COMRADE NTANYIWA "06/11/2024" - KUKUBWERA MA DEMOSTRATIONS ANYOOOO!

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 5 ноя 2024

Комментарии • 78

  • @FransincoChirwa
    @FransincoChirwa 15 часов назад +10

    kumeneko ndiye kuyankhula kwachinvenve tiyenazoni oasaopa tikunva kupweteka ndipo mulungu arowererepo amen

  • @GraceChikosa
    @GraceChikosa 5 часов назад

    Woooooow boss Comrade Mtanyiwa 🎉🎉🎉🎉🎉Inuyo pangani zotheka mkumene ndipo am very happy to here that ndipo ofunika mukatumedi nthumwi yanu kupita kunjaki .. may the Good Lord protect you wherever you are boss Mtanyiwa .. you're still kutimvetsa kukoma ife a Malawi anthu osauka ❤❤❤

  • @TimeAbilu
    @TimeAbilu 16 часов назад +3

    Most welcome Mr comrade mtanyiwa 100%

  • @EllenGomani-i4f
    @EllenGomani-i4f 5 часов назад +1

    Mumakwana Comrade ❤❤

  • @HashmInnussa
    @HashmInnussa 18 часов назад +4

    We have to take action and they must know that we are not interested with smartmatic.

  • @SelinaGamaliyere-q8v
    @SelinaGamaliyere-q8v 13 часов назад +5

    Agalu amenewa atikwana achoke

  • @NoahPeter-t6h
    @NoahPeter-t6h 16 часов назад +5

    Poyamba ndikupempha anthu ndi mabungwe omwe anachititsa kuti anthu awa alowe m'boma munatisokeresa ndinu ndi DPP sitimavutika chonchi koma mtambo ndi anzake apite pamsewu atichosere Mikango anatibweretserayi

    • @EverlantNdeule-w6t
      @EverlantNdeule-w6t 14 часов назад

      Zoona anakwanitsa kumenyela. Khondo kuti chakwera akhale pa mpanda ndiye pano zikuvuta pati zisilu zimenezi ndizomwe zatipwetekesa

  • @PaulRice-c5f
    @PaulRice-c5f 14 часов назад +2

    Amalawi anzanga tiyeni tiziwona patali
    Chonde chonde ili si boma
    Azipani zotsutsa pempho
    Mugwirane manja
    Pakufunika mademo anyooo mademo okwiya
    Otsutsa osango yan'ganira zonunkha ngt zimenezi

  • @RabeccaChiumia
    @RabeccaChiumia 17 часов назад +2

    Inuyo ndi achina kalindo ndi omwe mumaika mcp pampando nde muwachotsaso nokha munatipusitsa😢😢😢😢

  • @PaulRice-c5f
    @PaulRice-c5f 14 часов назад +2

    Mau amenewo mtanyiwa
    Osango yang'anira nyansi ngt zimenezi

  • @HamiltonwaNamuwah
    @HamiltonwaNamuwah 17 часов назад +2

    Yah, zoyankhuladi zakwana , akufunika action tsopano. Chifukwa Chakwela waumitsa mtima kukhetsa mwazi basi

    • @AgnesChirwa-n4u
      @AgnesChirwa-n4u 17 часов назад +1

      Munthuyitu akuyesesa kutiunikira komaifetilindwiiiii

  • @PeterKainga-e3h
    @PeterKainga-e3h 14 часов назад +2

    Ndipo imeneyi azipani zotsutsa tikudikirai inu tisamangokamba nkhamba kamwa

  • @FortuneNdawala
    @FortuneNdawala 14 часов назад +1

    Ngati akakamila machine amenewo atule pansi udindo pabwele boma logwiliziila mpaka September 2025 basi.

  • @LuckiaMatemba
    @LuckiaMatemba 16 часов назад +1

    Akambilane atiuze zochita sure 😊😊😊

  • @EverlantNdeule-w6t
    @EverlantNdeule-w6t 14 часов назад +1

    Kod nyimbo yamademo ituluka liti chifukwa ndiyetu zatikwana munayambira muja mademo koma mademo sakuchitika ndiye mukuona ngati zinthu zisitha ndima Audio

  • @LOKAMJ
    @LOKAMJ 16 часов назад +1

    Malo mokonza dzikoli koma kufuna mangotiberabe pa zinthu zopanda pake,,,,bora ndalama zimenezo akanagulira fertilizer ndikugawa Kwa anthu,,,shame....akakonza manda kut mwina anthu azavotere,,,, Boma ili tatopa nalo,,lichoke

  • @TakondwaSulani
    @TakondwaSulani 15 часов назад +1

    ❤❤❤ Mademowo akuchedwa pati ndizomwe tikufuna anamuchotsa peter muthalika ndi mademo koma pano zinthu sizilibwino mumangoti ma demo koma kulizii tapangani zakupsa comrade

  • @IvyKanyenje-d1c
    @IvyKanyenje-d1c 15 часов назад +1

    Munatipusitsa Amtanyiwa ndi amwanja kalindo kukavotera mavutowa inunso onetsani action mulichotse boma limeneli nokha musamangolimbana ndi otsutsai inuyo mukhale patsogolo

  • @MartinoBanda-c8k
    @MartinoBanda-c8k 13 часов назад +2

    Nkhaniyo ndiyoona

  • @WandileTradding-ph6fb
    @WandileTradding-ph6fb 13 часов назад +2

    Vuto mumangowuwa muli kumpnda akananena Bon kalindo ndi Anamiwa tikadava inu muli ngati gulu wapachingwe chimene mumadzibisila ndichani zikuwonetselatu kuti ndinu achitsilu kwambili

    • @AyamiMustafa
      @AyamiMustafa 2 часа назад

      Iwe pamtumbo pakho galu iwe pamnyelo pa mayiwakho iwe nyatsu munthu ophutsa kwambili iwe ndi ndani kuthi ukayakula nyatsi ngati zimenezo iwe ndindani Kapopa ngolo ngati iwe comrade akumenyela ufulu wakho galu iwe ndiye uzikayakula manyi ngati amenewo mbunzi yamwana fuseg msunu kanyoko wa Bazali bakho wena

    • @AyamiMustafa
      @AyamiMustafa 2 часа назад

      Undiyakhe ine ndipanga kanthu kwaiwe galu iwe ine ndiye ndikoza kukupetsa kwa mcp omwewo

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 17 часов назад +1

    tizingokhalira MCP this 7:56 MCP that no action zikudwalitsa mutu zedi a Malawi tili ndwiii,Tizangw'empha sure

  • @MpasulavisaSonjo
    @MpasulavisaSonjo 17 часов назад +1

    There no evidence. We need evidence based issues

  • @kaheboAcafish
    @kaheboAcafish 5 часов назад

    Msalankhure za DPP apa tikufuna UTM, AFORD AND UDF. DPP ndi imene inayamba kuononga ziko lamawi

  • @SteynMaduka
    @SteynMaduka 17 часов назад +1

    Akuwona ngati nde anthu Atha kuwavotela chifukwa cha zimenezo, mukuganiza kwao

  • @ephraimphalawala4720
    @ephraimphalawala4720 15 часов назад +1

    We support

  • @HlupekileMazunda
    @HlupekileMazunda 16 часов назад +4

    Angochoka tatopa nawo zinthu kukwela dairy

  • @FredKanyerere
    @FredKanyerere 17 часов назад +1

    Amen powerful comrade.

  • @lyiemanganjira9708
    @lyiemanganjira9708 15 часов назад +1

    Mademowo mukuchedwetsa kaya 😂😂😂😂

  • @TchakaChisuse
    @TchakaChisuse 15 часов назад +1

    İnu nda boni kalindo timophy mtambo manganya mitu yanu sikoka ai musamatitenge kupusa inu ndinumudamumenyera nkhondo chakxera inu damene numuchotse sind ife opusa amalaxi

  • @jelozalbzakaria7978
    @jelozalbzakaria7978 13 часов назад +1

    Monga ine ndili ku Vietnam

  • @NelsonKasanga-b6q
    @NelsonKasanga-b6q 17 часов назад +1

    Asewe basss sitikufunaso efe

  • @KunyengaMoyo
    @KunyengaMoyo 14 часов назад +1

    Vuto mademo mumawalengedzetsa for a month then date likakwana boma limapangapo kanthu mademo nkulephereka, ku SA chomwe amapanga akuluakulu amakambirana kukonza tsiku lamademo then amazalengeza usiku mademo amawa kukacha umangomva whistle basi mademo ayambika km kumalawi mmmmmm

  • @MagieJames
    @MagieJames 17 часов назад +1

    Makwanira inuyo boss mulungu akudaliseni zipani zotsutsa zikakhala chete nd zawo

  • @JoelTchuma-g3s
    @JoelTchuma-g3s 10 часов назад

    Azipani zo sutsa nganizirani izo anthu anu akutikiramu omadya nazo chitedze,kodi zikachitikanso ndi iowa zidzala zotani pomwe a Malawi ngosaphunzira zidzatani?Tadzukani kutulo.

  • @FavouredMasambuka
    @FavouredMasambuka 10 часов назад

    Tikuyenera tonse okhudzidwa kuchitapo kanthu ndpo tidzakhale ndimademonstration amphamvu Malawi ndiwathu uyu chakwera asatipusitse

  • @sabinaphili
    @sabinaphili 16 часов назад +1

    chipatala cha thyolo mazi anadula kale kale

  • @IdahKadewere
    @IdahKadewere 17 часов назад +1

    Kod abon kalindo dzulo sanapezeke leroso agwidwa kapena adwala chifkwa dairy timawavera ma audio

  • @KelvinMangwengwe
    @KelvinMangwengwe 15 часов назад +1

    Mawu mawu mawu comrade

  • @ThomasSalaka
    @ThomasSalaka 6 часов назад

    Where is opposition parties?

  • @nyanguoipa6996
    @nyanguoipa6996 10 часов назад

    Kuwona Kwa ine chimafunika mademo ake akanakhala oti achakwela atule udindo pasi.

  • @Christopherchapeta-q2j
    @Christopherchapeta-q2j 11 часов назад

    Koma ma activectes Kodi mwalembetsa my kaundulu wa ma vote

  • @stephanonkungula5858
    @stephanonkungula5858 16 часов назад +1

    Go komko

  • @alfredmahere2553
    @alfredmahere2553 4 часа назад

    Chikangawa must go

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 12 часов назад

    A ntanyiwa ma audio okha atitopesa nothing change mene munayambira muja ndiposo mukubisala nanga mademowo tipanga ndindani pomwe inu mukubisala

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 16 часов назад +1

    Kod amtambo ali kuti sindikwawonatu ali chete

  • @MaxwellKapalamula
    @MaxwellKapalamula 15 часов назад +1

    Chakwera ndi chiwanda

  • @ReginaMulipa
    @ReginaMulipa 11 часов назад

    Nanga Chocho paka November athe koseko paka tiliwe December manyaka Malawi MOTi mukanayambila pompano koma paka mwezi uthe nde ndiliti limenelo

  • @FredKanyerere
    @FredKanyerere 18 часов назад +1

    Let's show action.

  • @peterbyson6269
    @peterbyson6269 18 часов назад +2

    Guys anthuwa atikwana asiye pansi udindo

  • @Blessings-b7h
    @Blessings-b7h 6 часов назад

    Ifedi ndie ndife ofoira chifukwa tikulekelera zinthu zikuonongeka.

  • @VeronicaChirwa-ct4os
    @VeronicaChirwa-ct4os 9 часов назад

    Ndi pastor wa pansi pa nyanja galu wa chabe-chabe

  • @GiftChilanga-u3c
    @GiftChilanga-u3c 10 часов назад

    Chakwera watikwana kokwanira pompano wuwona mademo omwe tichita chonde zipani zosusa gwiranani manja

  • @GraceChikosa
    @GraceChikosa 5 часов назад

    Ndi zitsilu amene akunena zokuti boma ndilomweli ... Akagwere uko anthu amenewo

  • @ThomasSalaka
    @ThomasSalaka 6 часов назад

    Tizakhale ndi kavotedwe ka manual not electronic please!

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 12 часов назад

    Muzipanga mademo anu koma ssmatic sichoka mpaka kale chakwera azingolamulila kaya muphwanye zinthu mapeto ake ma election alephereka chakwera azingolamulila inuyo muzilila

  • @ThomasSalaka
    @ThomasSalaka 6 часов назад

    Mtambo please! Come up

  • @phillipstamaley7901
    @phillipstamaley7901 11 часов назад

    Muwuze amanu kuti akachite demo

  • @VeronicaChirwa-ct4os
    @VeronicaChirwa-ct4os 9 часов назад

    Mademowa akanangokhala ongomuchotsa Chakwera

  • @HamzahMiles
    @HamzahMiles 10 часов назад

    Kodi guys inuyo mulibe kuthekera komasowesa modzi modzi ku mcp ku, Aaaaaa or kungomusowesa, kukhuyu ndi Kamwendo basi

  • @phillipstamaley7901
    @phillipstamaley7901 11 часов назад

    Chokaa iweee mbuli ya munthu

  • @JacksonBanda-x9s
    @JacksonBanda-x9s 6 часов назад

    Welcome Ntanyiwa chakwerayu abanduke

  • @VeronicaChirwa-ct4os
    @VeronicaChirwa-ct4os 9 часов назад

    Ndi zitsiru zokha-zokha zimenezi

  • @GeoffreyMaulana-rh5rx
    @GeoffreyMaulana-rh5rx 10 часов назад

    2.8 billion pamandapokha that's tatol nonsense

  • @IrvinLeo-y1n
    @IrvinLeo-y1n 18 часов назад +1

    Ulem wanu

  • @NtabaKali
    @NtabaKali 17 часов назад +1

    Okay

  • @StalnLossan
    @StalnLossan 17 часов назад +1

    Zoonad tidikira

  • @wezimwalebanda-ux4sm
    @wezimwalebanda-ux4sm 18 часов назад +1

  • @andiwochishadreck3753
    @andiwochishadreck3753 17 часов назад

    Please malawi