People have power more than the army and police. Malawians shouldn't be intimidated These institutions are there to defend and protecting Malawian not intimidating please. Intimidations and threats will never work.
Ok ,,vuto ndiloti wamkulu wa army amachita kupangidwa apoint by the state president, had it been amachita kuvotedwa or through applying on vacant position bolaaaa,, but mene wanenera DC its so pathetic, MDF must stand between, and i feel sorry akamalankhura these Institution leaders does not regard that in their departments there are mixed people with mixed political parties, such that writing one biased stanza might violet some😮,, Ku MDF, kuli ena a DPP, UTM, MCP, UDF, AFORD, PP sikuti they are all happy with biased statements and actions carried out
Kodi a police wonse Ku Malawi ko NDI army yonse ndizi tsiru zokha zokha eti?Achitetezo ama lowerera za ndale,tinali Ndi general Chigawa Osati Chitsiruu ngati chimenechi, ndipamene chiri kuda bii Ngati makala mpamene adapha nawo Chilima panyini pa Mache wamkulu wa polisi yoo, Ndi Wa army yo,tizawona DPP akayamba,akuchoka amenewa pa Nyero pa azimayi wao wonsewo
Koma bwana kalindo mumatiimilila amalawi koma apapa zikuonekelatu kuti anthuwa ndiomwe aja anali ku MCP kumbuyokuja MOTi mwina ma president omwe anali pakatipa maybe sakawakonda zikuonekelatu kuti amafinya chifukwa wa ame sangazilowelela izizi aaaaaaaaa
More fire Mr DC may God give you long life to stand for Malawias
Iii koma chaswatu ndipo chadelera mpaka kutchula mayina a zigawenga 😂😂
That's is ambassador of Malawi ❤❤❤❤
Well spoken that's bravo the DC am here at Ndalapa GVH Chimwala TA Mabuka ❤❤❤
Moni kundalapako but just make sure that on these coming elections you must vote wisely
Long live mwana wakwathu🎉💪🔥🔥
The Dc he waz once a teacher ilove that words just teach them mr kalindo osaopa
Not 100 people,18 milion people in malawias wi like kalindo
In malawi if we can have 100 people like Bon kalindo we can have better malawi
Exactly
Kalindo umatha comrade 🎉🎉🎉🎉❤ velantino Phiri , mapwala akeso Pati???
Uyu saamapanga nawo zauchitsiru, zamantha
Mwana woopsa kwambili The DC
The most dangerous child ❤❤❤
❤❤❤❤❤❤❤ the deeeeceeee
More fire🔥
Eeeee Koma Kalindo Guys 😂😂😂😂
The DC🔥🔥
Umakwana brother kalindo
Namiwa, born kalindo, Bakili muluzi TV, Limpopo FM, apa surah Iman, plus chisale inu mwanyamula Malawi 🇲🇼 or amene akulamula Ali ndi mantha
THE DC ❤❤❤
Iwed nd mwana wooopwa kwambiri big up Mr DC
ati Dala Kadula ndidzakutikita kwambiri hahaha....Dala Kadula nde utinso abale?
The DC ulemu wanu big
Chulungamo Chenicheni
Wamkulu wa army bwanji wogwira ntchito mopusa ngati munthu wamba mukuchitisa manyazi anyamata anu kumeneko tikuziwa sionse zikuwakonda mukuchitazi akuopa kukuzuzulani poteteza ntchere wawo
Koma aphili amenewa azangwilidwa nkholingo kuchiona chinkhopecho ngati chouka kwakufa
People have power more than the army and police. Malawians shouldn't be intimidated These institutions are there to defend and protecting Malawian not intimidating please. Intimidations and threats will never work.
Lero muli English Mr Born kalindo wakwiya heavy, yes tili ndi zoyankhula anthufe nde poti tilibe kuthekera please spoke to us Mr, awa akuonjeza
Our Pangolin the Deeeceee
Akanachuluka anthu otelewa bwezi Malawi atasintha
The DC😂
Penatu anthu mumakonda mango pansana owopya amawopa mademo 5years yatha kale osawuka alipobe iweyo umbuli wathandiza chani aMalawi akuvutikawa Nonse andale ndiwofanana iweyo suja anafera kuvhosa Peter muthalika sanalakwe lelo wabwera Ndi boza lina
Mr Kalindo your respect .....you are our ambassador keep it up
Acondenser bas
Aziuzidwa ngamo ndipo Valentino Phiri usamale ndikuchikamwa kwakoko
Ulemu wanu d c❤❤❤❤❤❤
Kalindo saliyekha amlawife tilikumbuyo kwake ndipongati amumange mumange tonsefe sitikukuwopani inu a silikali mumalo moti mutetedze nzika koma mukutetedza chipani cholamula cha mcp zoona anthutu akuwukiranitu pasachedwapa ndetizawone muzatiphe tonsefe ndikutetedza chakwerayo ndi gululake
Upite akakuphuzitse achina nundwe bwezi titathatu thawi ya dpp, ukubisa chani, tonse mutitha koma ukolora
The dc 😂😂😂😂😂😂munuro iwe kadura ukamapita kwa bon muguliretu mabokosi anu osatipatsa busy osalafe
Uyu nde anatopa naye kumumanga pano amasowa chomumangirano😅
Njeza village
Ok ,,vuto ndiloti wamkulu wa army amachita kupangidwa apoint by the state president, had it been amachita kuvotedwa or through applying on vacant position bolaaaa,, but mene wanenera DC its so pathetic, MDF must stand between, and i feel sorry akamalankhura these Institution leaders does not regard that in their departments there are mixed people with mixed political parties, such that writing one biased stanza might violet some😮,,
Ku MDF, kuli ena a DPP, UTM, MCP, UDF, AFORD, PP sikuti they are all happy with biased statements and actions carried out
Mbuli zaathuizi zinangokhala pamawudindopo
ndili pa mbuyo panu bwana DC
Ngati titafe tidzafa chifukwa cha mbendera 🇲🇼 imenei,,, anapitadi ngati bodza eeeeeeee
Chomvetsa chisoni mchakuti anthu ogwira ntchito ma department amenewo sangakwanitse kumanga nyumba ndi salary yao popanda kutenga ngongole chifukwa imakhala yochepa bwanji sakupanga zoti aonjedzele malipiro
Anthu awiri awa ali mbali ya chikangawa government
Ndipo bon kalindo wanena zoona zokha zokha osawopa osatopa osafowoka
Kodi a police wonse Ku Malawi ko NDI army yonse ndizi tsiru zokha zokha eti?Achitetezo ama lowerera za ndale,tinali Ndi general Chigawa Osati Chitsiruu ngati chimenechi, ndipamene chiri kuda bii Ngati makala mpamene adapha nawo Chilima panyini pa Mache wamkulu wa polisi yoo, Ndi Wa army yo,tizawona DPP akayamba,akuchoka amenewa pa Nyero pa azimayi wao wonsewo
*Zikuonjeza osanama mmalawi wathu koma mulungu alinafe ndipo akumva kulila kwathu*
banja lodala la mutharika sitiziwa makolo awo adawalanga bwanji? Sizipukwatu zakumadzi alien
2025 ndi unoyi chakwela anapha chilima kupangila this year, Mantha ena achakwela ndife amalawi kaya atiphaso kaya
Koma yaa
Wa nkulu wa MDF mbole yake ndi chitsiru kwambiri sakudziwa ntchito yake akufuna aziophyeza anthu pantumbo pake panyini pamai Ake panyini pamai ake
Chilungamo chimawawa bola zaveka tu poti chilungamo chinayandikana ndi mwano koma dc wanena chilungamo wa kunva wanva
Kkkkkkk akt azawabandukatu Ena watopa Dc
Asala dimezi yochepa kuti chito iwathele akuopa thawi yawo ya tha gati mene ananenela pa dayele kuti ufumu wani watha
Zitsiru ndaona ma commander kuno ku malawi koma awa ndiopusa olo yohane sadapangepo zopusa kodi chimene adalumbirira umachiziwa? zopusa ngati ukuzipopa osapita kukalanda nyanja bwanji? Zopepera ukuona ngati asilikari ndi achipani?
Kodi commander uyu bwanji akugwiritsidwa kwambiri pa ndale pamene onse ambuyomu samapanga zoterez
Ndi savage muone chinkhope ngati mfiti
Ndpo awone zomwe zacitika ku Mozambique ma family ena asilikali amagwidwaso kumaphedwa ndi athu amademo ndye iwowa ma family awo awathawisiletu
guys now it's 2much mkulu wasittikali eeeee ndava chisonk olo kusitikali sinapiteko how men like that
Mwana owopsa zedi
Chilungamo ichi
The DC
❤❤
Koma bwana kalindo mumatiimilila amalawi koma apapa zikuonekelatu kuti anthuwa ndiomwe aja anali ku MCP kumbuyokuja MOTi mwina ma president omwe anali pakatipa maybe sakawakonda zikuonekelatu kuti amafinya chifukwa wa ame sangazilowelela izizi aaaaaaaaa
Koma uyuyu ndiyemweyu
Kkkkkkk
Awuzen zoona akamba zopusa akuiwala kt achoka kumudxi
The Dc
A Bon kalindo muzingolankhula Chichewa chifukwatu chizunguchi chimakugayani
Inu ndaabodza chamugaya pati
Inuo kuphunzila kwa mbiri?? Za zii muli mbuuu
Waziwa bwanji ndi chizungu?
Tamuwuze wodziwa chizungu abweletse mafuta.
Makomenti achithuphya party sasowa, kalindo anali mphunzitsitu ngat simukuziwa asanayambe ndale ndiye chizungu munenacho chalakwika pati
❤❤
The DC