3 дня назад

    Pa jatu Ali pamenopo chifukwa chachinyengo

  • @Preciouskamkwamba
    @Preciouskamkwamba 3 дня назад

    Nanga amalawi zikuvuta pati? Kunena chilungamo chakwera is a greedy president of all president's in Malawi. Amakomedwa ndi ndalama. That's why he is being used by many business tycoons to turn the country upside down.

  • @MartinLondon-l4l
    @MartinLondon-l4l 8 часов назад

    Iwe unasowatu timawu tachifuwa eee, usanamize amalawi pano ndili konkuno ku zambia. Ma judge omwe awachotsa kuno akuyikila kumbuyo former president ecl kuti ayimenso, osamanamiza a malawi kuno mazambian akuwona kuchedwa 2026 kuti a kulamulayu amuchotse

  • @HassanSaid-q8q
    @HassanSaid-q8q 3 дня назад

    Watuyu ndichisilu opanda mzelu ndiwa kumidima

  • @ziwani3682
    @ziwani3682 3 дня назад

    Chakwera ndiye mwini Yake wakatangale

  • @WallyMsiska
    @WallyMsiska 3 дня назад

    Wachinyengo wankulu ndi chakwela

  • @Musachott
    @Musachott 3 дня назад

    Chikawa aligulumo kubamo

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 3 дня назад +3

    1USD =26000MK

  • @DaisonPiston
    @DaisonPiston 2 дня назад

    Kuno abaliti

  • @Mahamudu-q6b
    @Mahamudu-q6b 3 дня назад

    Yes😢😢