JETU SIMUNATCHENE BEHIND THE SCENES FT DYOKHWE

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 10 дек 2024

Комментарии • 77

  • @RosinaWakuthera
    @RosinaWakuthera 4 месяца назад +6

    The truth that abiti Najere is involved just shows the kindness of jetu ... We grow by working together. Bravo Jetu bravo Kanchowa studios 🎉

    • @abccreatives245
      @abccreatives245 4 месяца назад

      Youre right
      It had to cross Jetus mind grabbing NAjere in her vidz otherwise akanathaso kungomutaya palipose
      Thats love

  • @PaulineChinthuli
    @PaulineChinthuli 4 месяца назад +21

    Aaaaa manager wa abit najereyo asatinyasepo angothokoza😅😅

  • @alinafefrazer
    @alinafefrazer 4 месяца назад +14

    Manager waBiti najere akuankhula zambiritu aaaa.... Kungothokoza bas anakuitanan bas aaaa😂

    • @wellingtonmilanzie
      @wellingtonmilanzie 4 месяца назад

      Inenso kudabwatu😅

    • @TsuzenThomas
      @TsuzenThomas 4 месяца назад

      Etieti mmalo mongothokoza kut aonekako mu video ya celeb wankulu bwanj

  • @blessingslupiya366
    @blessingslupiya366 3 месяца назад

    Ntchito munayigwila ma guy🔥🔥

  • @josephchitimbe5396
    @josephchitimbe5396 4 месяца назад +2

    We all never expected this guys bravo to Jetu and his management 👏

  • @ChikumbutsoPhimba
    @ChikumbutsoPhimba 4 месяца назад +2

    Aaaa jetu ndi president bx 😅😂😂❤❤❤❤

  • @EstherSamboh-wb5ni
    @EstherSamboh-wb5ni 4 месяца назад +2

    Manager wa Najere ayankhula mopusasotu. Osangothokoza bwa

  • @ishmaeldouglas5962
    @ishmaeldouglas5962 4 месяца назад +2

    Najere 😂 wafika pati mwati mukamati kuti afike pamene alipa . Kodi wasutha pamene anali kale eti

  • @ElizabetieMailosi
    @ElizabetieMailosi 4 месяца назад +6

    Nanga zugwilizana chani iwe manager wa najele 😢 tangoti zikomo kungoonekakoko basi mutibowe ndikhani zambili

  • @BridgetBester-j9v
    @BridgetBester-j9v 4 месяца назад

    Koma kumakhala ntchitooo mmmmmm🙌🙌🙌

  • @ruthkaunda3343
    @ruthkaunda3343 4 месяца назад

    Komatu kumakhala ntchito 🙌😂this is beautiful ❤

  • @PatrickChilambe-rz8tm
    @PatrickChilambe-rz8tm 4 месяца назад +1

    mumatha madolo🔥

  • @janetGondwe-r8q
    @janetGondwe-r8q 4 месяца назад

    Jetu for president

  • @ireenbanda8517
    @ireenbanda8517 4 месяца назад

    Ayi ntchito imakhalapo🙌🙌big up🔥🔥🥳

  • @emmanuelphetembe4948
    @emmanuelphetembe4948 4 месяца назад +1

    Manager wa abiti Najereyo asathe mawu, akothokoza. Ku music kuli ngati ku ndale kulibe udani

  • @chissomomombanya
    @chissomomombanya 4 месяца назад

    This the 1st most viewed behind the scenes in a day 🎉

  • @maggiekadzombe7658
    @maggiekadzombe7658 4 месяца назад +2

    Choipa chanjiso aaah osangothokoza kuti muli pamap aceleb wankulu abiti najereso nawo

  • @agnessliwonde
    @agnessliwonde 4 месяца назад

    Dyokhwe must be crear on helping this poor woman in the name of manager. Try to help not to benefit from innocent sauls. Help her to excel not to win by yourself.

  • @happinesschitika9556
    @happinesschitika9556 4 месяца назад

    Koma imakhalako eeee😂🔥

  • @gracesawa-zl6uo
    @gracesawa-zl6uo 4 месяца назад

    😂😂😂 komatu please abiti ndi manager eeeeh

  • @emmanuelsiwinda5422
    @emmanuelsiwinda5422 4 месяца назад

    Eeeh km yah😂❤️🔥

  • @TadalaChilichokha
    @TadalaChilichokha 4 месяца назад

    ❤❤❤

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 4 месяца назад

    Big up abiti nanjere

  • @happinesskamwendo2106
    @happinesskamwendo2106 4 месяца назад +5

    Kuzichepesa chani nawe
    Zoduka mutu basi

  • @DivineAbraham-fj3qk
    @DivineAbraham-fj3qk 4 месяца назад

    Aaaah aaaah so abiti najere akuti choyipa sabwezela nkhani yake itiso kkkk

  • @TinnahKhondovela-s9e
    @TinnahKhondovela-s9e 4 месяца назад

    Anafika pati abiti najelewo😂😂😂😂😂😂😂

  • @SpringZee-m9n
    @SpringZee-m9n 4 месяца назад

    Able, simayembekezera chigulu chonchi

  • @Giniahchanza
    @Giniahchanza 4 месяца назад

    Zovala zajambulidwa crown 👑 zo ndo label yanji? Zandisangalasa

  • @nishakaitano
    @nishakaitano 4 месяца назад

    Naye biti Najere ndi Manager wake akuti chani aaah😂😂😂

  • @LindaMugayafriday
    @LindaMugayafriday 4 месяца назад +1

    Nde choipa mubwenzera kwa ndani?

  • @mikkyjackson-bo3lp
    @mikkyjackson-bo3lp 4 месяца назад

    A Manager osayankhula zambiri 😅

  • @samdistone4521
    @samdistone4521 3 месяца назад

    jetu kunyoza naje kumeneko

  • @emmanuelshora23
    @emmanuelshora23 4 месяца назад

    😂😂😂😂Abiti naje

  • @nivycarolnamanja7089
    @nivycarolnamanja7089 4 месяца назад

    Jetu angokhala ngat wandaletu😂

  • @hendresonsande5156
    @hendresonsande5156 4 месяца назад

    Jetu anabwela kuzakhala Komaso madolo oshuta video WA eee ndimadolo amatha

  • @MaulenikingPhiri-r9v
    @MaulenikingPhiri-r9v 4 месяца назад

    Sanatchene leroli😂😂

  • @Ungweray
    @Ungweray 4 месяца назад

    Kkkkk koma Jetu unadza🔥

  • @elliousBowman
    @elliousBowman 4 месяца назад

    Eeeee imakhalako

  • @KanyengaMatres
    @KanyengaMatres 4 месяца назад

    ❤❤❤❤❤

  • @austindickiesainani5766
    @austindickiesainani5766 4 месяца назад

    mpaka bible limanena kuti kkkkkkkkkkk kusunga mngawa basi 🤣🤣🤣🤣🤣

  • @georgechikafutwa1334
    @georgechikafutwa1334 4 месяца назад

    Tivine zimenezi😂😂😂😂

  • @MphatsoGona-px6bq
    @MphatsoGona-px6bq 4 месяца назад

    manager wa majere sanadziwe Kuti awa dissa najere mkuitana najere

  • @kantande
    @kantande 4 месяца назад

    Akati choipa sabwezera anawapangira choipa ndi ndani?

  • @josephchitimbe5396
    @josephchitimbe5396 4 месяца назад

    Ife sanje tilibe welcome Najere

  • @karenmalindi-xc1jc
    @karenmalindi-xc1jc 4 месяца назад

    Kodi ukuti chani? Tangothokozani😂😂😂

  • @PromiseZimba-x6t
    @PromiseZimba-x6t 4 месяца назад

    😂😂😂🎉🎉

  • @DraidaBusili-wu5lg
    @DraidaBusili-wu5lg 4 месяца назад

    Waitha najere

  • @ChristinaChibwana
    @ChristinaChibwana 4 месяца назад

    Jetu ati bigili yodula🤣

  • @AlnordMaleca-ll2xb
    @AlnordMaleca-ll2xb 4 месяца назад

    Mpaka t shirt ya a'ba.lé

  • @Filomift
    @Filomift 4 месяца назад

    Zinali bho🎦

  • @Its_Desire05
    @Its_Desire05 4 месяца назад

    Koma kumakhala ntchito eh😂

  • @chikondichabwera6974
    @chikondichabwera6974 4 месяца назад

    Fans kuchita kuposa wina wake

  • @Japlennthondowa
    @Japlennthondowa 4 месяца назад

    Mamba chani

  • @SleepyLake-nf7dc
    @SleepyLake-nf7dc 4 месяца назад +1

    Ndipo choipa sitibwezera ndithu

  • @tawongakakusa3437
    @tawongakakusa3437 4 месяца назад

    Behind the scenes ya Nambe simunaponye bwa?

  • @TryPhiri
    @TryPhiri 4 месяца назад

    Mp jetu

  • @CedricChavi-f4z
    @CedricChavi-f4z 4 месяца назад

    Kwachema tu

  • @andresmiguel258
    @andresmiguel258 4 месяца назад

    Nchito mwagwira

  • @WonderBen-q1k
    @WonderBen-q1k 4 месяца назад +1

    Choipa sabwrzera

  • @gospelmagaleta7479
    @gospelmagaleta7479 4 месяца назад

    Tachoka iwe

  • @PetrosMhone
    @PetrosMhone 4 месяца назад

    Zomwe zikundibowa apa ndi ma comment omwe ena akupanga ati najere adisidwa alimomo aaaaaaaaa

  • @Truly_Arthur
    @Truly_Arthur 4 месяца назад

    😂🔥🔥

  • @TsuzenThomas
    @TsuzenThomas 4 месяца назад

    Nanunso aNajere nd manager wanuyo mukuchulusa zokamba mwatani kodi, mot munakangoti zikomo kut mwaonekako mu video ya celeb wankulu

  • @FloraBanda-w7t
    @FloraBanda-w7t 4 месяца назад

    Kumalawi chikuvuta ndi njala basi

  • @tissybonomali6611
    @tissybonomali6611 4 месяца назад

    Zobhebha

  • @ashersiska9498
    @ashersiska9498 4 месяца назад

    Koma abiti naje

  • @perpetualmsonda
    @perpetualmsonda 4 месяца назад

    🔥🔥🔥🔥

  • @Bigceemacover
    @Bigceemacover 4 месяца назад

    Typing..............

  • @AaronMwandira
    @AaronMwandira 4 месяца назад

    Building ina 😂

  • @JackSelemani
    @JackSelemani 4 месяца назад

    Kawawa