TIKUDZIWENI - 18 MARCH 2019 with Lazarus Chigwandali
HTML-код
- Опубликовано: 8 сен 2024
- In this week's Tikudziweni, Senior Presenter Brian Banda talks to Lazarus Chigwandali, a man with albinism who is using music to fight evils people with albinism are facing in the country.
He was joined by his managers, Spiwe Zulu and Esau Mwamwaya.
👍👍😍zilibwino
This is awesome! All we need is the love of no boundaries, empowering each other!
I like this guy's, God bless you.
Proud of you Brian, you chill with anyone by not looking the way someone is looking
God bless you guys zimenezo ndiye zofunika kumagona nkumamva kukoma kuti mwasinthapo moyo wa munthu wina.
Good hearted people....bravo
Amazing
Amazing God bless you guys
Thanks Sphiwe and Esau keep on helping those people God blessvu guys
Following Braani Banda zikukoma ndipo inakukhala program ya tikudziwen, God bless you
Proud of you my brother sphiwe....keep on helping the needer
Brian Banda: Your programme is so interesting seeing you with Lazarus. Watching from Sandton RSA.
Brian please musamanene kuti kuoneka pa BBC sizocheza, tiyeni nafenso tidzichemerera zinthu zathu, kuoneka pa TTT kapena TV station iri yonse yachimalawi ndi chinthunso cha mtengo wapatali.
Anyamata inu Mulungu azikudalitsani,ndinu anthu opanda nsanje,dziko la pansi likadakhala ndi mtima ngati wa inu,anthu ambiri akadapita chitsogolo,Mulungu akudalitseni ndithu
Guys MULUNGU azikudalisani sanje mulibe
Mulungu alemekezeke
Yewo yesu
Kkkkkkkkkk koma zosangalatsa zedi iiiiiii Razarus wandiseketsa or kuisisita ndengeo kkkk
Zofunika izi abale athu achialubino akufunika zisomo zamulungu ngat izi
Koma Inu Anyamata inu mulibe jealous. .Ambuye akudalitseni