Well done chawezi, an accurate translation of the report. Komana mwadula dula for this ikanakhala extended ,uti asadumphe dumpe. Simunanene mafunso omwe enquiry imayankha, kapena what they recommended? Ngati dzikoli liri lachilungamo anthu ena amangidwe chifukwa cha negligence and incompetence.
Kodi maloya ndi majaji mukunenawo...ntchito yawo ku Malawi kuno ndi chani? Kukhala muma committee ofufuza kapena kugamula milandu. Nkhani za alubino, cash gate, chisale, phwiyo, mapeto whitehead. General chigawa, muli matafali, majaji 5 kupangidwa offer ndalama, satta, escom house ndi zina zambili.... Zinathela kuti, zinatha bwanj? Majaji ake siwomwewo. Mukati jaji wakuti anali momwemo pofufuza....mukuthawauza kuti sipangakhale chinyengo... Please stop being naive. Kumudzi kuno sikungatukuke till there transformation ku judiciary....l am not saying CHANGE the judiciary no. Total transformation including inuyo ma journalists. You can't do investigative journalism. Pali mayi wina wayipisa mbili ya kaliati pankhani yomweyi....palibe akuyankhula olo mayi kaliati can't defend herself to such an allegation....don't you find that strange. Her name is soiled but its business as usual.
Chawezi you are the best
Well done chawezi, an accurate translation of the report. Komana mwadula dula for this ikanakhala extended ,uti asadumphe dumpe. Simunanene mafunso omwe enquiry imayankha, kapena what they recommended? Ngati dzikoli liri lachilungamo anthu ena amangidwe chifukwa cha negligence and incompetence.
A Mcp awa
😂chawezi usamaoneke ng at I odziwa zaziiii
Enawo nde angovomera....mabodzawo
Lero ndinu madolo mawa mudzakhala makape tiyenazoni
Chawezi uzikumbuka kut kukusala mez 8, zingayambe kukusalira
Akanafa m'bale wako Galu iwe. Iwe unaona ndege Kuti inafika ku Mzuzu .Ungaliudze dziko kuti aPule samadziwa kuti SKC wabwera mdziko muno? Kwinaku nditukwana zamkabudula
Ee koma achilima amadyetsa anthu ambili ndiye kuti amakusamalani kuposa abale anu anamwalila aja? Mizimu ya abale anu.ikuyendeleni ndipo ikukwileni ipange nsanje chifukwa mukusapota mizimu yoti siyabale anu
Kodi maloya ndi majaji mukunenawo...ntchito yawo ku Malawi kuno ndi chani? Kukhala muma committee ofufuza kapena kugamula milandu.
Nkhani za alubino, cash gate, chisale, phwiyo, mapeto whitehead. General chigawa, muli matafali, majaji 5 kupangidwa offer ndalama, satta, escom house ndi zina zambili....
Zinathela kuti, zinatha bwanj?
Majaji ake siwomwewo.
Mukati jaji wakuti anali momwemo pofufuza....mukuthawauza kuti sipangakhale chinyengo...
Please stop being naive. Kumudzi kuno sikungatukuke till there transformation ku judiciary....l am not saying CHANGE the judiciary no. Total transformation including inuyo ma journalists.
You can't do investigative journalism. Pali mayi wina wayipisa mbili ya kaliati pankhani yomweyi....palibe akuyankhula olo mayi kaliati can't defend herself to such an allegation....don't you find that strange. Her name is soiled but its business as usual.